A man in Chikhwawa has been killed after he was found skinning his child’s skull.
According to a source, the man wanted to take out the child’s brain in order to sell it. The child has since died. Fellow villagers have however stoned the man to death.
More details to follow.
shaaaaaaaaaaa khaya ndi ndalama komi iiii ayi ndithu.
God have mercy!
Satana sanyendi mapazi kumalawi .munthu wa mulungu iwe poyamba pake umayamba bwanji.uyang’ane bwino majeti amene akugulidwa ndikulowa m’malawi.air port amavomela.bwanji??????????????
Sad nws
Sad nws
Sad nws
Sad nws
Malawi dziko la mkaka ndi uchi chakuwona ndichani? Eishiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
Malawi dziko la mkaka ndi uchi chakuwona ndichani? Eishiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
its scary
Last days no wonder but hey guys this is too much poverty musnt take you to this point of killing each other ..work and get paid try to make something on your own..Zokhimiranazi munayambira muja look at those who believed in that kind of shit whre they are today..?Stoned him to death isnt enugh l wish l was around chained him and tow him with car till he s finshed into pieces..He was real bastard that guy to hail straight..
Hesh maundilibe
Anthu a ku Chikwawa asowa pogwira ndalama yavuta kumeneko nanga adya chiyani?
Malawi wa sanduka network yasatana tsopano
Malawi wa sanduka network yasatana tsopano
Lord have mercy
Eeee guyz ichinso ndi cian abale
25 yrs in jail with hard-labour for him…WITCH
koma dziko la malawi zafikapo
Ayayaya umphawiwu uchimwitsa ambiri gazi lako zoona?
Mmmmm Malawi
Zoopya mmasiku wo tsiriza
Mmmm
Lord of mercy
Komaakuluakulu ukambachilungamo tsikulomalizalo mulungu ndiyeakalangadi anaakuphedwawa siatsogoleliamawa amewa ? Ambuye tiululilenichinsinsi chimene musungila moyowathuyu, komamulungu akalangadi iiiii.
Mmmmm noo why? Shocked!
hmmm koma wats goin on in Mw if I may ask today umva Albino this tomorrow eeeeeh mafupa lero izi za mwana wosalakwa ngati uyu somewhere somehow Malawi we r under attack by Devil pofunika kulipemphelera zolimba kuti mulungu atichosele chiwanda chimenechi
eeee ndangozizidwa..
mmm. koma chani malawi iwe?
mmm. koma chani malawi iwe?
We are in the last days when people like money than God.
Koma mwanayo alimoyo ???
Ufiti wopitira ku xul uwu sure!! Devil @ his work
malawi chikukutsata ndi chani?
Very bad
sign of last dys, tilape ndi kubatizidwa
…. … …. tanic
now what is happening in Malawi is strange,dreadful and extraodinary which is uncalled 4 .Malawi now is no longer the warm heart of Africa but the cold heart of Africa
Jesus is about to come believe me
That’s not a good news at all he deserve to die too
God pliz punish malawi, we r going on the wrong direction.
God pliz punish malawi, we r going on the wrong direction.
Nanga tikulowela kuti, abale tiyeni tikondane
Nanga tikulowela kuti, abale tiyeni tikondane
Malawi simwakale anamela manuo
Malawi simwakale anamela manuo
Munthu Akuwopsya Kuposa Zinyama Masiku Ano
Munthu Akuwopsya Kuposa Zinyama Masiku Ano
Tit for tat well done those of you who have killed this man because if he was to be arrested he would come back to kill other. Now that he is dead children will be safe
Tit for tat well done those of you who have killed this man because if he was to be arrested he would come back to kill other. Now that he is dead children will be safe
zonsezi the root is money too much kuzisaka
zonsezi the root is money too much kuzisaka
very sad
very sad
Zoooopsa
Sad newz mmmmm!
Yooooooooo!!!! Ndilibe chonena zandipatsa mantha
Yooooooooo!!!! Ndilibe chonena zandipatsa mantha
Very bad,Malawi where are you going???? Tell us….
fuck is him amuchita bwino
This is symbol end of the world Gayz tichenjele.
amupheranji mesa mwanayo ndiwake munthuyo? nosense
He was not only skinning the child’s but wanted to kill.Its an attempted murder case
it’s because of these faulse profets, u can’t take anything from devil n expect no returns, blood shed is wat devil is after
This is beyond!but I thank the community who gave the wright judgement for stoning him to death.My community should continue doing this so that the rest should learn a lesson.
Nthawi ya MCP anthu opha anzawo nawonso amaphedwa, nanga lamulori munalichotseranji abale? Tawonani masiku ano kupha munthu sinkhani. anthu akudziwa kuti ku court akapatsidwa 10years imprisonment and by the grace of the devil they can make it and come back to society and continue with their archaic behaviours. The fruits of democracy. Zachilendo pa Malawi.
I cry for my beloved country Malawi……
So inhuman!!!!!
Kholo Limeneli Tiziti Ndi Mulungu Wachiwiri? Ndapota Nanu Makolo! Tikathodwa Timabwera Kwa Inu, Nkhanza Zimenezi Tithawira Kuti?
guys let’s pray hard, your own kid doing that? may the Lord forgive you
Ndakhumudwa ndi izi mwanaokhala wawo
Zoopsa za masiku omaliza ndiye ndizimenezi,
Kumati Malawi z a God fearing nation? Mmmmmmh No takhala tikudzinamiza kwanthawi yaitali en mulungu akationa amangonva chison ndithu
Eee,komatu Malawi Wasanduka Agalatiya Tsopano, Albino Akusowa Mtendere Ndiye Anaso Kodi?
Too bad! God forgive us
He deserve to die!!
Koma mwanayo Ali Moyo?
Zachabe.chabe
Shupiti, mukanamudula machende alimoyo
u pipo ar sure priz tiyeni tisaikwanisile dara nthawi pliz. its over mmwandi.
Azibambo eish!Whoa!
Boma la pitala chilichonse chasokonekera basi…ma albinos akuzuzika kuphedwa zina nd izi aaaah bola kaleso
الحقوووو :O بمناسبة قرب حلول شهر #رمضان المبارك كروت شحن ببلاش فودافون وموبنيل واتصالات انا اتشحنلي كارت 100 جنيه ادخل اشحن انت كمان وشوف تعليقات كل الناس الي شحنت لو مش مصدق من هنا >> http://goo.gl/fkybWd
anthu ozndkla ameneyo kip it guys am very proud of u.
Eye to an eye mob justice is only the solution otherwise tizingophana ngati nkhuku mpakana mwana?
He is satanic you did the rightful thing by stoning him to death
Wicked world
Y Malawi
Last days tikuenera kukhala ochenjera
Bambo ameneyi kunali kwabwino osabadwa ndioipa koposa,zakhala bwino kuti waweruzidwa moyenera.
Malawi wandikwiyitsa
Komano penapake ineyo ndikamaona zinthuzi,boma likanalimbikisa chitetetezo mnjira zingapo.aMalawife ndife anthu oopa mulungu yes,ndikuvomereza)komanso mukaonesetsa ndife anthu okhulupilira zitsamba heavy.Choncho satana akumatinyenga pogwiritsa ntchito zisamba ndi Chipembezo.Muzaonaife aMalawi chisinthireni ndale 1994 talandira mipingo yachirendo yoposa 90 komano boma silikufufuza zolinga zamipingoyi,munthu angochokera kwawo kuNigeria ndikuyambisa Church kuMalawi boma nkuvomereza kuti ndimmbusa,pamene munthuyo akufuna njira yophweka yolowera mdziko mwathu kuti ayambe zake zokhetsa mwazi waanthu osalakwa.Ndiye pamafunika pakhale comittee yaazibusa ndima detective kuti munthu akafuna kuyambitsa mpingo azifufuzidwa mokwanira chifukwa zipembezo zina ndizimene satana akugwiritsa ntchito pofuna kusokoneza dzina la Yesu.Azising’anganso ndi ena mwaomwe satana akugwiritsa ntchito,aMalawi anzanga tiyeni titsegule maso satana ali padriving seat.
were is our malawi
Satana watambalala pa malawi
Malawian Fake story
Ayi kutha kwa dziko sopano chikondi chasowa
Why skinning his own child skull, is he craze?
Malawi!Malawi! What’s going on???
Ndisazamveso kuti Mw is the warmheart of Africa
dont leave him
Alakwitsa kumupha one time,akanamba kaya kumudula chiwalo chimodzichimodzi ali moyo kuti nayenso akanamva ululu m’mene umakhalira.
What is Malawi turning into?
masiku osilidza ano tiona ndi kumva zachilendo mmmmm Malawi ndichani? ulemele usauke uzafabe zonse ndizotsala eeeeeee?
Like Tan zania likeMalawi oterewa aphedwe kwa nzathu kuno sanyengelela wakuba opha ma albino ana aphedwe basi. Midzi mu tikawapeza achiwembuwa aphedwe basi tikapita nawo ku police akatuluka mwachita bwino kupha galu ameneyi
madona
madona
Malawi akulangidwa kungoti tapanga khungu sitikuona.
ophaa zake naye aphedwe ramuro rikutero guys ngati mwakanika kupha guys plz ndiuzeni ndibwera ndi gireinda ndizayamba kudura kumene anaturukira mwana watisiyayo kenako ndizadura nkhosi wopha muzeke aphedwee ndiwo amene ari muguru rasataniki ameyo eich koma guys
Ameneyotu basi ndi wa shire ng’ona zikumbuke chikale.
such an innocent soul, malawi is no longer safe, i wonder how the mother is feeling right now…. God please comfort her. and my the baby’s soul rest in peace…. this is sad
The killers are guilty as the victim
koma abale zoopia
SHAME! Killing his own son?
God is very angry as a result of being blamed by these earthly leaders bcz of the drought
very sad nws malaw al pa moto walawlaw!
very sad nws malaw al pa moto walawlaw!
God help Malawi
we are enjoying in extra time,agentleman can nt do it to his kid maybe he is insane
Kod Malawi wanga adamka kut otchuka ndi mbiri yabwino?
Nyc treatment
Akawotchedwa ndi moto wosazima ameneyoooo!!!!!!
He deserves that judgment foolish idiot
Eeeeeee komanso guys APA NDE zafika pa chimake. God is watching!!!!!!
This is not latest news. It’s history and very archaic
Economy ya dziko ikamavuta zimachitika nzimenezi wina akulemphera Ntchito yake
What?!! A biological father? Oh no this is total insanity.I cry for my mother Malawi.
Mmmmmm
crying for nyasaland
Zosakoma
No,No.
Stoning was a quick death warrant.He was supposed to be tied to a tree branch, make some fire under neath, roast him slowly.
Lack of humane leads to a deadly prey attack like animals it’s so disgusting you don’t mess up with innocent people its SAD and nobody like it even our Heavenly Father poverbs 6
Malawi yasala nkhondo basi
civic education on mob justice, maphunziro pofuna kubwezera chilango chokupha ngati naye wapha:
yambani kumenya mwapang’ono pang’ono kuti ululu uzilowerera kenaka zimufunsani wapangiranji zoterezo nanga alipo angati amchitidwewu. mukatero mukhoza kumadula chiwalo chimodzichimodzi. pliz onesesani kuti pazidusa 4 hours asanafe kuti aziwona ululu waimfa. sibwino munthu kumukonza 20 minutes basi mkumwalira ndiye mumakhala ngati mwamupha ndimfutitu imene imfa yake siipweteka. zimafunika kumadula mkono ndi chikwanje mbali yosathwa kapena yosanola ija mpaka mkonowo uduke. zandikwiyisa kwambiri
Eish!,satana pano ali pa chiongolero jst imagine mwana wake kuntero,,,he deserve to b killed
Ufiti basi
Eshiii! this not Malawi I used to know!
Ashame!whr mw going on
Musade nkhawa kasala kanthawi kochepa ulamuliro pano uli mmanja mwa oyipa. The chapter is about tobe closed. Tingoti pheeeeee tione
Thats bad I think b4 stoning this man, first the same thing should have been done to him
a dem father
If it is the love of money, eish! Then you made a wrong choice.
wawo or wanga??
I support the idie of banning traditional doctors there are the ones encouraging this malpractice
Fucken idiot he deserved to be stoned
Good job people of chikwawa for killing the father
Msambi.mwana osalakwa kumupha mwankhanza chocho?komabe ndakunyadirani anthu akuChikwawa simulora nosense,mwagwira ntchito yotamandika pokupha Chilombocho,simunthu ameneyo
Ndangozizidwa ine
opha nzake aphedwe, ndiye nkhani yaketu basi.
Akongolelenji mwana ?,mzimu wake uuse mumtendere #MHSRIP amen
It wasnt enough. They could have stoned him to death, and then burnt him to ashes
Opha Mzake Aphedwe
Iiiiiiiii koma abale ndichani kodi amalawi ndi maluzi omwewa kapena ufiti?
koma abaleeeee dzikolikupita kuti?
Ameneyo mtembo wake musaike nsanga nafe tizagendeko njokayo
Ijoo
Stoning him wasn’t a best solution. I mean,he deserved something better than that. I don’t care the reason why he did that but adhawo amayenera nawonso asendedwe. End of story…
Yesu wayandikira tikhale maso
why such an innocent soul ??
Zakhala Bwino Pati Nayeso Waphedwa Imfa Yowawa Munthu Woyipa Ameneyi Poti Samadziwa Kubeleka Komaso Umunthu Analibe
Ziwanda kapena eti.
koma zowopya
PAli magulu azipembezo ndi asing’anga akumalengezesa kuti KODI MUKUFUNA CHUMA? Bwerani kwa…..MAGULU amenewa musamale nawo kapena athesedwe at once ZIZASITHA Once kapena kutheratu .ino sinyengo ya MANNA a Busa ma sheik phuzisani molingana ndi thawi

Eish
Bambo opusa ameneu, kutengela kusaudziwa ululu momwe ukhalira kti mwana abadwe
Jesus is really coming soon, tsoka kwa okwanilisa malemba
Mchani kod amalawi?
if this things wouldnt b hapening,wat wuold u say about bible? the time has come ,alimmaso aone,alimtulo akale choncho.
Ena tikufuna ana, ena akuwasenda, zoona koma amalawi zmenezo????
Congrats pomupha.diso kwa diso even a police ali happy ntchito yawachepela yopita ku court ndi vampire ameneyu
Oooh!… my Allah!!…. let’s prying had akapolo amulungu dix ix end of our dziko let’s believe it ma brothers and ma sisters
dairy nkhani ikhale yakupha basi Malawi????? koma ndiye wafikapo
dairy nkhani ikhale yakupha basi Malawi????? koma ndiye wafikapo
That man deserve to die
That man deserve to die
kufuna kukhwimatu konseko
kufuna kukhwimatu konseko
koma picture mwaikayitu ndiyabodza. No blood oozing
koma picture mwaikayitu ndiyabodza. No blood oozing
Can’t u see that the child is dead? Open the link for more info
Zikungosonyezela2 kuti tili masiku otsiliza palibile2 umunthu .am very shocked & scared oh my lord…..
Zikungosonyezela2 kuti tili masiku otsiliza palibile2 umunthu .am very shocked & scared oh my lord…..
Science imeneyo koma ndiye mwamalizatu eeee!!!!! Zamasiku otsiliza
Science imeneyo koma ndiye mwamalizatu eeee!!!!! Zamasiku otsiliza
Now that’s what i cal justice keep it up chikwawa !
Now that’s what i cal justice keep it up chikwawa !
The bad thing is that they stoned him too much forba short time and he died. Skinning his skull first and stoning him finally could have made a good combination before he died. What was he thinking to do that, in Malawi these days people have no respect for life God gave others.They think theirs is more important than others.

Malawi stop thinking about witchdoctors why .?why a man like him doing this to a innocent child like that ….?he must burning ever hot in gahena
Malawi stop thinking about witchdoctors why .?why a man like him doing this to a innocent child like that ….?he must burning ever hot in gahena
What that Fu,,,,,,,,,k
What that Fu,,,,,,,,,k
Mmalawi akakopela chinthu kuti wadziwa chili ni ndalama amakhala nacho serious galu, dududu wachabechabe kukonda ndalama ngati hule
Mmalawi akakopela chinthu kuti wadziwa chili ni ndalama amakhala nacho serious galu, dududu wachabechabe kukonda ndalama ngati hule
Mwana yo alimoyo pano
Mwana yo alimoyo pano
brothers en sisters when u liking things do u know what u like or u dnt know? cause on this isue there’s no nothing to like here this is sad news think about it b4 u coment en like this devil at the work, may his soul rest in piece this child

wat has this world come to?
wat has this world come to?
Where is this world going to with such atrocities?
Where is this world going to with such atrocities?
Mmmm its over Malawi iwe. Mukuti Malawi akupita kuti? Umphawiwo wayambira iwe? Chilango chokuphacho ndikuona kut sichikukwanira coz mwana wako obala wekha sungamupange zimenezi, nanga mai amwanayo alikuti?

Ubwino wake mwat ndwake nde chowawa nchan pamenepa ngat mmamuthandiza kudyesa
Ubwino wake mwat ndwake nde chowawa nchan pamenepa ngat mmamuthandiza kudyesa
iiiiiiii km Malawi ndi chaniiii??????
iiiiiiii km Malawi ndi chaniiii??????
We have nothin’ we’re nothin’ still doing stupid instead o praying, ufit wakumalawi wauphawi akut kuli usatanik wauphawi prezdent GAlu wanchila
We have nothin’ we’re nothin’ still doing stupid instead o praying, ufit wakumalawi wauphawi akut kuli usatanik wauphawi prezdent GAlu wanchila
kodi Malawi yiziwike ndi kuphana conde siyani ufiti manyazi atipeze plz
kodi Malawi yiziwike ndi kuphana conde siyani ufiti manyazi atipeze plz
M’MASIKU OTSIRIZA ZIZAFIKA NYENGO ZOWAWITSA;CHIKONDI CHA PA UBALE CHIZACHOKA,ANTHU AZAKHALA OKONDA NDALAMA,OZIKONDA,ODANA NDI CHABWINO KUMAKONDA ZOIPA,OTSAZILETSA etc(2TIMOTHY C 3V1:3.)ANTHU ena kaya amaganiza bwanji kaya.Zoona kupha mwana wako?THIS IS SATANISM and indeed its inhuman,why killing innocent blood why!!!!!mwana iwe Mzimu wako wuuse mtendere, moyo unaufuna ,kuukonda koma amene umaganiza kuti ndi mnansi wako ndiye Chilombo chako.Zoona nkhondo ndi anansi.YOUNG GIRL ONCE AGAIN REST IN PEACE.
Ada amenewa alandira chilango pansi pompano
Ada amenewa alandira chilango pansi pompano
God what happened to that land of God fearing, i believe satani has found loot in Malawi thats the examples of the book of the revelation we better play hader because we are going towards to the end God for give our bueatful Malawi in Jesus name amen.

Weldone mob
Weldone mob
Koma vuto nkukhala chiyani abale.
???
Koma vuto nkukhala chiyani abale.
???
Ooooooooh!!!!! thr is now too much wickedness in the hat of man…. ooooooooooooooooooooo!!!!!!
Ooooooooh!!!!! thr is now too much wickedness in the hat of man…. ooooooooooooooooooooo!!!!!!
walakwa chani mwana. RIP Kumene uli uko akumbuse abambo awo kuti iwe si mpamba.
walakwa chani mwana. RIP Kumene uli uko akumbuse abambo awo kuti iwe si mpamba.
bamboyo mwamupha pang’ono mudakamudulaso mutu
bamboyo mwamupha pang’ono mudakamudulaso mutu
So sad mchiyani amalawi azanga,tikupita kuti mulungu konzani malawi wamvunda zedi kholo malo moteteza ndikuphanso
So sad mchiyani amalawi azanga,tikupita kuti mulungu konzani malawi wamvunda zedi kholo malo moteteza ndikuphanso
Ambiri tilibe mayakho, pazimene dziko dziko la Malawi likudutsamo. Komo bible limanenetsa kuti utsogoleri umabweletsa Madalitso or matembelero. Kodi ife utsogoleri wathu ndi otani pamaso pa mulungu.
Ambiri tilibe mayakho, pazimene dziko dziko la Malawi likudutsamo. Komo bible limanenetsa kuti utsogoleri umabweletsa Madalitso or matembelero. Kodi ife utsogoleri wathu ndi otani pamaso pa mulungu.
Am failing to understand… How could a father do that? These are indeed last days. God have mercy on us. Warm heart of Africa is perishing. I can’t even trust my blood relatives hmmmmm
Am failing to understand… How could a father do that? These are indeed last days. God have mercy on us. Warm heart of Africa is perishing. I can’t even trust my blood relatives hmmmmm
Why my Malawi???
Why my Malawi???
inhuman
inhuman
Amalawi ufiti tawonjeza
Amalawi ufiti tawonjeza
koma chikwawa chake patipati?
koma chikwawa chake patipati?
Amalawi ufiti tawonjeza
Amalawi ufiti tawonjeza
Ndakondwa ndi chiganizo chopamba cha wanthu a mudziyu kamba wakupha mnzake ayenera naye kufa
Ndakondwa ndi chiganizo chopamba cha wanthu a mudziyu kamba wakupha mnzake ayenera naye kufa
kuMalawinsotu kwayamba kudabwitsa mzedi aaaah
God fearing nation imeneyi eti ?? …
kuMalawinsotu kwayamba kudabwitsa mzedi aaaah
God fearing nation imeneyi eti ?? …
mmmmmmm malawi malawi dziko laponda satana ili kukonda ndalama osakonda wana dats not fair
mmmmmmm malawi malawi dziko laponda satana ili kukonda ndalama osakonda wana dats not fair
achina nyanga bomza
It’s insane!!
It’s insane!!
Mache……ake why why malawi dzikolija basi lawonongeka
Mache……ake why why malawi dzikolija basi lawonongeka
zachisoni ndizochititsa mantha
zachisoni ndizochititsa mantha
what is wrong with this country…..what the $%#& is this? are we that rotten?
what is wrong with this country…..what the $%#& is this? are we that rotten?
iii8iiiiiiiiiii guyx
iii8iiiiiiiiiii guyx
chakula ndi umphawi pa malawi ndi chifukwa anthu akumaganiza njila zolakwika zopezela ndalama koma sibwino kutengeka ndi anzathu omwa ali ochita bwino chifukwa sitikudziwa njila zomwa amapezela ndalama zawo

Amen
Amen
Was he a normal or an insane person? Anyway he has been given a fair punishment .
Inna lillah wa inna Illaih laji’un
They could have also skinned his skull.
They could have also skinned his skull.
Mmmmm too bad
Mmmmm too bad
Kodi ndiye ufiti wanji uwu mwayamba amalawi???
Kodi ndiye ufiti wanji uwu mwayamba amalawi???
Kumupha ndi miyala galu ameneyu palakwika kumafunika kumumangirira kumbuyo kwa track nkumududuluza mpaka ku Mozambique Chitsiru
Kumupha ndi miyala galu ameneyu palakwika kumafunika kumumangirira kumbuyo kwa track nkumududuluza mpaka ku Mozambique Chitsiru
OMG
OMG
Jesus is coming soon,
Jesus is coming soon,
Amuchita bwino kumupha mdala ameneyu coz akanagwidwa kupita naye ku police akanatuluka pa bail kapena akanamangidwa nkupita kundende kumakadyanso zakudya za boma zogula ndi ndalama zathu za misonkho. Kambewu kameneka ka anthu oterewa nkofunika katheretu poti boma silifuna kuvomeredza zakuti wakupha mzake aziphedwa njira yabwino ndi yomweyi basi, kugwira kukonza tokha.

There is big devil in Malawi, the country we respect.
There is big devil in Malawi, the country we respect.
U better read the book of revelation,if u have never read it be4.
U better read the book of revelation,if u have never read it be4.
Malawi! God help you.
Malawi! God help you.
devil at work. Is using the word poverty. Careful my fellow poor brother. Pray hard so that u may not be tempted.
devil at work. Is using the word poverty. Careful my fellow poor brother. Pray hard so that u may not be tempted.
This iz deval issue is not normal personal ivene he doesn’t have the spirit of God or human beings
This iz deval issue is not normal personal ivene he doesn’t have the spirit of God or human beings
Akafele kundende
Akafele kundende
ku malawi kuli boys kota ya satana
ku malawi kuli boys kota ya satana
Its likely that these things are going to continue happening cause the agent of satan himself is seating on the oily chair #sitinati
Its likely that these things are going to continue happening cause the agent of satan himself is seating on the oily chair #sitinati
Komano monga ine mMalawi okhuzidwa sindikufuna kuti ndimve kuti apolisi akufuna kuamanga anthu amugenda ndikupha mfitiyi,koma ndizakhala okondwa nditamva kuti apolisi akufufuza kumene mkuluyu amafuna kukagulitsa bongo wamwanayo.

Ambuye,bwelani muzatiweluze!!
Ambuye,bwelani muzatiweluze!!
Ine ndidaziwa kut dziko lathu pamene akut ndi loopa Mulungu kubwela ena nkumat ndi mpingo kuli kodzela satana kut azigwilirako nxthito zake lelo si izi mwana walakwa chan nanga amafuna atani nawo apulezident akungoyang’ana izi? Ndimamulira Mbendela bas kuwinitsa chitsilu chosadziwa mwanachi kut amabwela bwanji pano adakwatila chidukwa xha ndalama za upulezident machende ake ndipo pano akadakhala kut kumaloledwa ku nyumba kwake ine akadandiphela komweko

it’s not about Mr president Mr, let’s stop blaming the govt, it’s just that malawians have lost direction
Paja ndi wakwanu mundilakwitsa
KKkkkkkkkk aah mjomba mukutionjezatu
eeee nde akhara ndani ku kuMalawi
eeee nde akhara ndani ku kuMalawi
Munthu wamzeru zake kuganiza zaumfiti chocho osamasaka maganyu olima bwanji ngati mwavutika nde mumpha angati? khalani ndi umoyo wa uzimuuuu
Munthu wamzeru zake kuganiza zaumfiti chocho osamasaka maganyu olima bwanji ngati mwavutika nde mumpha angati? khalani ndi umoyo wa uzimuuuu
Ku chikwawa mutinyozetsa ufiti bwanji
Ku chikwawa mutinyozetsa ufiti bwanji
Under the influence of the devil. So sad
Under the influence of the devil. So sad
He deserve to die
Difficult to understand ndithu,ur own blood? Anthu amaononga ndalama kufuna mwana,osati kuononga Moyo WA mwana kufuna ndalama. Ameneyo ndi boliboli eti? He deserved to die like that
Where was the mother inu?
I hope she thought she had left the baby in the safe hands being a father.
Malawi for sale mmmmmm my Malawi where are you going where the Malawi known as warm heart of Africa now is cruel heart of Africa is better to be a foreigner and safe
Huh, you’re certainly not safe as foreigner – especially in South Africa. And you know it!
Huh, you’re certainly not safe as foreigner – especially in South Africa. And you know it!
I am safe than be hunting like animal
I am safe than be hunting like animal
This country is cursed
Mhuuuuuuu koma abale! Malawi ziko lamtendere lija taliwonongaso abale? shyaaaaa tsoka mtunda, Nyanja ndi mazi poti oipayo wasikira kwathu kuno sopano,
Chifukwa chani munthu uyuyu alipo maganizo otani, Koma mpaka chonchi abale plz? Aaaa wayenera kuulandira ukali wa Yehova !!!!!!!
God fearing nation now z evil national
mmmmmmmm this is sad story kodi nchiyani amalawi chomwe tayamba,kodi mkufuna kupeza chuma, plz dzikoli latsala pang’ono kung’ambikatu only god who knows,poti satana ali busy kufuna anthu omwe akalowenawo ku gehena
We must apply shareeah . Tit for tat and exclude western rights
Graphic image yet you display the picture as a headline
Yh,i think showing the pic like this is bad taste.
Yh,i think showing the pic like this is bad taste.
MOB JUSTICE RULES
Ziko linkuka kumalecheleche ili.
Better.
so bad please, why malawi why???
dziko lino ndi lotembeleledwa ndipo Yesu adzaweruza Malawi ali osaukabe ngakhale tikuphana
KOMA SATANA WALOWA KUMALAWI KUNOYU WATULUKIRA MBALI ITI EISH!!
ulesi umadzetsa ufiti amalawi. tiyeni tigwire ntchito molimbumika kuti tipewe izi. komano bambo ameneyu amuchita bwino
Mmmm people are realy hard hearted!! I have no word to say
The spirit of Assyrians on rampage!!! Churches don’t go to holiday!! The country need more prayers than before
Tooth kwa tooth
Kholo lomwe linayenera kukhala loyambilira kupeleka chitetezo kwa mwana apa zachitika mosemphana ndiye anawa athawira kuti? Paja mbewa zapa mapesi moto ukafika zimati ndithawire kopanda motoko, zimangowona ndodo zadikilira thupi lake, apa umatha kuona ikubwerera ku moto konko! An innocent kid.
God of mercy .please have great mercy to the country of Malawi eeeeshiiii so bad
Thank you all villagers for good job u done
…… Let’s kill all tradional healers coz that’s the source of all these madness…..
Mmmm wow no comment on this evils thing
he deserved it
My oohh…my…… Pls dis is nt good seriously but wat is really happening now? So sad……
Ma albinos akukhala mwamantha chifukwa tikuwapha!ananso aziwopa makolo?akabisala kuti?Malawiiii!Malawi iiii!rest in peace evison matafale for crying on behalf of our nation Malawi!this is beyond imagination
mukazaona zizindikilo izi ziwani kut chiweluzo chayandikila,koma inu khalanibeni maso
kulakwa uku mmmmmmm
Poor mind.
SHAME
Mfiti mwana wa njoka
So sad
Did they ask him where he was going to sell,if not am sad and angry! may the child soul rest in eternal piece of God and that of the father go straight to hell,iiiya ngati anali wampingo asamuimbire chifukwa ine ndikawabararitsapo ampingowo,zandikwiitsa kwambiritu
mulowerere ambuye……..by k baracks
This is in human
? ? ?
keep it up malabians dats de only solution 2 such people. Next tym just cut off both hands so dat he z able 2 feel pain.
WTF!!!!!
Anapenga??
Masiku omaliza
OK
Abale this is too much…Lord have mercy…an innocent soul has gone like this? Ooh no
We need GOD intrvesition to ur country MALAWI
Something is really wrong with Malawi . Trust me.
Very good
Sisi mwandisesha!
My dear I can’t take it anymore, bana sure, very vulnerable , why involve them in such, if you want to get rich get a day job like most of us, how have you been dear
Thats very unfortunate sis. I have been well and how are you?
Hobbes said, “Man is a wolf to another man.” imagine. Ambuye choooonde tapota nanu.
Mmmmmh ufititu kumupanga chonchi mwana ngt ukupanga dongo??? kma anthu ena eeeeeh ai mmmmh
What is happening in Malawi? Eeeeee zoopsa!
This has spoiled my night!
Koma zoona adayenda ndi mapazi satana pa malawi pano olo dziko lili m’manja mwa Galu mukuti chani a Malawi mwatani inu mwana wobala wekha ndithu akuchita bwino kukupha mene asowera mwanamu iiii mmmh
dzikolili mmanja mwa agaludi, ana akusowa??
Eti?
Iii umunthu unachoka inu mwamva
Iii umunthu unachoka inu mwamva
Mau man achita bwinodi iya.
Mau man achita bwinodi iya.
Dziko lilim’manja mwaagaludi ili!! Akukanika kubwelesa death sentence. Sindizamuvotela Galu ameneyu(prof. Pitala muthalika).
Dziko lilim’manja mwaagaludi ili!! Akukanika kubwelesa death sentence. Sindizamuvotela Galu ameneyu(prof. Pitala muthalika).
I new this before vote I rated JB better than APM u voted for musova
Ndiye mwati pitala watani ayi bodza sipitala ayi ndi umphawi kuphatikiza chamba musamikise ndale ndi chamba chachitikachi ayi.
Kkkkk Wantuma Ndi Pitala? Nzeru Zachepa.
I fil sori to the baby i wish him to get wel soon.
WTF?
Koma Amalawi Ndichani?Ndalama Basi Tiyeni Tilimbane Ndi Thaka Yathuy Ndiyomwe Ingatbweletsele Ndalama Zochuluka Not Killing Each Other God Pliz Help Us
So heartless
What people are doing in our generation is more dangerous than being beaten by poisonous cobra we are in our last days
Chikwawa nsanje timatero
this is beyond my imagination!but why my malawi!eishhhhhhh!
A Ritual murders avalanche…Signs of the time
Mmmmm!!! Koma Zoopsa
Eish! My Malawi
Shame
my mother Malawi where is this Malawi going mmmm Jehovah have mercy and muyendereni Malawi.
Nonse Mwagenda Munthuyo Ndikulembani Ya Police Forrum Mwayitha
Amchita Bwino Munthuyo Fanz Ya Ck
Ambuye bwerani nsanga.
ltink d faza wz mentally ill
Koma dzikoli abale
So bad. He deserved the punishment.
People r so evil nowadays!!! This is so terrible
Eeeee zandiopsa z bwanji kwenikweni a Malawi?
kodi ufiti chani makamaka??????
ya onse omwe agwira ntchito yogenda mfitiyi ofunikadi kuwalemba upolice Bravo ck pple 4 stoning tht wild animal to death Nde muva apolice ati akufunafuna amange omwe agwira ntchito yabwinoyi amangidwe
Mike kunotu ndikumalawi usayiwale malo moti awayamikiredi athu agwira tchito yotamandikayo pokhaulitsa bambo wakhazayu owona amangidwadi zovuta wava
eeee zopsa!!!!,,,,,,eee ndilibe chonena
deserved him right, ruthless brat
Eish!!!! Plz GOD hav mercy on us kwasalano kudyana tokhatokha plz GOD do somting mulowelerepo
Tisamve kuti anthu omwe apha bambo amwanayi amangidwa diso kulipa diso
I like the spirit of people from, Chikwawa, Nsanje and Neno, they don’t like bushit
Mmmm ndi zosadabwitatu izi bible linanena kale za masiku wotsiliza, zayambika zizindikilo
kukhosi kwanga kuti myaaaaa wakhala ndiamene akusautsa azathu alubino tiotchaso
Oh my god
Sad
koma abale mmmmm ayi ndithu Eish!!!!!
hmm kma gayz mwanayo ndiwaked ameneyu? apa pokha lamuro ligwire ntchito
Lord have mercy on us eish
May his soul rest in peace
Koma apo ndiye wakumana nazo ndipo anthu onse amene amugenda miyala munthuyi agwira ntchito yotamandika ndipo ndikanakhala president ndikanawalemba ntchito yaupolisi.
malan sukunama iyaa ndili mbali yako
Last days.
eshhhhhh dats bad rilly rilly bad
Wtf did I just read
may the child’ soul rest in pc
Oh my God dziko laipad ili timve za albino panonso izi mulowelerepo ambuye.
We need to pray strongly for our nation. This is very abnormal
Achita bwino kumupha nayenso amve kuwawa ngati mwanayo
End of days
Winau nd ufiti bax,last dyz.
Iiiiii Komazandikhuza
amuchita bwino well done the ck pple ambuye bwerani muzaononge malawi uja wasanduka nyama yolusa munthu akuopsq kuposa mkango
Eish abale zaonjeza ku Malawi
i believe devil has descended in Malawi how things are now we better pray had Malawians those signs in Bible i guess we have applied them My pray God of mercy i dont asky more but shed as more light so that we should know which is good and bad Amen
Zoooooooooopsa
kwambiri now is devil at work
koma chilembwe anabwela pa ndalamai atipwetekesa aliense phuma kufuna zachangu
Maluzi
Eeeee!God heip us
koma chilembwe anabwela pa ndalamai atipwetekesa aliense phuma kufuna zachangu
Miracle money needed maludzi anyanya
Za masiku osiliza….ndalama patsogolo
Koma abale……mxiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
The world is about to end so tiyeni chonde tikonzeke
What type of messed up human being was he? How can you do that to another human being?
ee wakumana nazo mdala ameneyu,mmm kupha mwana chifukwa chofuna kulemera?
Uchisilu Kodi iye Akanamupanga Chochi Makolo Bwezi ali Moyo
Aaa umenewo ndiuchitsiru? Ufitiwo ungamamupange munthu nzako like that ngati ukupanga chiweto kapena dongo?
Koma nde Uyu Wanyanya Ufiti Wake nde Kayaso.Kulemela ndi Magazi ndinthu MULUNGU alowelelepo.Mwana Mumene Aduliramu
Shame!!!
but for what…! may God v mercy on us we become so evil.
mmmmmmm ai kulakwa
kutamba masana mxiiiiiii
Koma akulu akulu ngati tufuna dollar tiyeni tilimeni osati izizi ayi
Kodi a Malawi zimenezi mukuzitengera kuti?Zinthu zinazi tiyamba kuwawopsyeza alendo osacheza dziko muno kamba kamakhalidwe onyasa amene tikupanga fe amalawi. Malo mulimbika kugwira ntchito kaya Bizinezi olo kulima zimenezo ndizinthu zomwe zingathese umphawi Kaya kupita kujoni ndi njiranso imodzi tingathese umphawi ndikusiyana ndikumapha albno ndizina zonyasa ngati zimenezi.
Amapanga anthu brain wash amwene like ya bambo waku Kasungu opha mwana wake alubino ija ati anamuuza kuti amugura 1 billion Kwacha it cant happen #Billion simaseweratu
Amapanga anthu brain wash amwene like ya bambo waku Kasungu opha mwana wake alubino ija ati anamuuza kuti amugura 1 billion Kwacha it cant happen #Billion simaseweratu
damn
He z,a witch