Police in Ntchisi district have netted 10 people for being found in possession of forest products.
According to the Public Relations officer for Ntchisi police station, Sergeant Gladson M’bumpha, the ten were arrested on 13 April 2016 at Kaombe forest reserve in the district.
“The incident took place on Wednesday at Kaombe forest when forest officials mounted a raid at the forest,” said M’bumpha.
He added that the 10 were netted when they were found with forest products.
M’bumpha further said that in the process they managed to recover 32 bags of charcoal.
The suspects will appear before court soon to answer charges of being found in possession of forest products.
Must go to hell with their cluel heart.
alangidwe akuwononga chilengedwe
alangidwe akuwononga chilengedwe
Njatani onse ndi odula mitengo akalowe kundende
Njatani onse ndi odula mitengo akalowe kundende
Mwaiwala ntchito mmalo mogwira mbava mwayamba kugwira wamakala
Mwaiwala ntchito mmalo mogwira mbava mwayamba kugwira wamakala
Amakala akuphwekelan mbala zili tho mmakukam…….. za ziiii!
Amakala akuphwekelan mbala zili tho mmakukam…….. za ziiii!
Zankutu za ziiiii
Kuti tipite ku nyumba za apolisiwo sitikapeza makala kapena amaphikira magetsi?This iz unfair!
Mukumanga ma charcoal burner instead of akashgate Why?
WHAT ABOUT THOSE WHO STOLE GOVERNMENTS MONEY??
Mxiewwww zazi
Inu aboma tayambisani ma project kuti anthu akuotcha makalawa apeze mwayi omakagwira ntchito kumeneko
Cant someone come up with a better logo for this police service
Zonsezi ndi umphawi
Eeeeesh koma zafikapa tituluka mu dziko lino wapansi ndithu
Ku ntchisi umbava wachuluka ,mukalimbana nimakala inuso mmakomo mwanu muli makala omweo bwanji sakumangani ucitsiru basi
Nkhani zake zomangilanazo za zi!
Nkhani zake zomangilanazo za zi!
koma gays kumalaw kwalowa kumangana mwazibwana sopano ndikubwera kusathesa nkhaza kumuzi osakhala kumangana chilichose ayi
Wina anaba ma billion angomusiya
muwona chilango chake chikhala chofanana ndi anthu oipa aja opha albino
Chilango chake chizikhala kulambulira mitengo mnkhalango kwa sabata imodzi, kwinaku akulowa mkalasi ku police cell konko kuphunzira ubwino ndi kufunikira kwa mitengo. kkkk!
Kodi malamulo omangana chisawawa wa mwawatenga kuti?
mwina mwangosowa zochita mumakomo mwanu si nkhani zimenezo each and every day black-out,nde makala olandidwawo mumakataya kuti? tiziwe kuti mumaletsa manyaka inu olima chamba mumange,owotcha makala mmange nanga bwanji okupha somba komanso wa cash gate.
musawamange ai choyamba mufufuze kaye chifukwa chomwe anthuwa akudulira mitengo ndikumaotcha makala mupeza kuti vuto ndi umphawi
Don’t think to arrest them cz escom palibe ikutithandiza, nyani akagwetsa switch makalawo ndiomwe amatithandiza kwambiri
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.