Acting president of the People’s Party (PP) Uladi Mussa says the current hunger situation in the Malawi is due to lack of planning and coordination by the Peter Mutharika led government.
Speaking to the local media, Mussa described the shortage of maize in the country as due to lack of timing and lack of coordination with important organizations.
“There is no coordination with the World Food Programme who can help, as the country is struggling to provide enough maize in Admarc (Agricultural Development and Marketing Corporation) markets,” Mussa said.
Mussa who was once minister of agriculture said government need to take farming as a business by providing farm inputs so that Malawians can grow crops more than two times a year and have plenty of food.
Currently, Malawians are struggling to access maize in Admarc depots across the country. In some areas people are buying the staple food at 5Kgs per person per day contrary to a set policy of 20Kgs per person on a day.
However, President Peter Mutharika and his cabinet members continue to insist that no person will die of hunger in the country.
Uladi you are a useless person, man who is a fault finder and who fails to implement his own plans, you failed to lead your party and you want to disturb PP. Most people in PP don’t want you, PP members if you are not careful with this man the party will be without supporters by 2019 mark my word
Chimanga munaoletsa chija a pp munachipititsa kuti
peter nvr cozd floodz or hunger auladi nzeru alibe
#Elnet a think ur oblangata z not working,awu kil dat sh*t mada f*kr! lastly a gat special gift for president peter koma ndiika mu blankets nangasi nd munthu olemekezeka{peter yo asshole,fuck u,}pumbwa peter munthalika
Zipani zokwanira zinayi zalamulirapo malawi ndipati pomwe tinanenapo kuti zinthu zikuyenda bwino,ngakhale omwe akuti ndi osusawo nawoso analamulirapo zinawakanika tingovomereza kuti ikakuwona lisiro zoonadi mvura siikata,panopa aliyese angopanga zake basi ukatengera zandale izi mmm atha kukugoneka panya guys
If you have good plans share with the presindent because you are also a Malawian too.
Nanga uladi angakhale President? Mwaesa jando eti!?!!
We Malawians are too lazy talkative every President is bad from kamuzu till now due to individualism syndrome Nonsense here
umphawi suzatithela kumalawi kuno, chifukwa munthu sangalamulile dziko kwazaka 5, choyamba chimene mungamuziwe ndichoti munthu aliyense aliyese akamatenga mpando wa upresident amakhala alindizingongole choyamba chimene amaganiza iye kubweza ngongole,chachiwili amaona umphawi wake,chachitatu umphawi wazibale ake pozaganizila zadziko too late zaka zamuthela, kuyambano campaign ndalama zamuthela akutengano za boma poziganila kuti azawinaso,mwatsoka akuluza, kumbukilani kuti ndalama zimene amapangila campaign amatenga za boma pamepa angathe kubweza? pamapeto ake mumaitcha kuti cash gate
Chili chonse president, anthu openga mwapanga bwanji??? Mbuli za anthu ngati uladi mulipo ambiri eti ??? Lucky Kelvin Tambala
21 days ago / Reuters
JOHANNESBURG – About 14 million people
face hunger in Southern Africa because of
a drought that has been exacerbated by an
El Niño weather pattern, the United
Nations (UN) World Food Programme (WFP)
said on Monday.
The worst-affected country is Malawi,
where 2.8 million people, 16 percent of the
population, are expected to go hungry,
followed by the Indian Ocean island of
Madagascar where almost 1.9 million are at
risk, WFP said in a statement.
In Zimbabwe, 1.5 million people, more than
10 percent of the population, face hunger,
WFP said.
“With little or no rain falling in many areas
and the window for the planting of cereals
closing fast or already closed in some
countries, the outlook is alarming,” the UN
agency said.
“WFP is looking to scale up its lean season
food and cash-based assistance
programmes in the worst-hit countries but
faces critical funding challenges,” it added.
The drought has hit much of the region
including the maize belt in South Africa,
the continent’s most advanced economy
and the top producer of the staple grain.
South Africa faces its worst drought in
decades after 2015 was the driest calendar
year since records began in 1904.
Expectations of a dire crop this season
could force the country to import up to six
million tonnes of maize, over half of its
consumption needs.
Maize prices in South Africa hit record
highs on Monday, with the March contract
for the white variety scaling a new peak of
R5,106 a tonne, according to Thomson
Reuters’ data.
In countries such as Malawi, much of the
maize crop is produced by small-scale
farmers, often just to feed their own
families. The vast majority are utterly
dependent on rainfall as they cannot afford
irrigation systems.
The drought has been worsened by an
exceptionally strong El Niño weather
pattern, a warming of ocean surface
temperatures in the eastern and central
Pacific that occurs every few years with
ripple effects around the globe, scientists
say.
El Niño events typically bring drier
conditions to Southern Africa and wetter
ones to East Africa. The dry, hot conditions
are expected to persist until the start of the
southern hemisphere autumn in April or
May.
“One particularly worrying symptom of
southern Africa’s vulnerability to food and
nutrition security is the alarming rate of
chronic malnutrition. Levels of stunting
among children in Madagascar, Malawi,
Mozambique and Zambia are among the
worst in the world,” WFP said.
Oooooh thus so bad
Really worse
Kuteleko ngati kuli wamisala wamkulu ndiye iwe, umangotolera m’ma bin , which mean u don’t know even how and where food come from. Ngati mutu wako umagwira just find out pa net or umdzimvera ndikuwonera TV wamva! Lucky
kodi U Musa sakuthesa njala kwawo bwa popeza nayenso ndi president.
kodi U Musa sakuthesa njala kwawo bwa popeza nayenso ndi president.
Ulad Musah Mwazindikira Pano Kuti M’dziko Muli Njala Mulibe Manyaz Inu Eti Mwaiwala Nthawi Yanu Chimanga Chidayamba Kusowa November Pamsika Wamavenda Komaso Kwa Admark? Pano Bolan Chimanga Chikupezeka Paliposo Koma Ndalama Ndizimene Anthufe Tilibe Mudakati Mutsatire Mau Amalemu Bingu Wamutharika Okana Kutsitsa Ndalama Yakwacha Bwez Pano Zinthu Zilibwno Ndye Musaime Pachulu Mkumati Peter Wamutharika Walephera Zopusa Basi Mufuna Kuphimba Zolakwa Zanu Mesa Inu Kuti Muluze Mavoti Ndikamba Koti Mudalephera Kuyendetsa Dziko Lomweli M’ndani Adali Ndichakudya Pakhomo Pake Mu Ulamuliro Wanu Mudziganizire
Sleeping cat never catch a rat!
Mavuzi awo a president nyapapi wopanda nzeru,vuto la anthu opita sukulu zamakedzana ndilimenelo,’Zinthu zinasintha kutsatira old sylubus akulephera nazo masamu.
Scotrand plz come back
Ine chonene ndilibe, anandiphunzitsa kukhala mphunzitsi now its two years sakundilemba ntchito nde njalayi ane nditani? Ndimakhala ndi agogo okalamba amadalila kut mzukulu wawo ndimmphunzitsi moyo usintha koma mpka pano adakvutikabe. Kulima kumene feteleza akumasowa. MUZONSE NDIYAMIKA MULUNGA. MULUNGU ADALISE MALAWI
Khulupila mulungu ndiothekela zosatheka ndimunthu zimatheka ndi mulungu, ndiothekela kusintha nyengo zako, ngati anasintha nyengo zanga chingamuvute ndichani kusintha zako there is no too much problem that God can’t solve
Amen
Amen
Mwians are good at talking. Nothing changes we fail to improve as a nation
The greatest mistake u did my fellow malawian z voting de same government involve in cash gate back to power.they r de same person anamusokoneza bingu nd by dat time peter fails to leads all de ministrie given to him amangomutsina pafupi pafupi,how do this type of person be apresident?Being aprofessor sikuti u r greater than God or pipo,leadership z based on fearing God alone.
The greatest mistake u did my fellow malawian z voting de same government involve in cash gate back to power.they r de same person anamusokoneza bingu nd by dat time peter fails to leads all de ministrie given to him amangomutsina pafupi pafupi,how do this type of person be apresident?Being aprofessor sikuti u r greater than God or pipo,leadership z based on fearing God alone.
Ulamuliro Uwu Mulungu Sanausankhe!
Anthu akumalawi ndiwogona. Muzazuka liti kaya. Impeachment is needed
Well cam twapochele akuno kwa ayao MMWE wawiyi kaka yachisagula ligongo lyawiyi. Akulungu akanyisye wula naga mli mpwawo mose mutende mlungu abugulile lilanguka ndawi jache muluzi kwaliji kwana sala mambo wula jaliji mkunya sano mmwe walunda kumposa mlungu mtende yalunda yenuyo tulole nikawa ngambwa chibudu une jwachi yao
N u so called Uladi Mussa what u did when u was minister v Agriculture!? Now u came with new idea v planting twice a yr when ppo hv no money to buy farming equipments! N this so called DPP gvnt aaaaaaa very shit! N Peter u r urine indeed!
Mbava mussa ungauze chani fuko la Malawi just keep yo shit close
iwe ndiwabodza Ku South Africa kuli njala aaaa ukunama
uladi simunthu!
Kaya msova? government inja?? 2 much talking 4 nothing inja government?????? F,,,,,,,,,,,ck ,,,,,,,,,,,,the,,,,,se,,,,,,,,,,,bit,,,,,,,,,,,,,,ches,,,,,,,,,,,,,government,,,,,,,,,,,,the,,,,,se,,,,,,,,,, shit,,,,,,,,?,?
In every aspect of this Mthalika’s administration is nonsensical approach.
What a failure and disgrace to our young democracy Malawi.
An educated leader as he claims himself, really Malawi would never be where it is today, shame on him.
Hunger,and all they can think of is paper money the leaders,why do they not allocate land,and peopel can sart plating not sell it,allocate on provision people should plant,is it hat diffucult not at all
Wanzeru ana kamuzu chakudya sichimasowa akaona kuti zivuta amalimitsa a payoniya zakudya nkuzipanga control mitengo now pano nonse ndi a business palibe anganene chanzeru mungofuna zanu zizyenda ife tikufa ndi njala adyera ngati inu sindinawaone. What a shame
Ay peter sivuto mu blmy satan coz he z de 1 amene anapangitsa chigumula ku chikwawa and other areas
Kkkkk mpaka pano amalawi simumadziwabe kut cashgat idayamba nthaw y mutharika?nde ndinu ovesa chison bwanj….azikuposani azungu kuziwa zadziko lanu aaaa,577 bilion ili kut?tiyen tizingopitiriza kuvutika azanu akupitirira nd casgat tochepa tomweto
zose akut ndi jb ,iwo anatilonjeza kuti azathesa mavuto onse ngat iwo ndi a yesu lelo tawonan amalawi azanga akugona njala zitheka kapena anangoti tingowavotela basi zatha
Munthuyu ndi amake aja anaba ndalama zambiri pano akudya mavolosi ndiye akutumbwanso fotseki zanu ana anjoka inu
Limbana ndikukonza chipan anthu akuthawa chan mwa iwe mulibe utsogoleli.
Angaganize zanjala kusiya za mathanyula?
Ulandi Musa, umenewo ndi umbuli kapena dale??? Ndani sakudziwa kuti chigawo cha Southern Africa chakhudzidwa ndi njala! Ngati South Africa ikulira ndi njala, ndiye akulamulira ndi Peter ku SA ko?
R u realy malawian or ur 4rom s.africa? y r u against de truth?if ur dpp supoter dat shud not affect us a real malawian cn not bak up wt peter iz doing ur stupid and u knw nthing about malawi shit
Malawi news
Malawi nation
The most stupid person is u Lameck bcoz Peter is God who can bring rain, there are economic crises all over the world, but bcoz u r busy sleeping there u can’t see even hear. Wake up mother fucker haaa!!! Go in Zimbabwe and in Ethiopia!!! In south africa things are tearing apart , within five years everything will in mess.
Southafrica,Zimbabwe Ndi Malawi Njala Yokhayokha! Enawa Anadyanawo Za Cashgate Awa!
Southafrica,Zimbabwe Ndi Malawi Njala Yokhayokha! Enawa Anadyanawo Za Cashgate Awa!
south Africa yake iti?iwe wamisala eti?
21 days ago / ReutersJOHANNESBURG – About 14 million peopleface hunger in Southern Africa because ofa drought that has been exacerbated by anEl Niño weather pattern, the UnitedNations (UN) World Food Programme (WFP)said on Monday.The worst-affected country is Malawi,where 2.8 million people, 16 percent of thepopulation, are expected to go hungry,followed by the Indian Ocean island ofMadagascar where almost 1.9 million are atrisk, WFP said in a statement.In Zimbabwe, 1.5 million people, more than10 percent of the population, face hunger,WFP said.“With little or no rain falling in many areasand the window for the planting of cerealsclosing fast or already closed in somecountries, the outlook is alarming,” the UNagency said.“WFP is looking to scale up its lean seasonfood and cash-based assistanceprogrammes in the worst-hit countries butfaces critical funding challenges,” it added.The drought has hit much of the regionincluding the maize belt in South Africa,the continent’s most advanced economyand the top producer of the staple grain.South Africa faces its worst drought indecades after 2015 was the driest calendaryear since records began in 1904.Expectations of a dire crop this seasoncould force the country to import up to sixmillion tonnes of maize, over half of itsconsumption needs.Maize prices in South Africa hit recordhighs on Monday, with the March contractfor the white variety scaling a new peak ofR5,106 a tonne, according to ThomsonReuters’ data.In countries such as Malawi, much of themaize crop is produced by small-scalefarmers, often just to feed their ownfamilies. The vast majority are utterlydependent on rainfall as they cannot affordirrigation systems.The drought has been worsened by anexceptionally strong El Niño weatherpattern, a warming of ocean surfacetemperatures in the eastern and centralPacific that occurs every few years withripple effects around the globe, scientistssay.El Niño events typically bring drierconditions to Southern Africa and wetterones to East Africa. The dry, hot conditionsare expected to persist until the start of thesouthern hemisphere autumn in April orMay.“One particularly worrying symptom ofsouthern Africa’s vulnerability to food andnutrition security is the alarming rate ofchronic malnutrition. Levels of stuntingamong children in Madagascar, Malawi,Mozambique and Zambia are among theworst in the world,” WFP said.
Tamulandileni Uyu Zikumulaka Kuyendetsa Dziko&to Solve Problems Mayi JB she tried not wat u call prof. people u are jst wearng t shirts with logo of maize then u are sleepng with hunger, DPP govt please distribute maize in all admarc depo b4 it ‘ll b 2 late.
Tinene zoona munthu ndiwachabe bola nthawi ya cash gate
Tinene zoona munthu ndiwachabe bola nthawi ya cash gate
Kamuzu anali oyipa misewu yake mkuyendamo, Muluzi anali woyipa xool yaulele ana anu akupitabe, Bingu woyipa subsidey mukulandira, Jb woyipa mudzi transformation, now Pieter? Amalawi ndiuti adzakhale wabwino
Kamuzu anali oyipa misewu yake mkuyendamo, Muluzi anali woyipa xool yaulele ana anu akupitabe, Bingu woyipa subsidey mukulandira, Jb woyipa mudzi transformation, now Pieter? Amalawi ndiuti adzakhale wabwino
Kambani zina abale kodi ma flood s aja mwaaiwala mmmm mwatopa eti i don’t agree with u greedy pple. Uladiyo osagawa chimanga iyeyo bwa ha ha ha musova.
Kambani zina abale kodi ma flood s aja mwaaiwala mmmm mwatopa eti i don’t agree with u greedy pple. Uladiyo osagawa chimanga iyeyo bwa ha ha ha musova.
Don’t cry muna vota nokha DPP yimalakwisa payamba inu mwayipanga double koma mukuliso asa mukulila zichani apa
Don’t cry muna vota nokha DPP yimalakwisa payamba inu mwayipanga double koma mukuliso asa mukulila zichani apa
Kodi si inu nomwe ukutizunza ndi njala ndi ma cash gate munachita aja. M’malo molimbikisa chipani chanu anthu akuthamo, kuthawa. Olo mutani simudzawina ndi kulamula Malawi. Ufiti munachita uja wakwana.
Kodi si inu nomwe ukutizunza ndi njala ndi ma cash gate munachita aja. M’malo molimbikisa chipani chanu anthu akuthamo, kuthawa. Olo mutani simudzawina ndi kulamula Malawi. Ufiti munachita uja wakwana.
Uladi vutoli linadza chifukwa cha mvula yomwe inagwa mowononga,angakhale amabungwe akudziwa izi
Uladi vutoli linadza chifukwa cha mvula yomwe inagwa mowononga,angakhale amabungwe akudziwa izi
abale pitala muulamuliro ake wakumana ndizambiri ma floods zenofobia no rains inuyo mukanatani includ. cash gate think twice ziko saendetsa ngati njinga
abale pitala muulamuliro ake wakumana ndizambiri ma floods zenofobia no rains inuyo mukanatani includ. cash gate think twice ziko saendetsa ngati njinga
Go 2 zimbabwe, mozambique southafrica and elswhere. Ppo are cryng. Climate change iz th main coz. Kugwa kwa ndalama ngakhale ku sa .america iz th main problem. Stop the blame. Uladi dont campn in dat way
Go 2 zimbabwe, mozambique southafrica and elswhere. Ppo are cryng. Climate change iz th main coz. Kugwa kwa ndalama ngakhale ku sa .america iz th main problem. Stop the blame. Uladi dont campn in dat way
we tok abt de current prblm,not de past i.e kale limabwerera? shame!
Umbuli ndi ufiti paokha moti president akhale ngati meal ticket for everyone kkkkkk.tiyambire kuchapa mitu mopanda nzerumu zithuzi sitizionaso mwa upside down.
Mwa umphawi ndi umbuli..adasankha olakwika! akuti chikuwawee!
How many tones of maize is Uladi expected to harvest end of this season & much did he in 2014 & 2015?!.
That is wat we call democracy pipo allowed to talk bull shit
Zavuta kumpanda mavuto aja amati athesa pano nde worse bola jb osati mbuzi iyi kaya ndiwakuti nkuluyi anthu akufa ndinjala msundu wake
We think that government can do every thing to your family, then you will be complaining each year. How many acres have you planted this year? Non, job many bags of maize did you buy to feed your family? None. Malawians are sometimes pathetic. Those who fail to prepare, prepare to fail. Its either way.
Timemark! In Malawi
Dpp ndi chipani chokanika ndi chikutumbwe wanuyo ine bolani wa pp/mcp kaya tiziona
Kelvin u r right chikala uyo y u voted him luk pipo arw suffering now galu wachabe uyo
Oonelela mzelu akalawa mgalaund ku heda mpila wa mmapazi,
President aliye amalawife timamdandaura!!!!! vuto siPresident koma ndikusauka kwa dziko,,,,
I dnt think we can blame z govt,I think a comment is becoming from a frustrated politician! Let’s all work together 2 develop Malawi.Malawi does not belong 2 Peter
true!
true!
Nthawi ya Jb sitimadziwa kuti kuzambia kuli chimanga obwerawa ndi amene amatigula chimanga chathu, koma lero tagwanayo under bingo’s goverment.
ndiayankhile a APM zachisilu
Anthuni musamaiwale kuti pachisankho timasintha President koma ena onse mumipando yonse ndi omweaja. Chipani chawo chikaluza, amangolowa muchipani cholamula osalabadila section 65. Believe me all the Politician are Crooks palibe angazapange zinthu aliyense kukondwa never. Tisachedwe ndi maCrookwa tiyeni tigwire ntchito molimbika, kuti tizidalire pachuma osati kukhulupiliqa andale. Onse ndi amozi ndipo njala olo tinakakhala opaoda President ikanabwelabe. Mitengo yobwelesa mvula mesa ndi ine tikudula. Kodi simunawelenge Baibulo? Kuti masiku osiliza kuzakhala njala?
Zachisoni amalawi w really need to change our mind set, moti a uladi mussa 1, nanu ndi mu malawi 2, mwakhalaposo nduna mu maboma a udf,dpp ndi pp 3,mwakhalaso mp nthawi yayitali mpaka panopa moti ku consituency yanu anthu akuyembekeza zeru zanu 4,mwayambisapo chipani chanu kuti nanu mukufuna usogoleri wa ziko 5, mwa yendaso zipani zambiri moti mwabera ma manifest ambiri 6,pakati panoso mukuyankhula monga musogoleri wa chipani chomwe chimene chalamu lirapo ndiku chosedwaso ndi eni amalawi pazisanko posachedwapa, pempho ndiloti ngati muli ndi luso, zeru,njira,maganizo, ukadawuro ndi machitidwe taturusani poyera kuti tonse pamozi amalawi tithese mavutowa but but but kubweleza monga tonse tikukuziwira a change goal mumutu mulibe cha zeru choti anganene, Pliz pliz leave prof APM & DPP alone amalawi tikuwona kuwala pasogolopa moti tikugwira momwe anayendera azathu kuchoka ku egputo kupita ku canaani anakumana ndi zovuta koma mpaka ana kafika,nafeso 4ward ever
Musalimbane ndi boma. Anthu oipa a pp
sukuzapezekaso dolo ngat chair munthu wamkulu ameneuja
Udindo uoneke apa
Zofuna a Malawi
nvula ikavuta kumakhala njala mmene nde sizoblema munthu njala siinayambe lelo kumalawi
He is right
kod anthu mumangoti masiku omaliza kod mudawelenga kut nanga masiku omalizawo akuwonekela ku malawi kokha bas khan ndimavotedwe apa akakhala mulungu amaona zaiwewekha pawekha mungot tsiku lachimalizilo mukulidziwa nanga adakuuza ndindan kut chimanga chimanga chikadzasowa kumalawi lidzakhala tsikula chimalizilo ndindan dpp pusi ichoke sitiifuna anthu tooooooooooose kupatula iwe wakumulange fuck yu nay
Mukalimbana ndi president mugwa chagada, kulibe amene amadziwa za mawa kuti mukaloze mavuto omwe ku malawi alipo! Ndiye uladi mussa wapanga chani ngati akuona njala kumalawi osapanga zoti ithe bwanji kusiyana ndi kumangoyakhula iye atakhuta! Haters go to hell! 2019 wooooo mudakaliratu maso mpaka kutupa
Jb mpakana liti? Zangowavuta ababawo.mukukamba za Ndege muzikambaso za k577 billion zonse ndi ndalama za amalawife.
Inu takambilanani zothetsela njalayo or chotsani nkhalamba zonse alowepo achinyamata! Nanga nkhani ikhale yomango blama wina!
Ndale pa nyasaland hahahaha bora ife anthawi ya Hestings kamuzu Banda za njala tinkangova dollar ndi kwacha zimapherana pano iiiii dollar ili pa K700, Pound ndie tisachite kutchula hahaha Boma ilo
Zoona man bora kare
when the ship is sinking,you blame th captain…not th passengers
Achair one day said Vuto limene amalawi tilinaro ndikuyiwala.munthu amene akunena zowona sitimufuna koma wogawa ndalama kapena nsalu.INE NDIKUTI ZAKWANILITSIDWA ZIMENE AMALAWI AMAFUNA.
tisalodzane dzala baibulo linanena kale kuti matsiku otsiriza kudzakhala njala ,nkhondo ndi zina zambiri. mau akukwaniritsidwa ,akulepheletsa mvula dziko lonselino ndi a president? tapitani ku mozambique mukaone mavuto ali kumeneko, katundu wakwera koopsa komatu sakulozana dzala.chomwe mungadziwe olo mutatani palibe amene azakonze zinthu,nthawi ya kamuzu,atcheya ,bingu,amanu munkati chani? musiireni mulungu akonza ekha. amalawi tatani kodi?
admin check ur english =in the malawi whats tht??
Kkkkk hand mistake my bro
I really understand
Ndizoona akuyenela kuchoka basi Achoke achoke achoke akuipitsa mbiri ya dziko la MALAWI
Ndipo sakunama akubena zowona
A Malawi anga osamathamanga magazi ayi.Kulaamulira dziko ndi kulammulira banja mzosiyana olomutakhala muli inu pa mpandopo anthumso adzati bola Peter mzoterotu.Abale,chachikulu msinkhu dziko lathu mlosaukadi.Mtamganizani chaka chatha ndingozi ya madzi ija wakolola matumba opitilira 10 mndani?Penapake tidziona influence yazinthu.Kodi iwe Malawi,udati kukhala dziko losauka lopanda chodalira ngati zomwe amadali maiko amzathu taona ukudanitsatu wanthu.Maiko amzako kuli,Copper ,Gold,Alluminium,mafuta,Bronze ndi zina koma iwe Malawi kumangodalirira mvula ndiyenotu auze anthu apepese kuti mkusauka kwako basi.A Malawi annzanga,wabwino ndi Mulungu yekha basi chomcho tingopempera kuti tisamakuma ndi mavuto odzetsa njala ngati chaka chatha.Malawi sintha msanje,kaduka.
AMathews mwangodana naye Peter.Zaoneseratu kuti inunso ngolephera.Mukuona ngati sitikukuziwani?Ngati mukulephera kuyendesa bwino banja lanu lija NDE mungayendese dziko?Osamachuluka nzeru pamene nzeruzo mulibe.Chepesani zoyankhula vuto lanjala ndi LA kumwera kwa Africa so Peter.Let’s join hands and solve the problem
Tamuuzani Uladi Mussa amve zimene Nzomera Ngwira akunena pa ZBS
Guyz!kodi bambo khola wa malawi(president) ndani? Chala chiloza amene ali pa mpando,potenga boma adali wakhungu samkaona kuti chakudya chochepa.sizöona kumazembaitsa mau a chulungamo pamene choipa chikuchitika.pachifwa pa zimenezi dziko lathu ndi nkhokwe ya corruption
kodi ndarama zomwe munagulisa ndege zija munazitafuna zinatha? bwenzi titagura chimanga panopa! koma inu ndarama kumalizira kugura ng`ombe
Government has three arms, Mussa is also in government, that means he is also a poor planner. Kkkkkkkk
Bola peter kusiyana ndi hule mwana wanjoka iwe hule u mislead JB ozafa imfa yowawa9
Ubwino wake njalayo ili ku Thyolo kumwera komweko i dont care mmene mumamvotera
ULADI,CHANGE GOLO ameneyo!akamalankhula ngati zenizeni koma iiiiiiiiiiii mbala yachabechabe! Ndimayesa munalephelesa Joyce inu? kumangotokota zopanda pake ndichifukwa Ngwira amafuna kukutikita!unachenjeresa iwe
fuck hu are playing blme games..fuck the opposition syd shud we say yayo ndiyomangobwebweta y cant the put aside dola inayake nd contrbte to the communities or matumba ochepa chabe i thot this oz the time to tek advantge to show us wat u a capable of..av seen churches donatng bt none of these so cod partys hav don that..which jus shows that all of u ndi mbava..campain is nw.fuck u nonse pa chithunzipo
Inde Bwampini walephera, but bring forth your ideas Mr Uladi Mussa, Malawians need solutions and not blame games like this. Its a waste of time
do we hv the przdnt in malawi? evry problem akut ndi JB chosencho nthawi imene ankapanga campaign ankati timuvotere azakonza zonse zolakwika amapanga JB.pano tinamuvotera mmalo mokonza akuonongerabe nkumatiso bola nthawi ya cashgate zinthu zinali bwino.tinakanakhala kut amalawi ambirife ndiozindikira ndithu uyu amayenera kuchoka nthawi yake isanakwane thru peaceful means ali ndi mwayi kut akulamulira sleeping country.
Mr Nyirenda Mumakhulupilila Kuti Peter Anasakhidwa Ndi Amalawi? Muiwale Zimenezo Chilungamo Chake Amadziwa Ndi Mc Sorn Mbendela & Saulosi Chilima. Mudzandifuse Ena Amene Anathandizila.
amandivetsa kuwawa muthu ameneyu
Vuto la a malawi sitichedwa kuiwala
why most of the pple who complain about munthalika ndi akumpoto?
Ine siwakumpoto koma peter sindimamufuna ayi or pang’ono ndiye usamaganize kuti anthu akumpoto okha ndiwomwe akhudzidwa
he wil rule till 2019 ngo,ufune usafune…lol
malawians ara dead pple……….. even chickens react when provoked. the problem is we believe in peace without justice.
Galu ndi iwe ukuti peter sukumufuna ukuwona ngati tnchito yoyendesa dziko ndi yophweka?? ukawafuse ambuye wako,, agogo ako komanso Amfumu akwanu Peter alipo mpaka 2024 wether u want or nt kkkk Mtumbuka iwe
Galu ndi iwe ukuti peter sukumufuna ukuwona ngati tnchito yoyendesa dziko ndi yophweka?? ukawafuse ambuye wako,, agogo ako komanso Amfumu akwanu Peter alipo mpaka 2024 wether u want or nt kkkk Mtumbuka iwe
Zachabechabe zonsezo,kulozana zala ndizinthu za ziiiiiiii
Zachabechabe zonsezo,kulozana zala ndizinthu za ziiiiiiii
@lonjezo ngati iwe kapopa tayala ukut APM siukufuna mapwepwete aname angakakufunenso ndakayika that is my vote no matter wat
@lonjezo ngati iwe kapopa tayala ukut APM siukufuna mapwepwete aname angakakufunenso ndakayika that is my vote no matter wat
Aise ndine kapopa ngolo wati et? Osamangonena zinthu chifukwa sukundidziwa bwino and mwina zinthu zomwe ndili nazo ineyo iweyo ulibe ine changa ndichisoni ndi abale anga amene akudandawula njala dairy pamene boma lili pheeeee
@ cisale Ineyo aise kucha kwa dzulo lomweli andibela radiater, disributer ndi tyre pa galimoto yanga nkhani yake ndi chitetezo kulibe and choti udziwe ndichoti njala imeneyi ndiyo gwelo la zose
@ cisale Ineyo aise kucha kwa dzulo lomweli andibela radiater, disributer ndi tyre pa galimoto yanga nkhani yake ndi chitetezo kulibe and choti udziwe ndichoti njala imeneyi ndiyo gwelo la zose
Douglas Zeya Nyoni anzathu muli ndi pulezidebti kwanu, nanga njala ikukudza anthu akumpoto okha poti iwowo alibe pulezidenti? Zomanyozana sizizakuphindulirani tonse ndife a Malawi mavuto agwera tonse olo enafe sitinavotere boma lilipoli.
#Nkasa, mkuluyi sananame a nyimbo yake ija” Sindidziwaaaaah aah kuti ndi chani……kodi linali lotoooo~ Koma ndinaona wina aliyeseeeee akuliraaaa
That’s great mr #JELSON MLOWOKA, we’re Malawian we’re one blood, and this disaster is for every Malawian. Zonyozana aiiiiii.
Tearing himself as if natural disaster is caused by a person as an Mp what is he doing for his people
The president has responsibility over the nation. He has national resources at his disposal. According to the constitution the president is answerable on all the affairs of running the government. Read the Malawi constitution Juliet.
Koma zafikapo. A Malawi kusankha molakwika. Chakwera analipo oti akanakuyendetserani dziko bwino lomwe koma kumakasankha Mr. Ibu. ndiye lero nkumalira. Nanga poti njalayi chaka chamawa iposa pamenepa, ndiye mudzatani?????
Peter is really lacking skills to curb hunger in malawi small state. Long time ago there was hunger in Egypt for 7solid years, but they survived becoz they followed proper skills to eliminate hunger.
give him.
Nena ndiwe he z ldy for ur fulsh idea
only GOD Knows the truth
Asatinyasepo awa aargh
Bola Amayi alowenso m’bwalo apa kkkkkkk
He is gud at tearing others but next tym iyeyo adzanyenyedwanso ndi ena
Olo mutinyoze ine ndili nganganga pamatako pa iyeyo
Malawians should tackle the problem and stop blame game.
ohhooo m matuluka nthawi yanjala yokhayokha eeeti ndakuwonani mukawuzane komwe munasiya ndalma ya ndege tikuzifuna nanga simawona ngat tayiwala mukuwona vuto lanzanu inunso anu ndiye kuchita kut mbweee kumbuyo zachamba zanuzo mukasake kochtila
you dont hav a point go to hell moron
Awizeni iya
Kodi Mumaona Mtundu Wa Amutharika Umasamala Za Amalawi Kuti Ndiamene Amawasakha Nkukhala Pa Mpandopo. Njala Yavuta Maka Anthu Akumudzi Aitenga Kuti K1500 Yokagulila Bigin La Chimanga Nanga Yogaisila Nanga Ndiwo Nanga Soap? Mavuto Tilinawo Bola Amayi Joyce Banda Anayesesa Kumbali Yawo Ngakhale Ena Anafuna Kuwgaipisila Mbiri Yawo Ndi Nkhani Ya Cashgate. 2019 JB Boma Basiii..
Who is the president now? When commenting guys, make sure that your Intelligence Quotience [IQ] is well balanced. Hunger is now. This is his poor planning!
kkkkkk thus why they just vote without considering about the future just because they are coming from the same village Thyolo
what about Zambia, South Africa, Mocambique, Zimbambwe, Lesotho, Swaziland and all other countries in Southern Africa…. is it still the same Peter poor planning? dont make me laugh with your comments… kkkkk
So what are u doing to solve the problems we are facing Mr Mussa,stop playin blame games,if u hv a solution bring it on after all u are also a Malawian
I agree with Musa
Uladi tears himself apart > why did he fail to run his party if he is a master of planning and co-ordination. Tatipaseni ndalama za ndege bwanji.
All DPP r foolz ndinu mbatama and mbutuma .
Agalu a dpp boma likugwa koma muli nganga kusapota chinthu cha kufa Peter
Uladi Mussa ngakhale maso ndimaso pa mseu ndi ngakutukwane za Nthupi kumene uli iweko undisamale ntheradi
Uladi Mussa ndi munthu openga kwambiri. Chimanga chake chiti chomwe chikanakhala mu admarc depots popeza iye ndi mayi wake oduka bere uja anachigulitsa nkumati chinali chowola.
Ukunama iwe wasuta kanundu eti
Pliz don’t blame peter only but we Malawians because we’re abit lazy, why can’t we invest in irrigation farming osati wasting our precious tym blaming somebody….
Dat z true frnd..
Were we hardworkers during Bingu era than we are today? I dont think we are more lazy than before,lets accept its time for prophecies to be fulfilled, things will get worse even if we change leaders,the incumbent presdnt is not d fault either, t z just the time we are in,lets pray that we shud make it to eternal life where all these shall come to pass.
Wow,in Bingus era pple worked hard,if u can remember well about green belt project where we as nation had surplus food and mpaka chimanga china tinatumiza ku Haiti but see now no more green belt at large scale, we’re importing maize from Tanzania & Zambia.
oh chimanga munagulitsa chija nkumanama kuti chaola chikanakhalapo bwenzi zinthu zitafika apapa? Stupid pp
oh chimanga munagulitsa chija nkumanama kuti chaola chikanakhalapo bwenzi zinthu zitafika apapa? Stupid pp
Inu musalilire peter coz ur jb ndiamene anatenga chimanga chonse munkhokwe chimene anasunga Bingu ndikumapasa anthu kumanama kuti chawola tataya anakataya kuti? Ur de one who makes hunger in dis countray is better to be quite.
Mmm thingz are becoming no bettr at all.. Malawianz are dying ov hunger
Inu musalilire peter coz ur jb ndiamene anatenga chimanga chonse munkhokwe chimene anasunga Bingu ndikumapasa anthu kumanama kuti chawola tataya anakataya kuti? Ur de one who makes hunger in dis countray is better to be quite.
mmmmm!!!bodza.
RAJAB CN U TELL US KUMENE ANAKATAYA CHIMANGA CHOWONONGEKA CHIMENE AMANENA JB KUTI CHAOLA???
we r talking of the current situation
Haha koma iweso Mr President said Nobody In This Country Will Die With Hunger. Awa nde mau amene anthu akuwasungabe mmitima yao. If you blame J.B then why Bingu blame Atcheya and Atcheya blame MCP and J.B blame Bingu and now APM blame J.B. And Mr Kapito ask who will direct us in right path. Coz every president since democracy came in Nyasaland every president blame winayo. We need to stop such this silly blame instead we should focus on development not politics. There is no way a citizen to follow such stupid ideas from political leaders coz politics is dirty game. Kamuzu was better coz he concetrate on development. We need such vision leaders. Bingu started well but at the end he concetrate on politics not development. It is my wish that the first lady should not be like Callista and Getrude coz the advise they gave to their husband will be politically. No politician first lady.
Fundules bwanji otsalima chake?Now 2years in goverment otsalima chake bwa? which means nthawi ya Bingo mkadya chimanga cha Bakili Muluzi? We are talking present tense nt past years
Inu Mukuwoneka Kuti Mukudya Naye Limodzi Peter Wanuyo. Mungalakhule Zopanda Mzelu Ngati Zimenezi Koma Mukuziwa Kuti Anthu Akuvutika Ndi Njala? God Will Punish U With Ur President In The Name Of Jesus Christ.
Anakapatsa anthu chimanga chotsekuka patsa anthu mutsogoleri wa nzeru iwe umafuna akapetse chiyani?
Iweso mathwes kupusa eti mmeneulilimo nkumadalira zopasidwa bwanji uzilima chako kusiyana nzongo nyoza a plzdnt anthu nose amene mumanyoza mnayamba mwakhalapo ndi nkhokwe pa nyumba panu.
JB left two years ago. What’s the professor doing?
Parliament gave them k30 billion for maize, Egypt has just pumped in millions and China has also pumped in billions. Where has the money gone coz there is no maize in markets? Sad eeee
wachamba uyu
Anthu amene mukuti God will punish even u God will punish two why peter is not God amabweretsa mvula ndi mulungu not peter.
Anthu amene mukuti God will punish even u God will punish two why peter is not God amabweretsa mvula ndi mulungu not peter.
UNADYA ZAMBIRI ZA DPP
Mmmm…..! mkamaliza nonse mundiuze.
Mmmm…..! mkamaliza nonse mundiuze.
Inu aname achoke ku state house azakupaseni chimanga mumakomo mwanu aa ndakayika manja lende ntchito ndikuminda
Thanks to JB 4 mercilessly devaluating our beloved Currency.