In one of the most shared images on social media this week, some Malawi Police officers have been pictured drinking beer while on duty.
In the picture which has gone viral on the social media, the officers are seen taking Chibuku beer at a tavern.
After taking one too many, one of the officers surrendered his Eagle to a woman who is with them while another officer left his eagle on the ground.
Meanwhile, Malawi24 understands that the officers have been called to a disciplinary measures.
The development comes at a time when Malawians say they have lost trust in the law enforcers and that is why they take laws into their own hands.
Amatelo awa kkkkkkk
amafufuza zigawenga uku akukonkha umodz umodz
They are lame.
They are lame.
Kkkkkkkkkkk Malawi walelo?
Kkkkkkkkkkk Malawi walelo?
Kusiya kumaka gwila ntchito uko basi chonchi basi zopusa

azimwa ngati ndivuto palibe chanu ndimigwanya basi isiyeni iwusumane

Apolice athu
Kkkkkkk
Kkkkkkk
Koma ka namwaliko kalibe nkhawa mpaka kubaya chisoti akanso ndi kandio kawina pompa fanz ina inali ku malumu apa nanga zipewazo nzandani

This happens all the time
This happens all the time
AKATHA KUMWAKO ANYEMGE MAHULE MWA ULELE POWAOPYEZA

Guys a police nso ndi anthu like u. Enanso amaona bwino akuba akalezera kkkkkk

Vuto palibe ndi anthu naoso fii nosi?
Whats wrong?
kkkkkkk!!! zazing’ono izi amabaso Ali pa duty ndithu
Kumwa saletsa manje kamwedwe..
Page Ya M.24 Kamakonda zimamabodza chimakhla chli chni??
Akuti democracy kuseweresa ntchito zimwani tsiku lina muzamwa madzi
Its very difficult to explain,the scenarial is so liquidy! So icannot judge
ndie mukulemba ndizidude zomwe ndicholinga chomawabela malipo et. At police
let dem enjoy ………
aaaaaaaaa guys ifeyo tiziukhuta basi monga mukudziwa opanda kuukhuta aaaaaaa sizingayende timaiwalako zina ndi zina.inu atola nkhani vuto lanu nlotani inunso mukafuna kuukhuta ziukhutani basss,oky ndikumangatu!
sakulakwitsa akudya thukuta lawo
Malawi ndidziko limodzilomwe apolisi amapitakumowa alimu unifomu. Sitidabwapopeza ndidziko lopanda malamulo
iwe siumalezera ukakhala ku ntchito kwako? drink as u can provided they take care of dea families

aaa zijoyi azanu asafewetse
Mowa wakenso kukhala ngati matope ngati amenewa madeya ali kho.
Oh! mkwagona kumeneko ku Area 25,these policemen were indeed intoxicated to the extent why reaching to the point for someone to them a photo.They have to be retrained.
Kkkkk ayayaya MPS
doing investigations
doing investigations
akuonjeza anthu awa malamulo.kodi akuwalila kymwa mu uniform? police mungoithesa palibe chomwe akuchita kubwere a prison basi awa akapume.
No way that female is not apolice officer check the dressing try to zoom it! and irepeat,those officers were not ther to drink.@Wilson Timvere
Chakumwa chinapangidwa kuti chizimwedwa kodi kukhala wa police ndichifukwa? Alekeni azipepese.
Amapelekeka chitetezo ku bar ndiye paja okaona nyanja onaona ndi mvuwu zomwe asiyeni alibe problem.
kkkkkk njota nanga tinene kuti chani apa asaa!
Aaaa Busy Ndi Za Eni Anzanu Asazipepese Chikhale Chifukwa Osangopepha Bwanji Ngati Mumafuna Kumwa Nawo
Imwani bola musalandidwe mfutizo
Amazitolera
Ndipepha Mulungu wa kumwamba awafikire mwapadera.
Muzapite pa Matete road block mseu wa lakeshore after Tukombo Girls apolice daily amakhala ataledzela.Samapanso ayi.
Mipite pa Matete road block mseu wa lakeshore after Tukombo Girls apolice daily amakhala ataledzela.
Very stupid indeed, that’s why their talk shit wen the ask u things
Apa namadzi awa
Apa namadzi awa
Apa namadzi awa
So wat? Amamwela ndalama zako? Acyen amakhala ndi zolingao akakhala malo ameneo

Kumwa Choncho, Mawa Lake Nkumamva Kuti Adziomberapo, #puremalawipolice

KOMA KUBA BASI WE HAVE LOST TRUST IN THEM

mankhwala a ntchito nanga amenewo kkkkk
nde mpaka pamenepa abale,kkk
eya ntchito ndiyophana iyi imafunika ziwindi kkkkk

ukakhala mu blackout nde umuonanso mdaniyo nanga?
Open ur eyes properly bro,u cant see that the female officer is holding a beer packet on this pic? @Daniel_Gondwe
Kudzipepesa mix ka salary ka manja,sakukondwa nao salary yawoyo sakukondwa nao.
What is this? Koma a police enawa kkkkkkkkkkkk wataya chipangano
All hope= killed
Imwani bola musalezele kkkk
Amafikapena pochitisamanyazi tikamawaona akukangana pamowa kuseli kwa mtsika wa tsokaku ku mashabini iye ukumapusa ali mu chovala chaboma mmmmm
Kodi kumwa ndikulakwa.
Kkkkkkkkkkkkk zikapezeka dyeratu amwene
Malawi is free country police they have freedom for drinking on duties.
bvudzi ramudhra i atificial thus wy risingagerwe
Dzuwa lakula ili lofunika tsenga basi sakulakwa…
imwani koma musalezele Malume Paul anatero
Yavutatu nkhani iyi.These guys adziwika
Yavutatu nkhani iyi.These guys adziwika
even your staff members do drink while they are on duty so nothing to blame let the police officers do what they want they are also human beings

Palibe cholakwka apa bcoz apolice amagwla ntchto malo aliwonse

awa amayenera kumwa mowa akamaliza, kapena akaweruka, mowa sumaziziritsa kukhosi ayi koma paralyse thinking capabilities, remember this money they get paid for is tax payers money!
whoever supports this is fake policeman!

Asiyeni akonkhe kukhosi ntchito imatopetsa

Izo ndiye zimachitika ntchito zolembana pa ubale.Anthu omwe mulungu adawalenga kuti azakhale apolisi onse munawasiya chifikwa analibe abale mu department ya polisi.Lero mwatenga anthu oti mwina akanakhala zigandanga zoba ndi mfuti ndikukhala apolisi.Kodi ndizotheka kuti chigawenga chikamange chigawenga chinzake?Nkuwona lero mukuona anthu akudulidwa ziwalo,ma albino kuphedwa koma apolisi alipheee.A Malawi anzanga katangale ndi tchimo lalikulu zedi.Chonde apolisi lekani mchitidwe olemba Ana kapena abale anu kuti chitetezo cha dziko chibwelere mchimake.

Do u want to tell me drinking beer while on duty is not a problem?Think of other govt depts like,education,healthy and others.
stupid department of police stupid goverment too,,,,,those uniforms is not drinking chibuku and fucking bitches
Kumeneku Nde Kukhala, Ngati Khukhosi Kwauma Timwe Basi.
Azilonda phuma
Sagulaso amangomwela anthu akuti iwo ndi boma.
imavuta polowa ntchito
Mpakana hule kuvala chisoti!!!!! Kikkkk yalowa china
Kkkkkkkkkkk uli bhooo
Some weya ntcheu imwani mwakathithi plus ma hule ali pambalipa shaa no chitetezo agagwire akuba amenewa
Apolisi ayiwara zisoti kamba kolezera nchonchi ndi boma????? DPP boma
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.
Pliz guys be serious
koma yeah ! mumati apolisi samamwa? alibe zibwenzi ? nawo sakonda mahule? si okhawo pitani ku capital hill mukaone mmene ma bwana amamwera mma office mwawo.
Thanks Francis Kakhobwe for your likeness on my comment.
Is it TRUE ? Ngati ndichocho ku Malawi ndiye KWABOOOOKA. That’s why people take laws in there HANDS…………!
Esh !shame this is not Malawi iknow
Amalawi 24 inu simukudziwa kuti amati tumsni mbala ikagwire mbala imzake mwina pali chomwe akupanga investigate pali njira zosiyana siyana zomwe amafufuzira opalamula i wish munakawafusa kaya kuti ndichifukwa chani amapezeka apa
Eetu nanga mumati azimwa chiyani? Tamec?

Cholakwika ndi chani pamenepa?? Cholinga muzimwa nokha,, ifeso timafuna kumwako,,

Vuto palibe apa,cash yawo,ntchito akugwila vuto ndichani?

Mpolisi nayenso ndi munthu (bwana ni munthu nayeve chirile)
malawian police officers are lazy,cruel,corrupt& thugs who always bring huge challenges on their work places even outside there

None of the police officers on this photo is holding apacket of beer!you never know they might be investigating acrime the scene could be tactical dont judge before you find out the truth,apolisi ndianthu ngati inu nomwe bwanji chiyambireni simunajambure apolisi akugwira zigawenga?apolisi akhonza kupezeka pa maloomwera pazifukwa zomwe inu simungazidziwe zolingana ndi ntchito yawo

Auze dan!! Palibe chabwino chimene angalembe choyamikira wa police koma kunyoza basi
Bt mukaonetsetsa ths photo ws taken by fellow police officer anakhala opposite side n zipewa zawo aunjika apozo,kupwetekana okhaokha

Chifukwa chomwe anapezekera pa malopo ndichomwe akupangacho Tangoganiza ali wantchito wako ungautani? Ndi amakulembani chifukwa chachibale sakunama muwopa ndani! Or kopanga kafuku fukuko atengane onse?
how do u explain that bakha hat on that prositute’ head? was it identification parade? They might not have been drinking yes but this photo compromises the mps. Wat about zipewa aziunjikazo?
wat job were they performing on the scene? Nanga eni zipewa zapasizo alikuti ..sanak…ke?
Analipo gulu awa ena anali ku malumu mpaka katsunalo kutha mantha mpaka kubaya chisoti

Kkjkjk
MAHULE PLUS TABULALASSA!
They want to reduce stress of being paid peanut out of their dangerous job.

koma amene wajambuIayo amuziwa?kkkkkk upoIisi u naIowa china pano apoIisi ake akumavaIano jeans wamba ndi maIaya apoIice akazi nde akumaminuIa koma guys,kkkkkk poIice inaIi kaIe

Asiyeni azibambo ovala makatoni awa ndinthawi yoti amwelere nditi mahure mbalimu. Akaledzera azikayiwala nazo mfuti Ku room ya hure

Tell them to wear shorts again then easy to c them drinking give Minster of Police a Bells

Bwino bwinotu mkulu Akabulikah Francis
Bwino bwinotu mkulu Akabulikah Francis
ubwino wake police siyamunthu ngat zakunyasa achose ntchito basi

kkkkkkkkj
kkkkkkkkj
hahahaha
Komanso mowa sagula amangopemphetsa.kodi kuli subject yamomwe angapezele ndalama thru begging kusukulu kwaoko?Nanunso akazi amapolisi kuteleku mukudya zaumasikini.Mwathamangitsa opempha cholinga muzipempha ndinu.

what ashameless police
what ashameless police
Samagulaso Akafika Pamowapo Anthu Amenewa Kwawo Ndikupemphesa Mowa Basi Ali Mbuuuuh

waziwa bwanji mpaka mbuuu
Kkkkkk yatsala ndi mfuti kuti apeleke zipolopolo zili momo kkkkkkk zavuta pa malawi kkkkkkkk

Akaledzela kuyamba abuse kwa ma civilians

anthu amamwera zawo inu muli nazo vuto?
anthu amamwera zawo inu muli nazo vuto?
Mwina anali ataweluka
Mwina anali ataweluka
Above the law 1
Above the law 1
sopano athuwo azingoenda ndidzuwa akakomoka minsewumu akuyenela kuthila mafuta kaye muthaki….

Ngati salary yalowa asazipepese?
Ngati salary yalowa asazipepese?
Apolice ambili olembedwa ndi abale awo aaaaa no proft

Amene anatumiza chithunzi,ayembekezere kukumana ndizokhoma zomwe olo ambuyache sanakumane nazo,ili ndi dziko.

Malawi at 50
Malawi at 50
Malawi at 50
Zantchito abambo! Kumowa ndikomwe timanva zambiri, ka chakumwa pang’ono, investgation mkati! Ma sivilian mungatiuze chani inu! Timamwera zanu? Fokolo zanu!

Thats wat dey r gud @
Thats wat dey r gud @
Thats wat dey r gud @
Ubwino wake akumwera zawo
Ubwino wake akumwera zawo
Ubwino wake akumwera zawo
It’s a lot of people they looking job, fire them those idiots.

what about those who sleep in parliament ?

Wrong timing, while on duty?
Wrong timing, while on duty?
Wrong timing, while on duty?
Shame on my country
Shame on my country
Shame on my country
Kung’wemberera man kkkkkk kupha dzuwa. hahaha

mpaka kumveka chisoti hule kkkkkk alibho

Akamwapo ndipamene amawona patali.
Akamwapo ndipamene amawona patali.
Akamwapo ndipamene amawona patali.
vuto ndi chani ngati kukhosi kwauma asamwepo ??? anakupemphabi ndalama mwina? instead kut mupange zot zikuthandizeni basi busy kupanga za ena!!! asiyeni azipepetse nawonso ndi anthu ngat inu nomwe!! kkkk

kom inu eeeh kom anakakhala minbus driver ndye usanena kanthu

Akuba akumapezeka ndi unyolo kkkk autenga kuti? mbava ndi apolice omwewa

Kuchotsapo nkhawa
Kuchotsapo nkhawa
Kuchotsapo nkhawa
A Police ake ati omwewa a beniwa kkkkk taona apolice ife osati vidakwa dza ku Malawi

asiyeni akuchosa manyanzi kuti asamakhale Ndi manyanzi anagwira wakuba

chidakwa-chingagwile-ntchito-ndichifukwa-akuba-sakuopa-boma-liike-lamulo–kodi-mmene-zikuchitikilamu-wa-police-kumenyedwa-kumowa-mkumati-winawo-walakwa-kkkk-siwolakwa-zakumana-zidakwa-oledzela-mpakana-kuyiwala-malamulo-antchito—

Asanjoye!!
Asanjoye!!
Asanjoye!!
Nawonso ali ndi zofuna zawo za kunthupi
Nawonso ali ndi zofuna zawo za kunthupi
Nawonso ali ndi zofuna zawo za kunthupi
Anali pa ivestigation yoti mowa umakoma bwanji

Malawi sazatheka mpaka kale. Olo maiko ena anzathuwa sizikusiyana ayi akakugwila apolice amakuuza kut…. My friend plz make aplan. Kukakhala kumalawiko ndie amangot tapanga ya Fanta. Mmmm dziko lapans lavuta ili.

Akumwera zawo
Akumwera zawo
Nosence alibe chochita
Nosence alibe chochita
Dikilani muonenso zina
Dikilani muonenso zina
Amenewa ali ku mowa osati pa ntchito ndalama zakenso zowabera anthu pa mseu , vuto lorembana ntchito pa chibale ndilimenero .

Shame“`
Shame“`
akumat malipilo akuchepa daily kudzera mbavaso zimenezi stupid
akumat malipilo akuchepa daily kudzera mbavaso zimenezi stupid
Dikilani muonenso zina
Dikilani muonenso zina
Ndie bvuto lanu
Ndie bvuto lanu
Boma likuyenela kumva maganizo ainu anthu chifukwa ndinu mwaona zomwe apolice akuchita,mukuyenela kupeleka lipoti kuti adziwe ndiye mukamangoloza zala ena mupindulapo chani?.

ndakuziwa uku…ndi ku ‘Club-G’..kuseri kuja uku….kkkkkkkk

Mowa umenewutu unali opempha, chifukwa akanganya awa ndikuwadziwa bwino sangagule mowa. Kkkk!

Kkkkk amidia mpaka kutola photoz kkk koma anakakudziwa kuti ukwajambula akanakumanga pajatu bomali limadana ndachulungamo chifukwa apa watidziwitsako zomwe amapanga ali pa job kumafunika chomcho mkuwagulira wambiri mpaka akodzedwe nawo mkuwamangilira pamtengo zitsiru kwambiri

Nanga akadatani kukhosi kutauma?
Nanga akadatani kukhosi kutauma?
Ana opanda yesu awa.
Ana opanda yesu awa.
lolest
lolest
kkkkkkk they are enjoying life too
kkkkkkk they are enjoying life too
Mwina aweluka ndiye aonakuti kunyumba kwatalika kuti akavure makhakhiwo kkkkk

so what?
so what?
Mowaso ndioletsedwa kupolisi…? shatap nzanu

kuyambana nawo pamowapo kuwakuntha mosayang na nkhope akasuma kuti khani yakumowa thats a solution

Nde nsanga ngat zimenezo kkkkkk
Nde nsanga ngat zimenezo kkkkkk
Police idali kale pano kuli G4S!
Police idali kale pano kuli G4S!
I blame DPP government and its officials for all problems in Malawi including this

did dpp ordered them to drink on duty?
did dpp ordered them to drink on duty?
did dpp ordered them to drink on duty?
did dpp ordered them to drink on duty?
did dpp ordered them to drink on duty?
did dpp ordered them to drink on duty?
Stevie DPP ikuononga zinthu!!! they are drunk cause of dpp
zaboza zimenezo sizikugwirizana
zaboza zimenezo sizikugwirizana
zaboza zimenezo sizikugwirizana
part of life
part of life
Mpana kumveka Chipewa cha boma kamtsikanako? Nanga zikanakhala kuti amakupatsani mifuti kuti muziyenda nazo bwenzi mukumabesatu??

Kumangotha ndalama za boma basi, asaa kukanika kugwira mbava za mfuti nkumakalimbana ndi anthu osalakwa olima chamba

Plz tell us ndikuti kumeneko koma police yinali yakale kkkkkk

Nawonso amafuna kupha ludzu asiyeni
Nawonso amafuna kupha ludzu asiyeni
Malawi-
Malawi-
Nothing good comes out of Malawi policemen and women,they are bastards who ask you you where do you buy these things in your house

its rily rily shame
its rily rily shame
well done officers kumazipepesa mumagwira ntchito yolemetsa. amene zamuwawa akagule wake amwe

Kkkkk yonseeeee
Nanga atani
Nanga atani
Malawi woyee
Kikikikikikikikikikik
Kkkkkkkkk awa ali ku mowa osati pa duty.

Even the president does that give the boys break.

Akaledzera ndipomwe amagwira ntchito bwino…lol.Area 49 dubai mwafikapo eeeh

Police never help at all its just same as guards

Ndimene amachitira makape amenewa, mumowa momwemo ndi momwe amagwirizana ndi mbava za civilian mkumapatsana ma mission okuba. apolice ndiomwe akuonjezela umbava ndipo no wonder mifuti ikumapezeka ndi okuba ochuluka. munthu sangagwire ntchito molongosoka ataledzela.

Tayamayamikirankoni amamwatu wopatsa thanzi usanawawe, enanu mumamwa kachasu kkkk

kma amalaw ziko lathu silizathek bas mpak chipew kupatsa hule
Koma mowa wakenso umenewo hahahaha
Koma mowa wakenso umenewo hahahaha
Ndizachilendo lero? Kuno ndiye ndi daily.

They are drinking beer to save water
They are drinking beer to save water
koma mbava zmenez zoona kumawabera madriver pamseu ndalama zake ndkumamwera tkawapeza guys mubar moh tiwalande mowa komaso apasen makofi

Police on @ work!
kkkkkkkkkk
Ndi mutanawo anthu ngat ameneo?
Ndi mutanawo anthu ngat ameneo?
nawo ndi anthu asiyen
nawo ndi anthu asiyen
Nde kuti ndi zomwe amakaphunzira zimenezo kikikikikiki Ma Hule mkazi akatero basi kumangomanga anthu wosalakwa kusiya Zigandanga..Fotseki Zanu…..

DPP presidents drink whilst on duty: nothing new: Our leaders are a reflection of the society that chose them:
It’s really amazing how people drag the president in any problem
Alakwa chiyani Mr President pa nkhaniyi?

hahaha koma mfana umakwana
hahaha koma mfana umakwana
hahaha koma mfana umakwana
hahaha koma mfana umakwana
Kodi nkhaniyi akunena president kapena apolice,mudaphunzila kuti sukulu za kwacha zoponda nazo ma certificate anzelu ndimakhalidwe?.Umbuli sizinthu

uyu walemba nkhaniyi ndi mchawa paja xool yao ndi via madrassa

Ana mwee che mayilosi zonizo akuwecheta a plezedent akumwa ukana aaah werewo unamii! kkkkk

vuto lolembana pachibale ndilimenero nanga awopa ndani? ife ntchito imeneyi timkaifuna koma tinalibe achibale

iwe ndie walasa iwe…khokhokhokhokhooooooo

Kkkkkk eyetu bwana
Kkkkkk eyetu bwana
Kkkkkkk eee amwene no mbale pa company no ntchito

Zoona boss
Zoona boss
Zoona boss
Kkkkkk Mpaka Pano Zikuchitikabe Anyani Amenewa.

Ndaziona ine ndili kusouth Africa kuno koma ngati ulibe munthu okudziwa pa tchito basi udziwilet kuti chako palibe
Kkkkk malawi malawi koma kumeneko
Kkkkk malawi malawi koma kumeneko
Akanatani Utapezeka Mix Kuchosa Nkhawa Ndimavuto Akula Pa Malawi Pano