Chiefs back Mutharika, fault calls for his resignation

Advertisement
Chiefs

Chiefs in Malawi have expressed disapproval on calls for President Peter Mutharika to resign following numerous challenges that have rocked the country.

The development follows a Public Affairs Committee (PAC) meeting held in the Blantyre aimed at putting down views from different stakeholders to address the economic and hunger crisis.

Chiefs
With the calls. (File)

During the meeting, members from opposition parties called for resignation of the Malawi leader arguing that he is responsible for the challenges that the country is facing.

Speaking during a press briefing, some chiefs have pleaded for patience arguing that the challenges have been there since the country was granted self-governance in 1964.

“This is not for the first time that people are eating madeya, during Kamuzu’s reign people ate madeya as well as during the era of Bakili Muluzi. The meeting that PAC had was aimed at bringing solutions not calling for someone to resign” said Paramount Chief Lundu from Chikwawa.

On his part, Paramount Chief Kyungu from Karonga said calls to have Mutharika impeached will worsen the situation in the country.

“As chiefs we are not in support of the idea to force the President to resign, Malawi has challenges yes, but they are not there because we have Mutharika, for example the issue of floods that have led to hunger crisis, I don’t think he is responsible for the floods as others have said that he is responsible for all the challenges” said Kyungu.

Kyungu further urged journalists to be “nation builders” arguing that the country lies on journalists to feed the country with information.

Advertisement

282 Comments

 1. READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS…

 2. KOMA INUZOONA MIKANJO PHOLI2 KUONONGA DZIKO LANDILANI MPHOTO YANU PADZIKO PANO KOMA KUMWAMBA MUDZAKHALA NKHUNI ZOOTCHERA ANTHU OCHIMWA FERTILIZER MUBE CHIMANGA MUBE MALATA SUBSIDY MUBE LDF MUBE MUBENSO MALO ANZANU

 3. But who these ppo called chiefs! What development they do in the country? Most v these chiefs they don’t even went 2 primary xool! Full v idiotic they r only knows witchcraft n stupid chiefs they got something from Peter n opening up their untidy mouth forgetting about their ppo in their villages how they starving! Be careful chiefs cos we r after u n we’ll show u

 4. Mafumu Anzeru Kwambiri, Kusintha President Sizingatithandize Chifukwa Palibe Angasinthe Zinthu Kupita Kuubwino Enawo Akungopanga Viwawa Chifukwa Cha Dyera Lolamulira!

 5. Mafumu Anzeru Kwambiri, Kusintha President Sizingatithandize Chifukwa Palibe Angasinthe Zinthu Kupita Kuubwino Enawo Akungopanga Viwawa Chifukwa Cha Dyera Lolamulira!

 6. MUNTHU OTI MUNAMUVOTELA ,munadumpha ndi kuvina mmisewu kusangalala kuti wawina! Kodi lero waipa? DYERA NDI LOMWE LAVUTA MDZIKO MWATHU MUNO, vuto ndi satana coz enawo angofuna mipando yonona,NGATI SIMUKUMUFUNA DIKILANA 2019 muzamuchose ndi vote, enawa achina chakwera ngat ali abwino;BWANJI OSAYAMBA KUTHANDIZA ANTHU PANO MMENE APANGILA BUSHIRI?

 7. MUNTHU OTI MUNAMUVOTELA ,munadumpha ndi kuvina mmisewu kusangalala kuti wawina! Kodi lero waipa? DYERA NDI LOMWE LAVUTA MDZIKO MWATHU MUNO, vuto ndi satana coz enawo angofuna mipando yonona,NGATI SIMUKUMUFUNA DIKILANA 2019 muzamuchose ndi vote, enawa achina chakwera ngat ali abwino;BWANJI OSAYAMBA KUTHANDIZA ANTHU PANO MMENE APANGILA BUSHIRI?

 8. mafumu ndiopenga awa alingat mitengo amangosatila komwe mphepo ikupita, kuti achoke pitala alowe wina aziyamikilaso thts simply shows kut they r not strong enough to stand on their own.. kuvela athu awa ukungotayapo tym apa… #peterMustFall

 9. Ngat mamulumuzana, mikhatheya, minkhula ng’ona, mikoko yogona, anamandwa, anamanyonyolo, magiling’ande, atero, ndine yani kutsutsa? Mutoyesa ndi ulidala wa mkalasi eti? Uyutu mpaka zino lasalamo lija ligwerukemo akulamulabe

 10. Ngat mamulumuzana, mikhatheya, minkhula ng’ona, mikoko yogona, anamandwa, anamanyonyolo, magiling’ande, atero, ndine yani kutsutsa? Mutoyesa ndi ulidala wa mkalasi eti? Uyutu mpaka zino lasalamo lija ligwerukemo akulamulabe

 11. Ngat mamulumuzana, mikhatheya, minkhula ng’ona, mikoko yogona, anamandwa, anamanyonyolo, magiling’ande, atero, ndine yani kutsutsa? Mutoyesa ndi ulidala wa mkalasi eti? Uyutu mpaka zino lasalamo lija ligwerukemo akulamulabe

 12. mafumu ndi magwero achitukuko!,kumeneko ndiko kutumikira anthu mwamzeru!,apm sangatule mukunama!,mukuwopa chani tiyeni tikumane 2019!,uladi simumamuziwa eti!,hule wachabe chabe change golo!,angalanulire?,achakwera phuma!,dikirani 2019,komanso sikuti mungazawuwonenso mpira ndakayika!,ana mwachepa mususa mpaka yesu abwera!

 13. mafumu ndi magwero achitukuko!,kumeneko ndiko kutumikira anthu mwamzeru!,apm sangatule mukunama!,mukuwopa chani tiyeni tikumane 2019!,uladi simumamuziwa eti!,hule wachabe chabe change golo!,angalanulire?,achakwera phuma!,dikirani 2019,komanso sikuti mungazawuwonenso mpira ndakayika!,ana mwachepa mususa mpaka yesu abwera!

 14. mafumu ndi magwero achitukuko!,kumeneko ndiko kutumikira anthu mwamzeru!,apm sangatule mukunama!,mukuwopa chani tiyeni tikumane 2019!,uladi simumamuziwa eti!,hule wachabe chabe change golo!,angalanulire?,achakwera phuma!,dikirani 2019,komanso sikuti mungazawuwonenso mpira ndakayika!,ana mwachepa mususa mpaka yesu abwera!

 15. Mukamakhala Musamanamizane Kuti Peter Mutharika Angatule Pansi Udindo Sizingatheke Zimenezo. Ameneyi Atilamulila Mpaka 2024 Iwe Amene Ukuona Ngati Peter Palibe Chomwe Akupanga Usamuke Mu Dziko Muno Ukakhale Ziko Lomwe Kulibe Mabvuto.

 16. Mukamakhala Musamanamizane Kuti Peter Mutharika Angatule Pansi Udindo Sizingatheke Zimenezo. Ameneyi Atilamulila Mpaka 2024 Iwe Amene Ukuona Ngati Peter Palibe Chomwe Akupanga Usamuke Mu Dziko Muno Ukakhale Ziko Lomwe Kulibe Mabvuto.

 17. Mukamakhala Musamanamizane Kuti Peter Mutharika Angatule Pansi Udindo Sizingatheke Zimenezo. Ameneyi Atilamulila Mpaka 2024 Iwe Amene Ukuona Ngati Peter Palibe Chomwe Akupanga Usamuke Mu Dziko Muno Ukakhale Ziko Lomwe Kulibe Mabvuto.

 18. Awa ndi choncho palibe tsiku ananena kuti koma apo Che pitala mwalakwitsa. Alandira tindalama basi ativutepo apa. Komanso mafumu athetse coz milandu ya ufiti ndi kulandana minda inachepa

 19. Awa ndi choncho palibe tsiku ananena kuti koma apo Che pitala mwalakwitsa. Alandira tindalama basi ativutepo apa. Komanso mafumu athetse coz milandu ya ufiti ndi kulandana minda inachepa

 20. Awa ndi choncho palibe tsiku ananena kuti koma apo Che pitala mwalakwitsa. Alandira tindalama basi ativutepo apa. Komanso mafumu athetse coz milandu ya ufiti ndi kulandana minda inachepa

 21. Mwadesedwa chani mafumu kapena tumakoponi timene anakupasani tumakukwanani muziganizaso zaanthu anu akufa ndi njala nde fweeee! Zachati ufiti basi mafumu no zeru muli after kudya nayo osati the development of the country think wise mmene zinthu zadulira

 22. Mwadesedwa chani mafumu kapena tumakoponi timene anakupasani tumakukwanani muziganizaso zaanthu anu akufa ndi njala nde fweeee! Zachati ufiti basi mafumu no zeru muli after kudya nayo osati the development of the country think wise mmene zinthu zadulira

 23. Mwadesedwa chani mafumu kapena tumakoponi timene anakupasani tumakukwanani muziganizaso zaanthu anu akufa ndi njala nde fweeee! Zachati ufiti basi mafumu no zeru muli after kudya nayo osati the development of the country think wise mmene zinthu zadulira

 24. Mwadesedwa chani mafumu kapena tumakoponi timene anakupasani tumakukwanani muziganizaso zaanthu anu akufa ndi njala nde fweeee! Zachati ufiti basi mafumu no zeru muli after kudya nayo osati the development of the country think wise mmene zinthu zadulira

 25. I salute to our chiefs for such realistic, good-minded move; lets consider things from all perspectives b4 misbehaving.

 26. I salute to our chiefs for such realistic, good-minded move; lets consider things from all perspectives b4 misbehaving.

 27. I salute to our chiefs for such realistic, good-minded move; lets consider things from all perspectives b4 misbehaving.

 28. I salute to our chiefs for such realistic, good-minded move; lets consider things from all perspectives b4 misbehaving.

 29. Mafumunso ndi anthu akangowapatsa k20,000 akumaiwala kuti ku midziko kuli anthu chondidabwitsa ndi chakuti mafumu athu amavomereza zopusa singati mmeme amayenera kupangira

 30. Mafumunso ndi anthu akangowapatsa k20,000 akumaiwala kuti ku midziko kuli anthu chondidabwitsa ndi chakuti mafumu athu amavomereza zopusa singati mmeme amayenera kupangira

 31. Mafumunso ndi anthu akangowapatsa k20,000 akumaiwala kuti ku midziko kuli anthu chondidabwitsa ndi chakuti mafumu athu amavomereza zopusa singati mmeme amayenera kupangira

 32. Mafumunso ndi anthu akangowapatsa k20,000 akumaiwala kuti ku midziko kuli anthu chondidabwitsa ndi chakuti mafumu athu amavomereza zopusa singati mmeme amayenera kupangira

 33. koma anthu inu ndale mukuzitengela pa n`gong`o yeti kkkkkkk zitayeni zimenezi palibe chomwe mungapindulezo anta

 34. Opanda nzeru ndi inu amene mukunyoza mafumu popanda chifukwa.Mumanyoza president Mutharika komanso mafumu anu amene amakuyang’anilani tsiku ndi tsiku. Ana otembeleledwa inu,ana osamvela makolo inu. Anthu omwe akukupusisaniwo azakusiyani nokha mutagwa m’mavuto,iwo amabisala ndikukutumani kuti muyambe kulimbana ndi boma. Mwaiwala kuti Bingu munkafuna kumuchosa atangolowa kumene m’boma koma mudamulephela.Lero mukufunanso kuti President osankhidwa ndi anthu achoke nthawi yake isanathe ,mwauponda ndithu. Mudazolowela kulowa ufumu ndi chakumbuyo paja,kuyembekeza wina amwalire inu nkubwela nkuzagwilizila mpandowo.Koma nthawi ino sizitheka olo mpang’ono pomwe. Chisankho chitati chichitike lero apambananso. Ambirinu simudayendepo ndipo simukudziwa kuti mavuto akusowa kwa chakudya akuchokela kuti? Mungoona ngati Malawi yekha ndi yemwe ali pamavuto.Amalemu a Bingu adatisiyila chaimanga koma anthu ena adyela adachigulitsa ndani amene sakudziwa.

 35. lnu mafumu , ngati mwapatsidwa timaswiti kukutsekeni kukamwa, izo ndi zanu ndi zimbalangondo zanuzo. Koma ife a Malawi tonse tikuti azipita, poti akukunyengererani ndi maswiti mutsatireni ku Thyolo konko muzikabulumunya maswitiwo,

 36. lnu mafumu , ngati mwapatsidwa timaswiti kukutsekeni kukamwa, izo ndi zanu ndi zimbalangondo zanuzo. Koma ife a Malawi tonse tikuti azipita, poti akukunyengererani ndi maswiti mutsatireni ku Thyolo konko muzikabulumunya maswitiwo,

 37. indedi malawi ngati akufuna kuti tivotenso no blem we can do bolangati mukudziwa kuti mutsonkhelana ndalama dzoyendesera chisankho otsati depend for government because we have got already financial ploblem,

 38. indedi malawi ngati akufuna kuti tivotenso no blem we can do bolangati mukudziwa kuti mutsonkhelana ndalama dzoyendesera chisankho otsati depend for government because we have got already financial ploblem,

 39. Ufumu olilira ndichocho opanda chisoni ndi amunthu awo agalu achabechabe aiwala kuti atukwanidwa ndi anthu awo kamba ka makoponi lero akumuikira kumbuyo satana

 40. Ufumu olilira ndichocho opanda chisoni ndi amunthu awo agalu achabechabe aiwala kuti atukwanidwa ndi anthu awo kamba ka makoponi lero akumuikira kumbuyo satana

 41. Mafumu oganiza ngati makanda kuyankhula ngati ma baby,ogona ndi mkodzo.when Bwampini is falling these marons must all fall,the have nothing to offer to the rural masses

 42. Mafumu oganiza ngati makanda kuyankhula ngati ma baby,ogona ndi mkodzo.when Bwampini is falling these marons must all fall,the have nothing to offer to the rural masses

 43. Mafumu oganiza ngati makanda kuyankhula ngati ma baby,ogona ndi mkodzo.when Bwampini is falling these marons must all fall,the have nothing to offer to the rural masses

 44. Mafumu oganiza ngati makanda kuyankhula ngati ma baby,ogona ndi mkodzo.when Bwampini is falling these marons must all fall,the have nothing to offer to the rural masses

 45. U support stupid things muthalika tod us that chimanga chilipo bt why pepo r suffering while the maize is there.during kamuzu i do remember we where receiving yellow maize osati zanuzi

 46. U support stupid things muthalika tod us that chimanga chilipo bt why pepo r suffering while the maize is there.during kamuzu i do remember we where receiving yellow maize osati zanuzi

 47. U support stupid things muthalika tod us that chimanga chilipo bt why pepo r suffering while the maize is there.during kamuzu i do remember we where receiving yellow maize osati zanuzi

 48. U support stupid things muthalika tod us that chimanga chilipo bt why pepo r suffering while the maize is there.during kamuzu i do remember we where receiving yellow maize osati zanuzi

 49. nkona mukamayakhula speach pa sokhamo maulemu mayambila olemekezeka ma youth, ma mp. kutsilizila president wanuyo mbuz za athu ..go bak to sxul

 50. nkona mukamayakhula speach pa sokhamo maulemu mayambila olemekezeka ma youth, ma mp. kutsilizila president wanuyo mbuz za athu ..go bak to sxul

 51. nkona mukamayakhula speach pa sokhamo maulemu mayambila olemekezeka ma youth, ma mp. kutsilizila president wanuyo mbuz za athu ..go bak to sxul

 52. nkona mukamayakhula speach pa sokhamo maulemu mayambila olemekezeka ma youth, ma mp. kutsilizila president wanuyo mbuz za athu ..go bak to sxul

 53. Nonsenu mukupanga coment zopusa nyini ya amayi anu,mwadyesedwa zambiri et simukuona komwe kukulowera malawi kodi xyuuu

 54. Nonsenu mukupanga coment zopusa nyini ya amayi anu,mwadyesedwa zambiri et simukuona komwe kukulowera malawi kodi xyuuu

  1. Zooona man sakudziwa mwina mwake mafumu adyera amenewa. uyu basi zakanika ayenera kumvomereza ndi kutula pansi udindo awapatse mphata anthu ena madzi asanafike mukhosi.

  2. Zooona man sakudziwa mwina mwake mafumu adyera amenewa. uyu basi zakanika ayenera kumvomereza ndi kutula pansi udindo awapatse mphata anthu ena madzi asanafike mukhosi.

  3. Zooona man sakudziwa mwina mwake mafumu adyera amenewa. uyu basi zakanika ayenera kumvomereza ndi kutula pansi udindo awapatse mphata anthu ena madzi asanafike mukhosi.

  4. Zooona man sakudziwa mwina mwake mafumu adyera amenewa. uyu basi zakanika ayenera kumvomereza ndi kutula pansi udindo awapatse mphata anthu ena madzi asanafike mukhosi.

 55. Chiefs in this country will always be STUPID.Akangodya chibanzi basi always behind the incumbent president.Only chiefs who went to school can stand up to the bullshit koma nkhalamba zosagerazi zimangovomereza any government of the day just to secure being elevated.Mbuzi zachabechabe kuzolowera kudyetsedwa zintuwitsa mmxxxxrm! :/ Afiti

 56. Wumene ndiye timati mafumu azeru,wokonda ziko lawo,wokonda ndiku wafunira zabwino anthu awo,wosatira zamumbuyo ndikusanamizidwa, woziwa zomwe zimapangisa nkhondo mumayiko ena, wozindikira kuti tanamizi dwa tatopa ndi amenewa adyera,mahule andale, wofuna zawo zokha,akuba ndi wogwirisa nchito azawo koma zikadusa ayiwara monga ubwezi wa muntu na nkhwangwa, so far bravo bravo our bosses w r with u,time has come let us standup,w also suport the introduction of A CHIEF FORUM, let it b at national level,regional and district so far GVH to b included moti pakati pano kuliso mafumu ena wophuziraso than these greedy/selfish politicians

 57. Wumene ndiye timati mafumu azeru,wokonda ziko lawo,wokonda ndiku wafunira zabwino anthu awo,wosatira zamumbuyo ndikusanamizidwa, woziwa zomwe zimapangisa nkhondo mumayiko ena, wozindikira kuti tanamizi dwa tatopa ndi amenewa adyera,mahule andale, wofuna zawo zokha,akuba ndi wogwirisa nchito azawo koma zikadusa ayiwara monga ubwezi wa muntu na nkhwangwa, so far bravo bravo our bosses w r with u,time has come let us standup,w also suport the introduction of A CHIEF FORUM, let it b at national level,regional and district so far GVH to b included moti pakati pano kuliso mafumu ena wophuziraso than these greedy/selfish politicians

 58. Ana a mahule,Mutharika palibe kutula pansi udindo.Anthu anamuika pampando ndi voti ndipo ndi voti yomweyo ndimene anganchotselenso,mwamva eti!Mavuzi a manu,palibe kulowa uprezident podutsa njira zachidule.Umbuli unachuluka kuMalawi,dziko linatengedwa mmanja mwa Jezebel Joyisi litavunda ili choncho silingakonzeke lero ndi lero.Mungozivuta DPP through 2019 to 2024 wooo!

 59. The most excited thing is that anthu amene mukuika ma comments onyoza APM and his regime simudavote enanu mudali musanakwane zaka 18 nde basi mudzitikwana apa,ask ur fathers and mothers akuuzani kuti iwo APM alibe naye vuto,vuto ndi loti tilli masiku otsiliza nde ziyenera kuchitadi zomwe zikuchitikaz komanso adandaula kaamba kobeleka ana amwano osalemekeza achakulungwa.if APM is stupid who is good?may be lazalo chakwela for dumping work of God to join this called diabolical politics or J kabwira yemwe pano akuthawathawa dziko lake lomwe,kapena mwina mai joyce Banda ataba ndalama zathu nkuthawa dziko lake lomwe kenako kumusankha Uladi mussa kuti alande boma mwaupandu kapena mwina abwino ndi atsogoleri a PAC omwe kwanthawi yaitali akhala ali patsogolo kuthandiza boma ndi ma plan abwino koma lero haa akuthandiza otsutsa kufuna kuti APM atule udindo,lets all pray for this nation so that Mulungu atithandize rather than kumati APM atule mpasi udindo,enaife tidavutika 2014 kukhal pa nzere 4hrs kuti tivote nde think 2ce

 60. mafumu opanda nzeru akakhuta iwo akuona ngati tonse takhutanawo pamavuto onse tikukumanawowa akusankha kuikila kumbuyo boma? amaimila boma kapena anthu wamba zamanyazi.

 61. Akamachoka m’bale wanuyu inunsu mutule pasi ufumu mwalephera anthu akufa ndinjala inu kumalakhula mwachipongwe ndinu mtundu wanji wamafumu

 62. Eee awa ndye samasewera ndinkhuni aise kuopa kusiya ufa..zitaye udzivia ku America bas cz kunena zoona waonjeza kwabasi chilowereni koma palibe cholozeka wapanga aaah ukuzunzitsa miyoyo yambiri kwabasi

 63. iwe tamvera kaye kuno, uyu palibe kuchoka ngati munalephera kuchotsa m’bale wake uja ali ndi a mphungu 6. kuona kuti ndi za nzeru kuti, lero mangamuchotse uyu pa mpando wa uprezidenti? chimene ungadziwe ndi ichi, ndi excuctive yokha ya Dpp imene ingathe kumuchotsa ndi imene ili ndi mphamva zoposa zakozo. ukakhala usalozedwe, kuti iyeyo angatule pansi udindo wake chifukwa choti wina wake akuti ndi wamkulu ku PAC ai ndi bodza limenelo ufatse uwone.

  1. iwe sibongile fatsa, ine ndili pano pa joburg koma iwe kumene uliko uzitsata chilungamo. ukafutse bwino-bwino agogo ako akakuwuza kuti uyu ndi munthu wina mpando umene aliwo ndi okhawo ali mamembala a DPP angathe kumuchotsa osati akuti kuli wa PAC akagwere uko futsek. udzaziona, bwenzi lako akazakhalapo pampando umenewo iwe ukutchedwa first lady hule iwe.

  2. Do u know the meaning of democracy? Osamangothamangira kunyoza anzanu,Kaya pitala ndi agogo ako ndikuti zinthu zamkanika,munthu ali ndi mamphunziro abwino but without wisdom on how to rule the nation,achoke he is selfish

  3. iwe watson, democracy inayamba ndili komweko ungandiuze chiyaninso iwe. palibe chimene ukudziwa, basi zolakwika wa ziona m’mene akulamula Peter yu basi tayesa kuyimirira nawenso mpando umenewu. udzamve m’mene anthu, azakutukwanire chifukwa ukuoneka ngati wanzeru koma ulibe ndi nzeru zomwe.

  4. Man Amene Akuti Mutharika Walephera Apange Resign Iyeyo.President Samagwetsa Mvula Ndipo Mabvuto A Chakudya Ndi Kamba Ka Mvula Yosalekeza Yomwe Idagwa Mu 2015.President Uyu Wayesesa,Takumbukani Anthu Okhuzidwa Ndikusefukira Kwa Madzi Ku Lower States.Ngakhale Ine Ndaganiza Kuti Dzina Langa Likhale Nedson Peter Wa Machokola Mutharika

  5. Man Amene Akuti Mutharika Walephera Apange Resign Iyeyo.President Samagwetsa Mvula Ndipo Mabvuto A Chakudya Ndi Kamba Ka Mvula Yosalekeza Yomwe Idagwa Mu 2015.President Uyu Wayesesa,Takumbukani Anthu Okhuzidwa Ndikusefukira Kwa Madzi Ku Lower States.Ngakhale Ine Ndaganiza Kuti Dzina Langa Likhale Nedson Peter Wa Machokola Mutharika

  6. Man Amene Akuti Mutharika Walephera Apange Resign Iyeyo.President Samagwetsa Mvula Ndipo Mabvuto A Chakudya Ndi Kamba Ka Mvula Yosalekeza Yomwe Idagwa Mu 2015.President Uyu Wayesesa,Takumbukani Anthu Okhuzidwa Ndikusefukira Kwa Madzi Ku Lower States.Ngakhale Ine Ndaganiza Kuti Dzina Langa Likhale Nedson Peter Wa Machokola Mutharika

  7. Man Amene Akuti Mutharika Walephera Apange Resign Iyeyo.President Samagwetsa Mvula Ndipo Mabvuto A Chakudya Ndi Kamba Ka Mvula Yosalekeza Yomwe Idagwa Mu 2015.President Uyu Wayesesa,Takumbukani Anthu Okhuzidwa Ndikusefukira Kwa Madzi Ku Lower States.Ngakhale Ine Ndaganiza Kuti Dzina Langa Likhale Nedson Peter Wa Machokola Mutharika

  8. panyopako xenophobia ya mbuyako, ine singandipeze ngakhale m’bale wako Peter amatumiza mabasi ine ndikuwawona. ndiye iwe fisi, undiuza chiyani? khoswe ngati iwe, usadandaule zaine ine ndili ndi wondibereka ambiri osakhala mfiti ngati iwe umasamba mankhwala tsiku ndi tsiku chitsiru.

  9. panyopako xenophobia ya mbuyako, ine singandipeze ngakhale m’bale wako Peter amatumiza mabasi ine ndikuwawona. ndiye iwe fisi, undiuza chiyani? khoswe ngati iwe, usadandaule zaine ine ndili ndi wondibereka ambiri osakhala mfiti ngati iwe umasamba mankhwala tsiku ndi tsiku chitsiru.

  10. Ndani president analamulira ku Malawi anthu osadandaula? aliyense angabwereyo anthu timakhala ndi zifukwa zomunyozera basi. Lekani kulota a phwanga,zotula pansi udindo sizingatheke, olo khoswe atadikula, mungodikira ma vote basi

  11. Ndani president analamulira ku Malawi anthu osadandaula? aliyense angabwereyo anthu timakhala ndi zifukwa zomunyozera basi. Lekani kulota a phwanga,zotula pansi udindo sizingatheke, olo khoswe atadikula, mungodikira ma vote basi

  1. Stupid Mwenefumbo,you know nothing about politics.You are neither wise nor intelligent.Regionalistic and tribalistic people,you won’t succeed this time around as you did with Bingu.As long as the south lives,MCP and a Northerner shall never rule this nation.You are silly people,the mbwenumbwenus & in particular you Mwenefumbo.Relying on religious bodies to assume power in government,not through votes,you have proved to be total failures,shame on you cowards,wait till 2019 and let the votes decide thats how democracy works if I may civic educate you idiotic Northerner.Today,you must resign,tomorrow,we want federalism,what do you actually want you foolish Northerners?Its time you rest your asses.We are tired of your barbaric behavior.

 64. Ndikuti achoke ameneyu palibe chimene akuchitapo mpaka r1 kusitha 48.72 nanga kumene kutere mchaka chino ndiye zinkhala bwanji?ndiye inu kaya akugulani kuti mudzilankhula zopusa ngati zimene mukunenazi palibe zimenezo ayenera kuchoka basi

 65. adyesedwa chibhazi awo, palibe chanzeru angatiuze, koma mr president ganizilani vuto la anthu ovutika, zisakomele ochepa okha to be honest zinthu sizili bwino, if I was him I cud have resign and go to America,

 66. Gyz mungotaya nthawi ndikumangotukwana akakhala mavuto azachumao avuta paliponse angakhale kuno south Africa zithu sizilibwino zikungokwela mtengo

 67. Those who said presdent must resgn…..fire your father first for failing to provide food in your familly,,,,then call for presdent resgnation otherwise wait till 2019 muzavotere acha abambo wanu…..case rested

  1. Stupid coment.The presedent must step down now.Ngati ukukhuta just thank God .Most people are sleeping without eating then you are talking nonsense.

  1. If he resigns your father will be new president and brings rainfall so that pple can harvest more mmmm i pity u

Comments are closed.