Malawi Super league promoted military side, Chilumba Barracks has been fined MK 5.4 Million by the Super League of Malawi (Sulom) due to their ‘swift’ withdrawal from the top tier.
Earlier last week, Malawi24 reported that the northern region based team had been written Sulom confirming their withdrawal due to financial constraints that have hit the club.
MDF also made revelations thatit will only have three army teams in the top flight from next season on.According to one of the Chilumba officials, Brigadier General Alick Mhone ,MDF willnot manage to support a fifth team in the league due to meager resources.
But Sulom says the withdrawal has been wrongly timed saying that key preps for the team just like the others in the top tier near completion and that the move would cost the body a lot of time and resources.
Sulom has since fined the side to pay MK5.4 Million up until Friday, a day before the league starts.
It is not yet known if the team will meet the fine as financial constraints remain the reason they said they would not take part in the league.
Zachamba
Abale dziko lapansi ndilovuta komanso ndilokondela.
Abale dziko lapansi ndilovuta komanso ndilokondela.
The whole sulom executive must go ,the malawi football is dwindling bcoz of u,u r failing to solve small issues eg chande,s saga,but u r gud at punishing small teams,what kind of sulomu is this?
The whole sulom executive must go ,the malawi football is dwindling bcoz of u,u r failing to solve small issues eg chande,s saga,but u r gud at punishing small teams,what kind of sulomu is this?
Ndalama zonsezo? Eeeeeh!
Ndalama zonsezo? Eeeeeh!
Aaaaaaa koma zinazi ndalama azitenga kuti shame on sulom
Tisonkhe limodzilimodzi tiwathandize anzathuwa
MWAGWANAYO A SULOM
MWAGWANAYO A SULOM
Major 1 anakakuthandizan
Major 1 anakakuthandizan
If they r withdrawing bcoz of financial prblms,where do u think they’ll get that amount to pay u thieves?u r dragging our game of ftball backward a team of bandits at helm of super league in co
If they r withdrawing bcoz of financial prblms,where do u think they’ll get that amount to pay u thieves?u r dragging our game of ftball backward a team of bandits at helm of super league in collabo with fam thieves.
Kkkkk Awatu Sapereka Ndalamayi,mukaumilira Asintha Chanel Aiwala Zampira Kenaka Mudzangodabwa TATA yafika muthizimulidwa inu!kkk
Kkkkk Awatu Sapereka Ndalamayi,mukaumilira Asintha Chanel Aiwala Zampira Kenaka Mudzangodabwa TATA yafika muthizimulidwa inu!kkk
Hahahaha sulom yiyenela kuganizanso mozama chifukwa ndalama akutchulayi anangolota kuntolo atagona ,kkkkkkkkkk
Kkkkk koma sulom simukuwaganizira anzanuwo
. . . .” Adzamulanda ndizochepa zomwe zimene ayesa alinazo”
This is typically biblical saying by Jesus Christ . . . .” adzamukanda ndizimene ayesa alinazo. . . . “.
Sulom Malawi Army cannot pay that money.Even post office they don’t pay postage stamps They do security jobs in other words their job is risky to save you and me.Think otherwise…
Klkkk sulomu ndinu achamba eti mwanyera
I dont blame SULOM, i blame the management in MDF teams. They knew all along that there will be no funds if the team qualifies yet they just watched as the team went ahead and qualify. Perhaps they should be taught a lesson so that others can learn from it.
inutu bwino akulipirani jombo ndithu dikiran
inutu bwino akulipirani jombo ndithu dikiran
Kod k73M ija ankati wapereka Major 1 Bushri znali zaboza eti
Lets wait and see
Timuyi ndi ana okha okha awona kt kumenya mu super League palibe chomwe aphule so inu mukuzitcha atsogoleri mukuti apereke ndalama zachani? Plz kumvesanso ndikwabwino, ine ndipita ndikatenge chiletso pachigamulo chimenechi
kkkkkkkkkkkk football in Malawi
A sulom mukuwonjeza zomwezi mpaka pamenepo mwaganiza kuti mugawana zingati zingati paja kwa vuta njala
zopusa 2 sulom
kkkkkk akapereka ndalamayo muzandifunse dzina langa lakale……mukananena kt apeleke Zipolopolo kapena Teargas mwina zikanamveka kma 5.4 mita hahahahhahah Malawi sazatheka
Iwo ndalama alibe,ndiye alipiranso bwanji, apaso ndiye nzeru zasowatu ku SULOM, munthu ali maliseche chifukwa zovala alibe, ndiye amubwerekaso nzake bwanji zovala kuti avale.
Ofunika a Chirumbao akangophulisa kuma offece a SUROMko coz awaonjeza kwambiri
Too much
MDF mkupereka yamahala ku sulom hee kaya
Azanu ndarma at alibe inu mukatchaja ndarma zambili ngati zimenezo mungowamangitsa bas mutchuke ndinu
Ku Sulom kulibe anthu anzeru.Ngati Nkhani ya Dedza ikuwakanika,do you think angakwanitse ya Chilumbayo?
This is a joke of a century and i think this s body is slowly loosing direction
Kuzolowera kuba zitsiru
Paja nkhani ya mpira sipita ku court.Mutani akapanda kulipira?
Anthu alibe ndalama,then mukuwapatsaso fine,ndalama azitenga kuti? Kkkkk Sulomu mbwelera zeni-zeni.
Sanachite Bwino Chifukwa Alephera Kumenya Mpira Mu Super Chifukwa Chosowa Ndalama Ndiye Ayimika Manja Iun Kumati Alipire 5.4 N’goooo!
Awa nde mukangoamangisatu chifukwa nde ndalama zanu simupasidwa…Ng’oooooooooooooooooooooooo..mundifuse..basi angotenga 5.4 million akupaseni chonsecho tunena pano kwaoko kuli ma floods.hahahahahahaha mwauponda a SULOM….
Palibe nzeru ngati team ilibe ndalama ndiye 5.4 ayitenga kuti?
Ku SULOMko antho olingalira kulibe…ana apanga withdraw kut samenya mu league chifukwa cha ndalama nde mukubwera nkumati alipile 5.4 million kwacha…mukuona ngat anakakhala kut ali ndi yokwana imeneyo akanazituluka??? Hahahahahah mwamba ma fundraising eti..kkkk
Sulom is not mistaking to give the MDF boyz fine coz they’ve taken so long to tell the SULOM about their Army problems. When did they sat down n think about their Gun problem? Lipilani basi coz mwaononga ndalama za sulom kukulembani maina anu osalongosokawo pa ma Jersey ndi zina zotero
Kkkkkkkkkk alipile basi tit for tat
Mbuzi
This is not milking the thin but the dead.
Kiki
Kkkkk anthuwotu akanika kumenya super league chifukwa cha ndalama sanakuuzeni kapena? ndiye inuso mukuti akupatseni ndalama.
Kkkkk anthuwotu akanika kumenya super league chifukwa cha ndalama sanakuuzeni kapena? ndiye inuso mukuti akupatseni ndalama.
Zili bwino pamenepa,Apereke basi amaphweketsa kwamniri.
Kuzolowela kubela anthu mulandu wanji wopeleka kwa muzako wodwala kale mbutuma za sulamu
ngati team yapanga withdrawn chifukwa choti iribe ndalama ndiye 4.2 mita akaitenga kuti?
kumeneko ndie timati kukama ng’ombe yowonda kale
Anzawo akulimbirana mwai wosewera mu Super League Iwo nde nkumaseweretsanso?
Mmmmmmm hm kandalama komwe anapisidwa ndi bushili kaja mufuna mudye nawoso.asiyeni alibe ndrama basi.
Vuto Si Chilumba Barracks Kma Ma Bwana Awo Nde Sulom Nayo…..
Koma nde uchikape
Akanakhala kut ndalama imenei alinao sibwez atasewera .ndie mukutenga mavuto kuikaso pamavuto azake ,mukatero mwangwira ntchito mchifukwa chake timu ya malawi imarephera pot nonse mzeru mukumaika pandalama .
Zosekesa kwambiri munthu wanenakuti sindidya lero poti ufa palibe, wokumvayo angatinso ndipase ufa poti wati sungadye
Koma apeleka? Coz anthuwa amadandaula za ndalama nde mukufuna ndalama zonsez why? Tose nda a Malawi tyen tziganizilana.
Big up @ SULOM simunalakwitse coz anayenera kunena kale lomwe kut saseweranawo TNM-SL
Boladi tayikwapula noma kaya zilipisanani.
alibe alibebasi
Where are they to get money for paying that fine?
Kkkkkk koma sulomo aaaaa ndiye ay2 muthu wakuuzan kut xakwanixa cifukwa candalama inu mukumuuzanxo ndalamaxo kkkkkkkkk
Kkkkkk munthu walephera kudya cz ufa alibe yet muti akupaseni 5.4 mita kkkkk anakakhala nayo anakagona tiziona.akangopereka ndiye kuti anangoopa zigoli
Zingayambe kuyiwalika bullets 2 noma 0! Abapatsana. Ma fine wo ife bola wanderers tikumayisosola heve
Mwaputawo ndi asilikali
Nonsese
Akufuna abele ndalama athandizidwa ndi bushili zija zikuwawawa mutima sulom kwakula ndikuba basi
Alephera kupikisana mu league mo kamba ka mabvuto a zachuma,ndiye kaya mukuti a” SULOM” akufuna K5.4 as fine. Zoswesa mutu kuti uzimvese
Mmmm its too much!
KUPUSA, BEST WAY WAS TO SIMPLY SUPPLY INADEQUATE REQUIREMENTS FOR CLUB LICENSING TO MEDIOCRE MANAGERS IOF FAM/ AND THEIR FIXTURES DEPARTMENT CALLED SOLOM (KAYA SULAM POTI ZENIZENI SIZIWIKA).
Nde azipeza kuti ndalama zolipilazo NATO akanika kulowa mu league
Anthu alibe ndalama ndie mukutinso apeleke 5.4 mita???? Palibe nzerutu apa a FAM mwaganiza bwanji? Ndiye akapanda kupereka muwatani? Haaaah muwamanga? A Walter Nyamilandu ndi gulu lanu muganizepo mofatsa apa, kaya ngati zili mu malamulo a FAM i tink lamulo limenero muliunikenso bwino cz ndalama yabvuta masiku ano,
MDF will not pay this fine, lets see what your SULOM can do
Ndiye mudziti ma play off achiyani ena akukanika kkkkkkk ndiye akhalamo ma team 14 mmalo mwa 15
Sulom nde yayala gen yotenthatu up to 5nyono? kkkkkkk
Thats good they have to pay even more than this, When they started taking part in Playing they new how much they will to spend if they finish at top, SULOM itself have waist alot of money for making their jerseys, they have already waist SULOM’s time
Nosense
Idiot, son of moron
why always on gover coffers ~were already crying that things are not ok in this country.we have too many of army teams.let others be nursely of teams like Moyale~Red lions ~kb
Akupatsan zipolopolo instead of money munya asulom
Who Is SuposedTo Punish Chirumba Sulom Or NRFL? I stil believe chirumba is stil in the hands of NRFL.if they registered with sulom then sulom is right but if they didnt register as i am hearing then sulom has goofed!Or
When they qualified to the super league the sulom started making all neccesary things for the team ie jearsey,scuffs and all de requirments that is needed for asuper league team
The question is…
Is Chirumba affiliated to sulom..?
I thought SULOM is the eye and head of NRFL,CRFL and SRFL as well and a mother body of all is FAM,any body else can help me but this is what I think
Guys All U Have Said Here May Be Tru.And The Un4tunate Thing Is They Have Withdrawn @ The 11th Hr Which Is Again Very Unfair.
Sulom is not telling us if Chilumba made a commitment to participate. Because being champions doesn’t mean u are bound to participate no matter what.
Munya sakupasani,,
kodi mesa akut Bushiri wapeleka 75mita kwa ma guyz amenewa?
Angowasiira supper league yaoyo bwa? Kkkkkk
nde kumalawi kumeneko. kukolora mosalima
Komatu anthuwa akudandaula za ndalama mpamene inu mukuwauzanso zoti akupatseni ndalama…kubera mphawi nde nkumeneko. Kkkkkkkk
Its MDF not chilumba as a club so MDF as a sponsor they are the one to pay the fine
fundraising sulom…5mllion..eee…?
ndalama yachuluka iyi,atenga kt?
Zokuba bas
Better
So where the hell do SULOM think Chilumba will get all that money from if they ddnt have a penny to participAte in the league? Akazakupasani muzandimbile foni koz iwowa zampira zachokamo
But these guys r saying they are too broke to play in the Elite league and then you fine them 5mita? ayitenga kuti
Thats too much money!