Man fined for growing chamba in game reserve

Marijauana

The Nkhotakota first grade magistrate court has fined a man for encroaching into Nkhotakota Game Reserve and cultivating cannabis Sativa locally known as Chamba.

Marijauana
Indian Hemp

According to Nkhotakota Police Public Relations Officer Sub Inspector Williams Kaponda, the man, Bernado Mikayele, 32, has been convicted and ordered to pay a fine of K40, 000 or in default to serve two years imprisonment with hard labour for illegal entry into the game reserve.

He has also been sentenced to pay a fine K200, 000 or in default to serve 6 years in prison for cultivating Chamba.

If he fails to pay the fines Mikayele will go to jail and serve the sentences concurrently.

The convict hails from Kapelura village, Traditional Authority Kapichira in Kasungu.

Advertisement

141 Comments

 1. Kod boma limalimbana ndi chamba chifukwa chani?azilimbana ndi zinazo kom mbali yokhayi ndiy ai xiku lina tizaukura ndithu ngati oxazitenga bwino coz tinatopa nanu a boma mukumva!!!

 2. Chamba ndi deal heavy fodya sakuyambapo let us try season ya mawa alimi a fodya asalimeso 4dya insted alime Ganja ucan see dora zomwe Mw ingapeze bt government kukhomerera……… work up just legaliz it Mulugu sanalengepo chinthu chopanda ntchito. muli chuma mu Chamba bt we cm like we r short sighted

 3. hahahahaha so funny why but why MALAWI GOVERNMENT TARGET dem idreans ahh guh plant da seed fi de healing nation ? malawi nuh guh stop yeye water

 4. Penapake inesindimamvesesa kusowa ntchito mkumalowa mnkhalango kumakayang’na olima chamba kodi mikango inali kuti imaleka kukuphani,ndiye mutiwuze chochita ndi judge wanuyo kapena tiziba kuti tizipeza ndalama?

 5. Penapake inesindimamvesesa kusowa ntchito mkumalowa mnkhalango kumakayang’na olima chamba kodi mikango inali kuti imaleka kukuphani,ndiye mutiwuze chochita ndi judge wanuyo kapena tiziba kuti tizipeza ndalama?

 6. Chaka Chino Inenso Ndilima Muzandimange,ndipoison Kuti Apha Anthu?Mesatimapangira Mavuto,ndimomwe Timapezera Ndalama Komanso Kuparliament Anakambirana Kuti Chiyambe Kulimidwa Ndemukuwagwira Anthuwo Kuti Atani? Ndipo Pamlando Wanji?

 7. achinyamata mbiri tilibe zocita boma likudziwasi za izi.inde xul tidalephela koma 4m 4 lidafika ndipo tsamba ambiri lilipo ndithu zocitazo ndie palibe umphawi. ndie mukuti titukula bwanji miyoyo yanthu o tizingokhala popanda cocita cazeru? bola chambacho pot akadatha kugulitsa ndikupezapo kenakake. fuck all the pipo who arrest and fine him.go to hello coz mmafuna ife tizingotuwa inu mukungoba ndalama zathuso nbomamu pa……….. pan_!!!!!

 8. A police ambiri school feed bamboo ako amalima chaba .tamusini muthu wamba akufunanso kulipila school ya ana ake azakhale ngati aja ananwelirs ndinjala chifukwa anakumba okha manda pamseu

 9. Asiyeni anthu azilima Chamba.Ulimi wa fodya ukutha.Ngati kuli kumanga inu aPolice kamangeni anaba ma Tractors,Kamangeni Mcheka Chilenje ndi Chiwaya anaba ndalama zamalendi

 10. Chaka chamawa ndilima changa, I didn’t know kuti it’s big money. Enafe kuba ndikupha ayi; tidzilima whatever can give us cash.

 11. Mangani aliese amene wapezeka ndichamba,,,muendeso mmakampumu aliese mukamupeze pa kampu mangani,,,sitikufuna kut anthu apenge kuno amene akufuna kupenga asamuke apite ku USA aadzikasuta mwaufulu kuno tikumangani chabe

 12. Akanapezeka Ndi Ziwalo,kapena Mafupa A Alubino Mukanammanganso Apa Walima Mukummanganso Kkkkk Akabe? Akangokhalanso Muziti Wa Ulesi Hahahaha Nde Mpatseni Chochita Bola Azidya Pakhomo Pake Ndi Ana

 13. Osamumanga Munthu Chifukwa Choti Walima Chamba, Zikhoza Kutheka Inu Mudaphunzira, Makolo Anu Amalimaso Chamba Nkugulitsa Kenako Kukakulipirirani School Fees. Mukumva Bwa?

 14. Osamumanga Munthu Chifukwa Choti Walima Chamba, Zikhoza Kutheka Inu Mudaphunzira, Makolo Anu Amalimaso Chamba Nkugulitsa Kenako Kukakulipirirani School Fees. Mukumva Bwa?

 15. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 16. Tsopano mukufuna tidzitani,tikulima chamba kukana kuba olo kupha ma arbinho,aaaaa mulibe pabwino munthu azilimbikire mukummanganso apa ndiye payelepayele chabadwa chafa sichiopa kuola olo kununkha dziko lopusa ngati ili sindinalionepo

 17. Tsopano mukufuna tidzitani,tikulima chamba kukana kuba olo kupha ma arbinho,aaaaa mulibe pabwino munthu azilimbikire mukummanganso apa ndiye payelepayele chabadwa chafa sichiopa kuola olo kununkha dziko lopusa ngati ili sindinalionepo

 18. Koma nde mulitu ndi sanje apolice osakama a k577 billion ya cash gate muzamange ine muzaone ndizakuyankhulanu pa public mu court aliyese akuva

 19. Koma nde mulitu ndi sanje apolice osakama a k577 billion ya cash gate muzamange ine muzaone ndizakuyankhulanu pa public mu court aliyese akuva

Comments are closed.