Man stoned to death for skinning child’s skull

465
IMG-20160528-WA0004

the child

A man in Chikhwawa has been killed after he was found skinning his child’s skull.

According to a source, the man wanted to take out the child’s brain in order to sell it. The child has since died. Fellow villagers have however stoned the man to death.

More details to follow.

 

Share.

465 Comments

 1. Satana sanyendi mapazi kumalawi .munthu wa mulungu iwe poyamba pake umayamba bwanji.uyang’ane bwino majeti amene akugulidwa ndikulowa m’malawi.air port amavomela.bwanji??????????????

 2. Last days no wonder but hey guys this is too much poverty musnt take you to this point of killing each other ..work and get paid try to make something on your own..Zokhimiranazi munayambira muja look at those who believed in that kind of shit whre they are today..?Stoned him to death isnt enugh l wish l was around chained him and tow him with car till he s finshed into pieces..He was real bastard that guy to hail straight..

 3. Komaakuluakulu ukambachilungamo tsikulomalizalo mulungu ndiyeakalangadi anaakuphedwawa siatsogoleliamawa amewa ? Ambuye tiululilenichinsinsi chimene musungila moyowathuyu, komamulungu akalangadi iiiii.

 4. hmmm koma wats goin on in Mw if I may ask today umva Albino this tomorrow eeeeeh mafupa lero izi za mwana wosalakwa ngati uyu somewhere somehow Malawi we r under attack by Devil pofunika kulipemphelera zolimba kuti mulungu atichosele chiwanda chimenechi

 5. now what is happening in Malawi is strange,dreadful and extraodinary which is uncalled 4 .Malawi now is no longer the warm heart of Africa but the cold heart of Africa

 6. Tit for tat well done those of you who have killed this man because if he was to be arrested he would come back to kill other. Now that he is dead children will be safe

 7. Tit for tat well done those of you who have killed this man because if he was to be arrested he would come back to kill other. Now that he is dead children will be safe

 8. This is beyond!but I thank the community who gave the wright judgement for stoning him to death.My community should continue doing this so that the rest should learn a lesson.

 9. Nthawi ya MCP anthu opha anzawo nawonso amaphedwa, nanga lamulori munalichotseranji abale? Tawonani masiku ano kupha munthu sinkhani. anthu akudziwa kuti ku court akapatsidwa 10years imprisonment and by the grace of the devil they can make it and come back to society and continue with their archaic behaviours. The fruits of democracy. Zachilendo pa Malawi.

 10. الحقوووو :O بمناسبة قرب حلول شهر #رمضان المبارك كروت شحن ببلاش فودافون وموبنيل واتصالات انا اتشحنلي كارت 100 جنيه ادخل اشحن انت كمان وشوف تعليقات كل الناس الي شحنت لو مش مصدق من هنا >> http://goo.gl/fkybWd

 11. Komano penapake ineyo ndikamaona zinthuzi,boma likanalimbikisa chitetetezo mnjira zingapo.aMalawife ndife anthu oopa mulungu yes,ndikuvomereza)komanso mukaonesetsa ndife anthu okhulupilira zitsamba heavy.Choncho satana akumatinyenga pogwiritsa ntchito zisamba ndi Chipembezo.Muzaonaife aMalawi chisinthireni ndale 1994 talandira mipingo yachirendo yoposa 90 komano boma silikufufuza zolinga zamipingoyi,munthu angochokera kwawo kuNigeria ndikuyambisa Church kuMalawi boma nkuvomereza kuti ndimmbusa,pamene munthuyo akufuna njira yophweka yolowera mdziko mwathu kuti ayambe zake zokhetsa mwazi waanthu osalakwa.Ndiye pamafunika pakhale comittee yaazibusa ndima detective kuti munthu akafuna kuyambitsa mpingo azifufuzidwa mokwanira chifukwa zipembezo zina ndizimene satana akugwiritsa ntchito pofuna kusokoneza dzina la Yesu.Azising’anganso ndi ena mwaomwe satana akugwiritsa ntchito,aMalawi anzanga tiyeni titsegule maso satana ali padriving seat.

 12. Alakwitsa kumupha one time,akanamba kaya kumudula chiwalo chimodzichimodzi ali moyo kuti nayenso akanamva ululu m’mene umakhalira.

 13. Like Tan zania likeMalawi oterewa aphedwe kwa nzathu kuno sanyengelela wakuba opha ma albino ana aphedwe basi. Midzi mu tikawapeza achiwembuwa aphedwe basi tikapita nawo ku police akatuluka mwachita bwino kupha galu ameneyi

 14. ophaa zake naye aphedwe ramuro rikutero guys ngati mwakanika kupha guys plz ndiuzeni ndibwera ndi gireinda ndizayamba kudura kumene anaturukira mwana watisiyayo kenako ndizadura nkhosi wopha muzeke aphedwee ndiwo amene ari muguru rasataniki ameyo eich koma guys

 15. such an innocent soul, malawi is no longer safe, i wonder how the mother is feeling right now…. God please comfort her. and my the baby’s soul rest in peace…. this is sad

 16. Lack of humane leads to a deadly prey attack like animals it’s so disgusting you don’t mess up with innocent people its SAD and nobody like it even our Heavenly Father poverbs 6

 17. civic education on mob justice, maphunziro pofuna kubwezera chilango chokupha ngati naye wapha:
  yambani kumenya mwapang’ono pang’ono kuti ululu uzilowerera kenaka zimufunsani wapangiranji zoterezo nanga alipo angati amchitidwewu. mukatero mukhoza kumadula chiwalo chimodzichimodzi. pliz onesesani kuti pazidusa 4 hours asanafe kuti aziwona ululu waimfa. sibwino munthu kumukonza 20 minutes basi mkumwalira ndiye mumakhala ngati mwamupha ndimfutitu imene imfa yake siipweteka. zimafunika kumadula mkono ndi chikwanje mbali yosathwa kapena yosanola ija mpaka mkonowo uduke. zandikwiyisa kwambiri

 18. Stoning him wasn’t a best solution. I mean,he deserved something better than that. I don’t care the reason why he did that but adhawo amayenera nawonso asendedwe. End of story…

 19. PAli magulu azipembezo ndi asing’anga akumalengezesa kuti KODI MUKUFUNA CHUMA? Bwerani kwa…..MAGULU amenewa musamale nawo kapena athesedwe at once ZIZASITHA Once kapena kutheratu .ino sinyengo ya MANNA a Busa ma sheik phuzisani molingana ndi thawi

 20. PAli magulu azipembezo ndi asing’anga akumalengezesa kuti KODI MUKUFUNA CHUMA? Bwerani kwa…..MAGULU amenewa musamale nawo kapena athesedwe at once ZIZASITHA Once kapena kutheratu .ino sinyengo ya MANNA a Busa ma sheik phuzisani molingana ndi thawi

 21. The bad thing is that they stoned him too much forba short time and he died. Skinning his skull first and stoning him finally could have made a good combination before he died. What was he thinking to do that, in Malawi these days people have no respect for life God gave others.They think theirs is more important than others.

 22. The bad thing is that they stoned him too much forba short time and he died. Skinning his skull first and stoning him finally could have made a good combination before he died. What was he thinking to do that, in Malawi these days people have no respect for life God gave others.They think theirs is more important than others.

 23. Malawi stop thinking about witchdoctors why .?why a man like him doing this to a innocent child like that ….?he must burning ever hot in gahena

 24. Malawi stop thinking about witchdoctors why .?why a man like him doing this to a innocent child like that ….?he must burning ever hot in gahena

 25. brothers en sisters when u liking things do u know what u like or u dnt know? cause on this isue there’s no nothing to like here this is sad news think about it b4 u coment en like this devil at the work, may his soul rest in piece this child

 26. brothers en sisters when u liking things do u know what u like or u dnt know? cause on this isue there’s no nothing to like here this is sad news think about it b4 u coment en like this devil at the work, may his soul rest in piece this child

 27. Mmmm its over Malawi iwe. Mukuti Malawi akupita kuti? Umphawiwo wayambira iwe? Chilango chokuphacho ndikuona kut sichikukwanira coz mwana wako obala wekha sungamupange zimenezi, nanga mai amwanayo alikuti?

 28. Mmmm its over Malawi iwe. Mukuti Malawi akupita kuti? Umphawiwo wayambira iwe? Chilango chokuphacho ndikuona kut sichikukwanira coz mwana wako obala wekha sungamupange zimenezi, nanga mai amwanayo alikuti?

 29. We have nothin’ we’re nothin’ still doing stupid instead o praying, ufit wakumalawi wauphawi akut kuli usatanik wauphawi prezdent GAlu wanchila

 30. We have nothin’ we’re nothin’ still doing stupid instead o praying, ufit wakumalawi wauphawi akut kuli usatanik wauphawi prezdent GAlu wanchila

 31. M’MASIKU OTSIRIZA ZIZAFIKA NYENGO ZOWAWITSA;CHIKONDI CHA PA UBALE CHIZACHOKA,ANTHU AZAKHALA OKONDA NDALAMA,OZIKONDA,ODANA NDI CHABWINO KUMAKONDA ZOIPA,OTSAZILETSA etc(2TIMOTHY C 3V1:3.)ANTHU ena kaya amaganiza bwanji kaya.Zoona kupha mwana wako?THIS IS SATANISM and indeed its inhuman,why killing innocent blood why!!!!!mwana iwe Mzimu wako wuuse mtendere, moyo unaufuna ,kuukonda koma amene umaganiza kuti ndi mnansi wako ndiye Chilombo chako.Zoona nkhondo ndi anansi.YOUNG GIRL ONCE AGAIN REST IN PEACE.

 32. God what happened to that land of God fearing, i believe satani has found loot in Malawi thats the examples of the book of the revelation we better play hader because we are going towards to the end God for give our bueatful Malawi in Jesus name amen.

 33. God what happened to that land of God fearing, i believe satani has found loot in Malawi thats the examples of the book of the revelation we better play hader because we are going towards to the end God for give our bueatful Malawi in Jesus name amen.

 34. Ambiri tilibe mayakho, pazimene dziko dziko la Malawi likudutsamo. Komo bible limanenetsa kuti utsogoleri umabweletsa Madalitso or matembelero. Kodi ife utsogoleri wathu ndi otani pamaso pa mulungu.

 35. Ambiri tilibe mayakho, pazimene dziko dziko la Malawi likudutsamo. Komo bible limanenetsa kuti utsogoleri umabweletsa Madalitso or matembelero. Kodi ife utsogoleri wathu ndi otani pamaso pa mulungu.

 36. Am failing to understand… How could a father do that? These are indeed last days. God have mercy on us. Warm heart of Africa is perishing. I can’t even trust my blood relatives hmmmmm

 37. Am failing to understand… How could a father do that? These are indeed last days. God have mercy on us. Warm heart of Africa is perishing. I can’t even trust my blood relatives hmmmmm

 38. chakula ndi umphawi pa malawi ndi chifukwa anthu akumaganiza njila zolakwika zopezela ndalama koma sibwino kutengeka ndi anzathu omwa ali ochita bwino chifukwa sitikudziwa njila zomwa amapezela ndalama zawo

 39. chakula ndi umphawi pa malawi ndi chifukwa anthu akumaganiza njila zolakwika zopezela ndalama koma sibwino kutengeka ndi anzathu omwa ali ochita bwino chifukwa sitikudziwa njila zomwa amapezela ndalama zawo

 40. Amuchita bwino kumupha mdala ameneyu coz akanagwidwa kupita naye ku police akanatuluka pa bail kapena akanamangidwa nkupita kundende kumakadyanso zakudya za boma zogula ndi ndalama zathu za misonkho. Kambewu kameneka ka anthu oterewa nkofunika katheretu poti boma silifuna kuvomeredza zakuti wakupha mzake aziphedwa njira yabwino ndi yomweyi basi, kugwira kukonza tokha.

 41. Amuchita bwino kumupha mdala ameneyu coz akanagwidwa kupita naye ku police akanatuluka pa bail kapena akanamangidwa nkupita kundende kumakadyanso zakudya za boma zogula ndi ndalama zathu za misonkho. Kambewu kameneka ka anthu oterewa nkofunika katheretu poti boma silifuna kuvomeredza zakuti wakupha mzake aziphedwa njira yabwino ndi yomweyi basi, kugwira kukonza tokha.

 42. Komano monga ine mMalawi okhuzidwa sindikufuna kuti ndimve kuti apolisi akufuna kuamanga anthu amugenda ndikupha mfitiyi,koma ndizakhala okondwa nditamva kuti apolisi akufufuza kumene mkuluyu amafuna kukagulitsa bongo wamwanayo.

 43. Komano monga ine mMalawi okhuzidwa sindikufuna kuti ndimve kuti apolisi akufuna kuamanga anthu amugenda ndikupha mfitiyi,koma ndizakhala okondwa nditamva kuti apolisi akufufuza kumene mkuluyu amafuna kukagulitsa bongo wamwanayo.

 44. Ine ndidaziwa kut dziko lathu pamene akut ndi loopa Mulungu kubwela ena nkumat ndi mpingo kuli kodzela satana kut azigwilirako nxthito zake lelo si izi mwana walakwa chan nanga amafuna atani nawo apulezident akungoyang’ana izi? Ndimamulira Mbendela bas kuwinitsa chitsilu chosadziwa mwanachi kut amabwela bwanji pano adakwatila chidukwa xha ndalama za upulezident machende ake ndipo pano akadakhala kut kumaloledwa ku nyumba kwake ine akadandiphela komweko

 45. Ine ndidaziwa kut dziko lathu pamene akut ndi loopa Mulungu kubwela ena nkumat ndi mpingo kuli kodzela satana kut azigwilirako nxthito zake lelo si izi mwana walakwa chan nanga amafuna atani nawo apulezident akungoyang’ana izi? Ndimamulira Mbendela bas kuwinitsa chitsilu chosadziwa mwanachi kut amabwela bwanji pano adakwatila chidukwa xha ndalama za upulezident machende ake ndipo pano akadakhala kut kumaloledwa ku nyumba kwake ine akadandiphela komweko

 46. Difficult to understand ndithu,ur own blood? Anthu amaononga ndalama kufuna mwana,osati kuononga Moyo WA mwana kufuna ndalama. Ameneyo ndi boliboli eti? He deserved to die like that

 47. Malawi for sale mmmmmm my Malawi where are you going where the Malawi known as warm heart of Africa now is cruel heart of Africa is better to be a foreigner and safe

 48. Mhuuuuuuu koma abale! Malawi ziko lamtendere lija taliwonongaso abale? shyaaaaa tsoka mtunda, Nyanja ndi mazi poti oipayo wasikira kwathu kuno sopano,

 49. mmmmmmmm this is sad story kodi nchiyani amalawi chomwe tayamba,kodi mkufuna kupeza chuma, plz dzikoli latsala pang’ono kung’ambikatu only god who knows,poti satana ali busy kufuna anthu omwe akalowenawo ku gehena

 50. Kholo lomwe linayenera kukhala loyambilira kupeleka chitetezo kwa mwana apa zachitika mosemphana ndiye anawa athawira kuti? Paja mbewa zapa mapesi moto ukafika zimati ndithawire kopanda motoko, zimangowona ndodo zadikilira thupi lake, apa umatha kuona ikubwerera ku moto konko! An innocent kid.

 51. Ma albinos akukhala mwamantha chifukwa tikuwapha!ananso aziwopa makolo?akabisala kuti?Malawiiii!Malawi iiii!rest in peace evison matafale for crying on behalf of our nation Malawi!this is beyond imagination

 52. Did they ask him where he was going to sell,if not am sad and angry! may the child soul rest in eternal piece of God and that of the father go straight to hell,iiiya ngati anali wampingo asamuimbire chifukwa ine ndikawabararitsapo ampingowo,zandikwiitsa kwambiritu

 53. Koma zoona adayenda ndi mapazi satana pa malawi pano olo dziko lili m’manja mwa Galu mukuti chani a Malawi mwatani inu mwana wobala wekha ndithu akuchita bwino kukupha mene asowera mwanamu iiii mmmh

 54. Koma Amalawi Ndichani?Ndalama Basi Tiyeni Tilimbane Ndi Thaka Yathuy Ndiyomwe Ingatbweletsele Ndalama Zochuluka Not Killing Each Other God Pliz Help Us

 55. ya onse omwe agwira ntchito yogenda mfitiyi ofunikadi kuwalemba upolice Bravo ck pple 4 stoning tht wild animal to death Nde muva apolice ati akufunafuna amange omwe agwira ntchito yabwinoyi amangidwe

  • Mike kunotu ndikumalawi usayiwale malo moti awayamikiredi athu agwira tchito yotamandikayo pokhaulitsa bambo wakhazayu owona amangidwadi zovuta wava

 56. Koma apo ndiye wakumana nazo ndipo anthu onse amene amugenda miyala munthuyi agwira ntchito yotamandika ndipo ndikanakhala president ndikanawalemba ntchito yaupolisi.

 57. amuchita bwino well done the ck pple ambuye bwerani muzaononge malawi uja wasanduka nyama yolusa munthu akuopsq kuposa mkango

 58. i believe devil has descended in Malawi how things are now we better pray had Malawians those signs in Bible i guess we have applied them My pray God of mercy i dont asky more but shed as more light so that we should know which is good and bad Amen

  • Kodi a Malawi zimenezi mukuzitengera kuti?Zinthu zinazi tiyamba kuwawopsyeza alendo osacheza dziko muno kamba kamakhalidwe onyasa amene tikupanga fe amalawi. Malo mulimbika kugwira ntchito kaya Bizinezi olo kulima zimenezo ndizinthu zomwe zingathese umphawi Kaya kupita kujoni ndi njiranso imodzi tingathese umphawi ndikusiyana ndikumapha albno ndizina zonyasa ngati zimenezi.