Trending: Malawi Police officers drink while on duty


Malawi Police officers drinking beer
Malawi Police officers drinking beer
Picture of Malawi Police officers drinking beer on duty is making rounds.

In one of the most shared images on social media this week, some Malawi Police officers have been pictured drinking beer while on duty.

In the picture which has gone viral on the social media, the officers are seen taking Chibuku beer at a tavern.

After taking one too many, one of the officers surrendered his Eagle to a woman who is with them while another officer left his eagle on the ground.

Meanwhile, Malawi24 understands that the officers have been called to a disciplinary measures.

The development comes at a time when Malawians say they have lost trust in the law enforcers and that is why they take laws into their own hands.  

384 thoughts on “Trending: Malawi Police officers drink while on duty

 1. Koma ka namwaliko kalibe nkhawa mpaka kubaya chisoti akanso ndi kandio kawina pompa fanz ina inali ku malumu apa nanga zipewazo nzandani

 2. Koma ka namwaliko kalibe nkhawa mpaka kubaya chisoti akanso ndi kandio kawina pompa fanz ina inali ku malumu apa nanga zipewazo nzandani

 3. aaaaaaaaa guys ifeyo tiziukhuta basi monga mukudziwa opanda kuukhuta aaaaaaa sizingayende timaiwalako zina ndi zina.inu atola nkhani vuto lanu nlotani inunso mukafuna kuukhuta ziukhutani basss,oky ndikumangatu!

 4. Oh! mkwagona kumeneko ku Area 25,these policemen were indeed intoxicated to the extent why reaching to the point for someone to them a photo.They have to be retrained.

 5. akuonjeza anthu awa malamulo.kodi akuwalila kymwa mu uniform? police mungoithesa palibe chomwe akuchita kubwere a prison basi awa akapume.

 6. No way that female is not apolice officer check the dressing try to zoom it! and irepeat,those officers were not ther to drink.@Wilson Timvere

 7. Amafikapena pochitisamanyazi tikamawaona akukangana pamowa kuseli kwa mtsika wa tsokaku ku mashabini iye ukumapusa ali mu chovala chaboma mmmmm

 8. even your staff members do drink while they are on duty so nothing to blame let the police officers do what they want they are also human beings

 9. even your staff members do drink while they are on duty so nothing to blame let the police officers do what they want they are also human beings

 10. awa amayenera kumwa mowa akamaliza, kapena akaweruka, mowa sumaziziritsa kukhosi ayi koma paralyse thinking capabilities, remember this money they get paid for is tax payers money!
  whoever supports this is fake policeman!

 11. awa amayenera kumwa mowa akamaliza, kapena akaweruka, mowa sumaziziritsa kukhosi ayi koma paralyse thinking capabilities, remember this money they get paid for is tax payers money!
  whoever supports this is fake policeman!

 12. Izo ndiye zimachitika ntchito zolembana pa ubale.Anthu omwe mulungu adawalenga kuti azakhale apolisi onse munawasiya chifikwa analibe abale mu department ya polisi.Lero mwatenga anthu oti mwina akanakhala zigandanga zoba ndi mfuti ndikukhala apolisi.Kodi ndizotheka kuti chigawenga chikamange chigawenga chinzake?Nkuwona lero mukuona anthu akudulidwa ziwalo,ma albino kuphedwa koma apolisi alipheee.A Malawi anzanga katangale ndi tchimo lalikulu zedi.Chonde apolisi lekani mchitidwe olemba Ana kapena abale anu kuti chitetezo cha dziko chibwelere mchimake.

 13. Izo ndiye zimachitika ntchito zolembana pa ubale.Anthu omwe mulungu adawalenga kuti azakhale apolisi onse munawasiya chifikwa analibe abale mu department ya polisi.Lero mwatenga anthu oti mwina akanakhala zigandanga zoba ndi mfuti ndikukhala apolisi.Kodi ndizotheka kuti chigawenga chikamange chigawenga chinzake?Nkuwona lero mukuona anthu akudulidwa ziwalo,ma albino kuphedwa koma apolisi alipheee.A Malawi anzanga katangale ndi tchimo lalikulu zedi.Chonde apolisi lekani mchitidwe olemba Ana kapena abale anu kuti chitetezo cha dziko chibwelere mchimake.

 14. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 15. koma yeah ! mumati apolisi samamwa? alibe zibwenzi ? nawo sakonda mahule? si okhawo pitani ku capital hill mukaone mmene ma bwana amamwera mma office mwawo.

 16. Amalawi 24 inu simukudziwa kuti amati tumsni mbala ikagwire mbala imzake mwina pali chomwe akupanga investigate pali njira zosiyana siyana zomwe amafufuzira opalamula i wish munakawafusa kaya kuti ndichifukwa chani amapezeka apa

 17. Mpolisi nayenso ndi munthu (bwana ni munthu nayeve chirile)

 18. malawian police officers are lazy,cruel,corrupt& thugs who always bring huge challenges on their work places even outside there

 19. malawian police officers are lazy,cruel,corrupt& thugs who always bring huge challenges on their work places even outside there

 20. None of the police officers on this photo is holding apacket of beer!you never know they might be investigating acrime the scene could be tactical dont judge before you find out the truth,apolisi ndianthu ngati inu nomwe bwanji chiyambireni simunajambure apolisi akugwira zigawenga?apolisi akhonza kupezeka pa maloomwera pazifukwa zomwe inu simungazidziwe zolingana ndi ntchito yawo

 21. None of the police officers on this photo is holding apacket of beer!you never know they might be investigating acrime the scene could be tactical dont judge before you find out the truth,apolisi ndianthu ngati inu nomwe bwanji chiyambireni simunajambure apolisi akugwira zigawenga?apolisi akhonza kupezeka pa maloomwera pazifukwa zomwe inu simungazidziwe zolingana ndi ntchito yawo

  1. Chifukwa chomwe anapezekera pa malopo ndichomwe akupangacho Tangoganiza ali wantchito wako ungautani? Ndi amakulembani chifukwa chachibale sakunama muwopa ndani! Or kopanga kafuku fukuko atengane onse?

  2. how do u explain that bakha hat on that prositute’ head? was it identification parade? They might not have been drinking yes but this photo compromises the mps. Wat about zipewa aziunjikazo?

 22. koma amene wajambuIayo amuziwa?kkkkkk upoIisi u naIowa china pano apoIisi ake akumavaIano jeans wamba ndi maIaya apoIice akazi nde akumaminuIa koma guys,kkkkkk poIice inaIi kaIe

 23. koma amene wajambuIayo amuziwa?kkkkkk upoIisi u naIowa china pano apoIisi ake akumavaIano jeans wamba ndi maIaya apoIice akazi nde akumaminuIa koma guys,kkkkkk poIice inaIi kaIe

 24. Komanso mowa sagula amangopemphetsa.kodi kuli subject yamomwe angapezele ndalama thru begging kusukulu kwaoko?Nanunso akazi amapolisi kuteleku mukudya zaumasikini.Mwathamangitsa opempha cholinga muzipempha ndinu.

 25. Komanso mowa sagula amangopemphetsa.kodi kuli subject yamomwe angapezele ndalama thru begging kusukulu kwaoko?Nanunso akazi amapolisi kuteleku mukudya zaumasikini.Mwathamangitsa opempha cholinga muzipempha ndinu.

 26. Amene anatumiza chithunzi,ayembekezere kukumana ndizokhoma zomwe olo ambuyache sanakumane nazo,ili ndi dziko.

 27. Amene anatumiza chithunzi,ayembekezere kukumana ndizokhoma zomwe olo ambuyache sanakumane nazo,ili ndi dziko.

 28. Amene anatumiza chithunzi,ayembekezere kukumana ndizokhoma zomwe olo ambuyache sanakumane nazo,ili ndi dziko.

 29. Zantchito abambo! Kumowa ndikomwe timanva zambiri, ka chakumwa pang’ono, investgation mkati! Ma sivilian mungatiuze chani inu! Timamwera zanu? Fokolo zanu!

 30. Zantchito abambo! Kumowa ndikomwe timanva zambiri, ka chakumwa pang’ono, investgation mkati! Ma sivilian mungatiuze chani inu! Timamwera zanu? Fokolo zanu!

 31. Zantchito abambo! Kumowa ndikomwe timanva zambiri, ka chakumwa pang’ono, investgation mkati! Ma sivilian mungatiuze chani inu! Timamwera zanu? Fokolo zanu!

 32. vuto ndi chani ngati kukhosi kwauma asamwepo ??? anakupemphabi ndalama mwina? instead kut mupange zot zikuthandizeni basi busy kupanga za ena!!! asiyeni azipepetse nawonso ndi anthu ngat inu nomwe!! kkkk

 33. vuto ndi chani ngati kukhosi kwauma asamwepo ??? anakupemphabi ndalama mwina? instead kut mupange zot zikuthandizeni basi busy kupanga za ena!!! asiyeni azipepetse nawonso ndi anthu ngat inu nomwe!! kkkk

 34. vuto ndi chani ngati kukhosi kwauma asamwepo ??? anakupemphabi ndalama mwina? instead kut mupange zot zikuthandizeni basi busy kupanga za ena!!! asiyeni azipepetse nawonso ndi anthu ngat inu nomwe!! kkkk

 35. chidakwa-chingagwile-ntchito-ndichifukwa-akuba-sakuopa-boma-liike-lamulo–kodi-mmene-zikuchitikilamu-wa-police-kumenyedwa-kumowa-mkumati-winawo-walakwa-kkkk-siwolakwa-zakumana-zidakwa-oledzela-mpakana-kuyiwala-malamulo-antchito—

 36. chidakwa-chingagwile-ntchito-ndichifukwa-akuba-sakuopa-boma-liike-lamulo–kodi-mmene-zikuchitikilamu-wa-police-kumenyedwa-kumowa-mkumati-winawo-walakwa-kkkk-siwolakwa-zakumana-zidakwa-oledzela-mpakana-kuyiwala-malamulo-antchito—

 37. chidakwa-chingagwile-ntchito-ndichifukwa-akuba-sakuopa-boma-liike-lamulo–kodi-mmene-zikuchitikilamu-wa-police-kumenyedwa-kumowa-mkumati-winawo-walakwa-kkkk-siwolakwa-zakumana-zidakwa-oledzela-mpakana-kuyiwala-malamulo-antchito—

 38. Malawi sazatheka mpaka kale. Olo maiko ena anzathuwa sizikusiyana ayi akakugwila apolice amakuuza kut…. My friend plz make aplan. Kukakhala kumalawiko ndie amangot tapanga ya Fanta. Mmmm dziko lapans lavuta ili.

 39. Malawi sazatheka mpaka kale. Olo maiko ena anzathuwa sizikusiyana ayi akakugwila apolice amakuuza kut…. My friend plz make aplan. Kukakhala kumalawiko ndie amangot tapanga ya Fanta. Mmmm dziko lapans lavuta ili.

 40. Boma likuyenela kumva maganizo ainu anthu chifukwa ndinu mwaona zomwe apolice akuchita,mukuyenela kupeleka lipoti kuti adziwe ndiye mukamangoloza zala ena mupindulapo chani?.

 41. Boma likuyenela kumva maganizo ainu anthu chifukwa ndinu mwaona zomwe apolice akuchita,mukuyenela kupeleka lipoti kuti adziwe ndiye mukamangoloza zala ena mupindulapo chani?.

 42. Kkkkk amidia mpaka kutola photoz kkk koma anakakudziwa kuti ukwajambula akanakumanga pajatu bomali limadana ndachulungamo chifukwa apa watidziwitsako zomwe amapanga ali pa job kumafunika chomcho mkuwagulira wambiri mpaka akodzedwe nawo mkuwamangilira pamtengo zitsiru kwambiri

 43. Kkkkk amidia mpaka kutola photoz kkk koma anakakudziwa kuti ukwajambula akanakumanga pajatu bomali limadana ndachulungamo chifukwa apa watidziwitsako zomwe amapanga ali pa job kumafunika chomcho mkuwagulira wambiri mpaka akodzedwe nawo mkuwamangilira pamtengo zitsiru kwambiri

 44. Mpana kumveka Chipewa cha boma kamtsikanako? Nanga zikanakhala kuti amakupatsani mifuti kuti muziyenda nazo bwenzi mukumabesatu??

 45. Mpana kumveka Chipewa cha boma kamtsikanako? Nanga zikanakhala kuti amakupatsani mifuti kuti muziyenda nazo bwenzi mukumabesatu??

 46. Nothing good comes out of Malawi policemen and women,they are bastards who ask you you where do you buy these things in your house

 47. Nothing good comes out of Malawi policemen and women,they are bastards who ask you you where do you buy these things in your house

 48. Ndimene amachitira makape amenewa, mumowa momwemo ndi momwe amagwirizana ndi mbava za civilian mkumapatsana ma mission okuba. apolice ndiomwe akuonjezela umbava ndipo no wonder mifuti ikumapezeka ndi okuba ochuluka. munthu sangagwire ntchito molongosoka ataledzela.

 49. Ndimene amachitira makape amenewa, mumowa momwemo ndi momwe amagwirizana ndi mbava za civilian mkumapatsana ma mission okuba. apolice ndiomwe akuonjezela umbava ndipo no wonder mifuti ikumapezeka ndi okuba ochuluka. munthu sangagwire ntchito molongosoka ataledzela.

 50. Nde kuti ndi zomwe amakaphunzira zimenezo kikikikikiki Ma Hule mkazi akatero basi kumangomanga anthu wosalakwa kusiya Zigandanga..Fotseki Zanu…..

 51. Nde kuti ndi zomwe amakaphunzira zimenezo kikikikikiki Ma Hule mkazi akatero basi kumangomanga anthu wosalakwa kusiya Zigandanga..Fotseki Zanu…..

  1. Kodi nkhaniyi akunena president kapena apolice,mudaphunzila kuti sukulu za kwacha zoponda nazo ma certificate anzelu ndimakhalidwe?.Umbuli sizinthu

  2. Kodi nkhaniyi akunena president kapena apolice,mudaphunzila kuti sukulu za kwacha zoponda nazo ma certificate anzelu ndimakhalidwe?.Umbuli sizinthu

Comments are closed.