Blantyre City Council (BCC) has banned the sale of green maize in the city effective Thursday February 18. BCC announced the ban through a press release and said the business of selling fresh, cooked or roasted maize has been banned with immediate effect.
The council has since warned residents to strictly observe the ban, saying anyone found selling maize in the city will be prosecuted.
Residents have also been reminded through the statement that the council has laws that need to be followed by individuals in the commercial city.
The constitution of Malawi gives power any council in the country to make by-laws and enforce them.
Early this year the ministry of local government issued a directive banning sale of green maize in gardens, especially this time when the green maize is ready for consumption.
Zikatere njala yatha
Zikatere njala yatha
How many tons of maize have we roasted?kodi chimenechi sichikanakhala ufa wa mawa?
Ndekut chayambka chankhwma kumunda eti
Zinazinali mbava
Zinazinali mbava
Thats gud akapezeka mnjateni nkhani ndi njara osatizimenezo

Kuletsako kti tikhoza kutenga matenda anji ngati ku south africa botswana akgulisa inu mutiuza chan? The problem inu andale kuno kmalawikuno athufe mmationelera kwambiri ambiri akdyesa ma banja awo busnes yake yomwey mukango khuta sausange basi kuyakhura zakukhosi kwanu mxiem #simuzaionaso8vote yanga

furk u !!!!!! chimangacho ndicha amako kut mukalese?

Chifukwa chanja?? Mlungu adalitse ndithudi

Every year amaletsatu mumunda chikakhwima chimanga ndipo zidayamba kalekale monga ine wamu lilongwe city kuva izi sizachilendo ndipo ukangopezeka a city council amalanda,,,

Vc Shyma pano ine ndi mchimwene wang tikugulitsa chootcha kuno kuchitekesa phalombe zomwe mwlembazo musova

Inde mwina tikolola ; zimakolezera kuba kwambiri mma 7koloko usiku kupeza munthu akutuluka mkanjira ka kochokera ku Wainela kupita ku Mbayani wasenza chithumba ; sungamfunsenso kuti mwatengacho nchiani mantha. Kukacha eni minda mumva akulira chabedwa

Zazii zopanda salt
Zazii zopanda salt
tidya chokazinga aaaaaa
tidya chokazinga aaaaaa
amene waletsa alibe mano.
amene waletsa alibe mano.
Ndizoonadi ineso ndagwilizananazo asiye chifukwa zimabweletsa njala mdziko chifukwa muone kuti ndi matani agati mumadya chimaga chootcho or chompika naga atamati azidikila kuti akolole bwezi anthu avutika chonchi? Ine chaga mchisoni kwaana abadwawa adzaona moto walu lu lu lu!!!

Chambachi chili pali posedi, kodi aMalawi mwazindikila liti? M’mela ukudyedwa or UK, muganize mofatsa!

Apo mwateta njara yiriko ndipo yizankhrako asiyeni anthu agule ndi kugulisa mwa ufulu bola chinkhare chosaba, malawi is democratic country

Aaaaah
Aaaaah
Mwayamba khuyu eti chimanga chinayamba kuochedwa nthawi ya JOHN CHILEMBWE nde mukanene lero kut faz isiye kuotcha chimanga or kuphika kumagulisa zafodya eti ngakhale dziko lomwe timadalila kopezela ndalamako ku SOUTH AFRICA faz ikuphika ndi kuotcha mela.
Auze man ku jonz timachidya cha pa chiwaya chomwecho
Last week ndinaonanso wina akugulutsa thobwa la mmabotolo
Chophika chothila m’chele man ku #SA

kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
kodi chayambika chimanga kumpanje guys
kodi chayambika chimanga kumpanje guys
Weed fan
Weed fan
kwanu
kwanu
How do they expect locals to make a living ?

chamba chimenecho akutenga kumunda
chamba chimenecho akutenga kumunda
Shaaaaaa mbola
Shaaaaaa mbola