Just in: Ten arrested in line with Neno gruesome killings

263
Neno Killings

Four coffins lie at village ground in Neno.

Reports that Malawi24 is following indicate that Malawi Police officers  have arrested ten people in connection with the brutal killing of four elderly men suspected of witchcraft in Neno earlier this week.

On Monday, a mob murdered the elderly people after suspecting that the four had killed 17 year-old Flora Kanjete in Chimbalanga Village by a magical lightening.

Police in the district identified the four as Eliza Ennosi Kanjete (86), Elenefa Kanjete (76), Byson Kanjete (73), and Idesi Julius Kanjete (69). They all hailed from Chimbalanga village, Traditional Authority Dambe in Neno.

Police in the district identified the four as Eliza Ennosi Kanjete (86), Elenefa Kanjete (76), Byson Kanjete (73), and Idesi Julius Kanjete (69). They all hailed from Chimbalanga village, Traditional Authority Dambe in Neno.

The act has been heavily condemned.

The arrests come just after Malawi President Peter Mutharika asked Malawi Police officers not to sleep over this matter.

Share.

263 Comments

 1. Yes,if they were practising witchcraft its a serious ofense which requires God’s judgement “not a man/men” because oly God has the full powers to give life and to takeout life according to his will.

 2. This is bad ,,,tsoka kwa iwo apanga izi amfiti ali phee munthu asakalambe walakwa…..rest in eternal peace azigogo

 3. Iwe yassin ukudziwa kupha nzako ndikulakwa. magogowa ngati amachita zimenezo akanangowapitira kwa apolice. koma pooti apha okha nawoso apolice awakhaulitse

 4. nanu inu ajohn musamakhale ngati opanda mzelu mwavaa kapena mumatambilalimodzi ndi timagogo tafati watsala naweso ndakuwona upita uwalondola magogowa mumadyela limodzi akapha et kkkkkkkkk

 5. Guys amalawi anzanga mpaka anzanu kuwapha chomcho. off coz mukuti mwapeza ndi ufiti bwanji osakanenera ku police magogowa. Ndizinthu zovuta kuti bola likukhulukiren chifukwa mwangokoza nokha. Ndiye amati lamulo lakumalawi amati okupha nzake nayeso amphedwe.

 6. Guys amalawi anzanga mpaka anzanu kuwapha chomcho. off coz mukuti mwapeza ndi ufiti bwanji osakanenera ku police magogowa. Ndizinthu zovuta kuti bola likukhulukiren chifukwa mwangokoza nokha. Ndiye amati lamulo lakumalawi amati okupha nzake nayeso amphedwe.

 7. hy khhani izi zafiti zatikwana tsopano tsoka kwamene amatamba mutiyikile yanjala kuno osati kumangoti athu apha khalamba zatikwana shuttt

 8. hy khhani izi zafiti zatikwana tsopano tsoka kwamene amatamba mutiyikile yanjala kuno osati kumangoti athu apha khalamba zatikwana shuttt

 9. we using Shaliya laws now,opha mzake nayeso anyongedwe,utsi sufuka pondanda moto l hope ena atengelapo phunzilo zosowetsana mmatsengazi sizabwino mwatani kodi? Tione mbali zonse apa maka,makaso kwa mwana ophedwayo analiso ndiufulu okhala ndi moyo

 10. Shame usaweluze pakuti uzaweruzidwa mukuweruza kusonyeza kumuderera Mulungu remember that ur a person and also u did mistakes and u will face a painful death as u did to ur friends God 4 give u cause u forget one of his comandmets “usaphe” Remember God is always awake

  • They have 4get 2 GOD’S COMMANDMENTS:USAPHE & uzilemekeza ATATE AKO NDI AMAKO.IT MEANS,WE MUST RESPECT all the elders. coz they are same with our mum & dad.

 11. Ine sindikudabwa paja malemba akuti masiku otsiliza chikondi chachibadwidwe chidzazilala anthu adzakhala odzikonda okha ukutu nkusowa chikondi tili m,masiku otsiliza wanzelu achenjele?

 12. Anthu Tasiya Kukhulupilira Mau A Mulungu,tikukhulupilira Satana Amene Kwake Ndi Kuba,Kupha Ndikuononga.Anthu Okalamba Akuzunzika Ndikuphedwa Popanda Chifukwa.Zomvetsa Chisoni,ambuye Atithandizire Kuti Dziko Lathu Liwomboledwe Ku Mavuto Amtundu Umenewu.

 13. respect to those who say ufiti kulibe, ndinu anthu olimba moyo kwabasi; respect to those 10 strong gays poti kuranga kwanu; respect to those muoneka odabwa ndikhaniyi poti bible mmango gonera. ananena ndani kut dzitsilu dzisama pasidwe ulemu?????

 14. Haaaa,, they should arrest the whole village. why being selective????? this is what I call it inanity of the president. actually I have no mercy for those idiots. they were killed for what they did

  • Killed for what they did? What did they do? Kill a girl with lighting? Are you serious and are living in this time of so much education and knowledge. You don’t know that people are strucked by lighting everywhere and lighting is cased by whay happens in the clouds when there are storms. You use internet for what if you can’t even google to educate yourself how lighting is made. Or is the standard of education that much low in Malawi that they just prefer to say lighting in human magic which does not exist as there is no such this as supernatural powers.

 15. It’s good a idea to kill those witchcraft her, just leave them them those guys, they know how to punish witchcraft.

 16. It’s good a idea to kill those witchcraft her, just leave them them those guys, they know how to punish witchcraft.

 17. kndi anthuni mmati atumbuku amazikweza okha nanga awa ophanawa ngati ngombe sorr malawi dziko lalowa chijoka satana malawi dzuka ona anhu ako akufa ndi njara kuphana anthu okhaokha ufiti mafumu akupezeka ndi ziwalo za anthu amuna kukwatira okhaokha akaza okhaokha mvula ikuononga zithu.ambuye thandiza amalawi ife tilikakasi tasowa chogwira ambuye.

 18. kndi anthuni mmati atumbuku amazikweza okha nanga awa ophanawa ngati ngombe sorr malawi dziko lalowa chijoka satana malawi dzuka ona anhu ako akufa ndi njara kuphana anthu okhaokha ufiti mafumu akupezeka ndi ziwalo za anthu amuna kukwatira okhaokha akaza okhaokha mvula ikuononga zithu.ambuye thandiza amalawi ife tilikakasi tasowa chogwira ambuye.

 19. Vuto la amalawife nkutengeka. Timatengera zinthu pamgong’o. Bwanji osapeza anu mankhwala odzitsirikira? Bible likupweteketsani popeza mzungu amadalira mfuti. Ife anthu akuda chitetezo chathu ndi nyanga.

 20. Koma abale kulakwa kupha anthu osalakwa eish.apolice chonde ndikukupemphani anthu ten mwawagwirawo asakhale kundende moyo wao onse ai koma mungowapha ndi BOMBA basi.

 21. I hope mchiyani kodi amalawi ndiimvera pa internet kudzera pa Zodiak,ndili okhudzika kwambiri. Ndaonanso kale a president atalamula kuti amangidwe anthu opha anzawowa

 22. I hope mchiyani kodi amalawi ndiimvera pa internet kudzera pa Zodiak,ndili okhudzika kwambiri. Ndaonanso kale a president atalamula kuti amangidwe anthu opha anzawowa

 23. kodi ngati nkhalambazo zikuphedwa chakachanjala ndiyekuti tikakolora zochuluka satamba?izi zikuonetselatu kuti opanga izi alibe nkhalamba yake .usaphe malamulo amulungu akutelo nanga inu bwanji????

 24. kodi ngati nkhalambazo zikuphedwa chakachanjala ndiyekuti tikakolora zochuluka satamba?izi zikuonetselatu kuti opanga izi alibe nkhalamba yake .usaphe malamulo amulungu akutelo nanga inu bwanji????

 25. Mfiti ndi zomwe zapha azigogowa,mfiti zotheratu.may God forgive them apangazi ndi malaulo kwambiri ndipo ndi zinthu zozizilitsa thupi.Akanadziwa kuti moyo ndi chinthu chamtengo wapatali sakadataya miyoyo inayi mwa kamodzi.ndangozizidwa ine……..

 26. Mfiti ndi zomwe zapha azigogowa,mfiti zotheratu.may God forgive them apangazi ndi malaulo kwambiri ndipo ndi zinthu zozizilitsa thupi.Akanadziwa kuti moyo ndi chinthu chamtengo wapatali sakadataya miyoyo inayi mwa kamodzi.ndangozizidwa ine……..

 27. Nanga mafumu anali kut mmene nkhalambazi zimaphedwa? Nkutheka anthu anatopa nazo inu utsi sufuka popanda moto. Mfiti zilibe chisoni, nanga nkhalamba zina bwanji sanaziphei? Izozi nkutheka zimazunza kwambri thas y azipha, chabe alakwisa akanayamba azidzudzula kae b4 kuzipha.

 28. Nanga mafumu anali kut mmene nkhalambazi zimaphedwa? Nkutheka anthu anatopa nazo inu utsi sufuka popanda moto. Mfiti zilibe chisoni, nanga nkhalamba zina bwanji sanaziphei? Izozi nkutheka zimazunza kwambri thas y azipha, chabe alakwisa akanayamba azidzudzula kae b4 kuzipha.

 29. CID Mwanza beef up CID Neno and arrest them pliz mbuli zimenezi should feel the pinch remand them fast to maximum prison and docket for perusal fast agalu amenewa eti,ndiye bwenzi tili ndi old people

 30. CID Mwanza beef up CID Neno and arrest them pliz mbuli zimenezi should feel the pinch remand them fast to maximum prison and docket for perusal fast agalu amenewa eti,ndiye bwenzi tili ndi old people

 31. Okey’Mwana wamwalira mosaoneka bwino chabwino’ pamenepo anthu am’mudzi;boma, Dziko komanso mabugwe aluza.Okey,ndiyeno mukupha enanso anayi why? how great lots like that? mukupanag vuto ndi vuto kuphatikiza = njala ; insufficient rains.Cashget etc
  ooh my God mtundu wangawe bwerera. Takumbukira za sodomu n Gomos

 32. Okey’Mwana wamwalira mosaoneka bwino chabwino’ pamenepo anthu am’mudzi;boma, Dziko komanso mabugwe aluza.Okey,ndiyeno mukupha enanso anayi why? how great lots like that? mukupanag vuto ndi vuto kuphatikiza = njala ; insufficient rains.Cashget etc
  ooh my God mtundu wangawe bwerera. Takumbukira za sodomu n Gomos

 33. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk Malawi woyeeeeee!!! Zisweke basi

 34. Kodi inu anthu aku neno bwanji osawatumizira mphenzi apolisiwo?Iyitu ndi njira imodzi yabwino kwambiri yowadziwtsira a president kuti kono ku malawi ufiti ulipo.This is a good time to strike

 35. THAT IS RIGHT TO TAKE ACTION WHAT ABOUT ISSA NJAUJU WAS BURRIED IN PRESIDENTAL VILLAS BUT THEY PRESIDENT DIDNT SAY ANYTHING THAT MEANS HE KNOWS SOMETHING BUT YOU MUST KNOW MZIMU WAMUNTHU UKAKWIYA YOU WILL SEE LOTS OF CALAMITIES IN LIFE

 36. Mukasunga malamulo anga ndikuwacita mudzalandila mvula ya nyundo ndi munthawi yake ,ndiye inu mukulimbana ndi anthu mwaiwala kuti mulungu ndi amene amagwetsa mvula bwanji mukanagwirizana zokasala kudya kuphiri ndikupemphera zolimba muone ngati mulungu sakuyankhani

  • That’s different we are talking about behaviour of human, and you know that the educated one is differ with uneducated person. Most people who like to believe in witchcrafts they are not educated.

  • Prisca M Boysen That’s not completely true. Witchcraft is a cultural thing. Some are from university and some of them believe in witchcraft and some practice it. Many consult witchdocters or traditional healers to protect themselves from witches. Witchcraft has been there for ages and it will be there forever. It is the power of magic. Unfortunately some witches use this power of magic in a negative way. Some use this magical power as their religious belief. Prayer is powerful as God is more powerful than witches.

  • Are you sure about religious belief? What kind of religious is that? But witchcraft will never protect someone. And that’s true God is our protector in every situation.

  • Lydia it pains me alot I lost my father because of these people panopa ndalama ndikungodya popanda bambo anga stupid people aziphedwa so that there friends can stop practicing ufiti

 37. Umbuli ndimatenda ndithu , who said munthu akakalamba ndi nfiti?,God have mercy may their souls rest in peace, mwawalakwira anthuwa

 38. Anthuwa2 ndawatulukila nzeru zawo nkhani yavuta kwambiri ndi Njala,akupalamula dala milandu kuti akakhale ku Jail,kuthawa Njala.so what can we say to our fellow malawian? Its true…Hunger too much!!! Azikadya zaulere.

 39. Kodi Apolice Aganiza Bwanji Ngati Alindiomboni, Ngat Akufuna Amange Mzi Onse Coz Sakuziwika Kut Ndiut. Izi Zingopitilila Mizi Yese Mzko Muno Zingakhale Bo Mwina Ndikukhalako Zikolopanda Afiti Kkkkk

 40. Kodi Apolice Aganiza Bwanji Ngati Alindiomboni, Ngat Akufuna Amange Mzi Onse Coz Sakuziwika Kut Ndiut. Izi Zingopitilila Mizi Yese Mzko Muno Zingakhale Bo Mwina Ndikukhalako Zikolopanda Afiti Kkkkk

 41. Amalawi tiyeni tichangamuke, zimene tikuchitazi tikuphunzitsa ana athu tisadzadabwe nafe titakalamba akutipangila zomwezi

 42. Amalawi tiyeni tichangamuke, zimene tikuchitazi tikuphunzitsa ana athu tisadzadabwe nafe titakalamba akutipangila zomwezi

 43. Zonsezi ndi bodza la asing’anga kudanitsa pankhomo basi munthu ukakalamba wachimwa? Amangeni mwatsekere makiyi mukataye kunyanja

 44. Zonsezi ndi bodza la asing’anga kudanitsa pankhomo basi munthu ukakalamba wachimwa? Amangeni mwatsekere makiyi mukataye kunyanja

 45. zakhala bwino fitizina zitengelepo phuzilo mwina otsalawo angamawope zitsilu zaathu afitinu mese mati mumatamba dzukani tikuwoneleni

 46. zakhala bwino fitizina zitengelepo phuzilo mwina otsalawo angamawope zitsilu zaathu afitinu mese mati mumatamba dzukani tikuwoneleni

%d bloggers like this: