The Football Association of Malawi (FAM) has announced that the 2015 Standard Bank Knockout Cup final between Civo Service United and Mighty Wanderers will take place at Civo Stadium on 1 November.
According to information made available to Malawi24, the organizing committee has decided to take the finals back to the Capital City, months after hosting another cup final involving Blantyre sworn rivals Big Bullets and Mighty Wanderers.
This means that Kamuzu Stadium will not get involved in any cup final in the on-going season despite being the best stadium the country has so far.
The last time the Stadium hosted Standard Bank Cup final was in 2008 between Bullets and Moyale Barracks. Civo will play host to Wanderers in the match.
This will be the third time for the two teams to reach the finals of the cup, with the Nomads winning twice whilst Civo are win less in all the attempts.
Nomads nd mooo!.. pa Civo ndpa home no pressure,Cup ndyathu BLue end white army.
Kod ku Malawi kunonxo kuli ma club a mpira??? Ine xndmadziwa, kod mexa ku Lilongwe nkwa gule bax?
bullets kukhala ngati olima fodya ndalama amadya kamodzi pa chaka kkkkk
zachamba. Mzuzu bwanji?
Akuti Noma sinapezeke point mu 2nd round ndizoona koma,,moti ikungogawa ma points
kuwina olo osawina ife a Noma tasangalala civo timalandila ulemu kusiyana ndi ku mudzi kwathu ku BT kotero ife ndiosangalala ndi maganizowa .
noma yomweyo kuti wawawa
Ma game a mbuli ndi choncho
Ndizoona pali nyanga
yea this is very good cz we the nomads know slready our home ground is civo stadium,,,and not a congusing thing that we havent lost any game at civo stadium ndipo we always win with a single goal viva manoma
Nomaa! Team Yangaaaaaaa Kkkk None Is Bad. Koma Tinjoya Mpaka Tikhala Ndi Dzipanda Ziwiri, Eeesh! Mulungu Mngwabwino Anthuni Uyu Mwe.
Akuwopesa mbuli za ma surporter a team ina yake chifukwa ndi a Nsanje kspena kuti akaduka
all the best noma
manoma pa L C ndpakwathu mulungu akhala mbali noma
Noma Itenga Standard Cap
Paja lilongwe ili mdziko lanji?Nkhawa ndlibe pasport kt ndpte nawo kma Nyerereeee indionesa dzko lachlendo bwanji L City nd kawawa ndmangoona pa news paper.
Zimenezo Ndi Zanu
Everywere we go to us we are lyk playn at home coz bwalo lamasewelo palokha cant play futbo.so ku L city nyelele zikubwela kuzakoka zindalama za std bank.
home ground yathu imeneyo ndasangalara heavey,masikwano civo ikumatotora pa kamuzu ndipakwawo agaluwa ife nyelele home ndi lilongwe mboni neba
Kuba komanso kumenyana zazii zampira ngati izi…BT fans kuchuluka mbuli asasamba!
wth the comin of bingu stadium n lcity BT iwalani lcity more fire akufuna muzolowerere2 ok?
Iyaaaa!!!! zilibwino ku Lilongwe koko.cz pa Kamuzu aBullets anakhwimilapo ndizowoona!! ife Anoma sitimawinapo.
kaya ndiye neba wakwera iti
kaya ndiye neba wakwera iti
kkkkk koma Noma ine aaaah kkkk
akamati awo awa ndi ma savage mwawona akhala choncho nchifukwa namaso imawathaes kupita ku Balaka
akamati awo awa ndi ma savage mwawona akhala choncho nchifukwa namaso imawathaes kupita ku Balaka
Mesa a bb anakhwimirapo?
Ife akumwela tnapanga chsankho chomangira stadium anthu apakat ,chowapasa captal city ,parliament kt mwna akhale anthu ozndkira nde osamadabw akamat finals il ku civo.
you robed us our university nchifukwa pakusowa madzi mukhaula
Muzndkir osadand
musanati mulira tikatsekulira yatsopano ija
Zilibe Kuti Pano Mpakwawo Paliponse Nyerere baaasi.
Nde tikatsegulira #Wembley Stadium Ku Area 49
Achita bwino ku BT kuli anthu amaluz kwambiri
Go konko ku LL! All the way from Mzuzu. atifupikitsira mtunda
btz cashgate bola pa civo pomwepo!!!
Bt Kuba Too Much Za Pagate Anthu Akeso Ku Vencha Kwabasi
Aisova
ku Bt kuba too much
I hate mouth gamez lets go on the pitch
ukufuna kuti tizinena kuti tikaluza?
Neba anaikapo nyanga
Civo yomweyo kuti wawawa! Umva bwanji neba?
wa ziiii.mpira sitimenya ndi pakamwa
paliso kamwa liku sewera mpila apa
Koma neba sanzatheka eti akukwera @civo yoti idawaphuntha kale kakakakakaka @neba nsanje.com
Inuso inakupunthani kale anapezapo.3points painu
Kodi bwanji ma results a gotv netball championship simukuyikapo. Tifuna ma results. Kukondera soccer eti
Kkkkk Neba Kugenda Kwambiri Ku Mastand Kwako Kkkkkk Usova Ubwele Ku Lilongwe Kkkkkkkkkkk Neba Kukonda Kuvencha!!!! #Mahulle Bullets
Waganyu akalilenso kuti nthiiiiiiiii,pa Civo ndi pa Home Ground pathu,,,,Mtima mmalo Nyelele
Zilikhengee pa Civo pomwepo kuti wawawa Manoma omwewo kuti wawawa
Ndikukufunila Neba Zoipa zonse!
Fans from Btz you’re not patriotic ndima player anthu, kuba ndalama zapa gate 2 much…ndiye Noma pa civo simaluza, kaya Uisova iwe wamahule bullets…#noma4Life
Apa Ndiye Zili Boo,aa Abale Inu Titengenso Standard Bank Cup Koma Iweyo Neba Zako Zinaipa Kale Watsegulira Kuluza. Go Noma Go Nyerele Koma Manoma Aaaaaaa
Bas titengaso chikho chija kkk
Wakwera yomwe inakuphayo.ndiye ukusangalala
Everybody knows that bibi have spoiled the stadium. It is producing foul smell
Ndiye tikasololera Ku CIVO? Sha! Zandinyasa kwambiri.
Zili boo neba amatilodza pa Kamuzu
standard bank u have done good nyerere woyeeee
btz kuba zapagate komanso kulipira zonyenyeka kkk noma ndi moo!
Aku Bt koma zikwanje ndizimene amaziziwa mpila samausata ndipo mulira mpaka mamina simunati
Kkkkkkkkkkkkk………..neba usova……….ine ndakwera inayo! Kkkkkkkkkkk tsoka lagwera kangaude wabisala kupaipi yafuti….phoooooooo
apa ndichimodzi modzi kuyala malonda ankhumba pa nzikiti anthu aku lilongwe zampira samazisata
vuto la anthu aku btz kuba 2 much, standard bank ulemu wanu
Hahaha
You eat alot of cash failing kukonza
Thats good
good move finals be at civo
Achita bwino ku capital kuzidziwika komaso ma pale (ma venda aku ndilande) ndi okonda ziwawa angakatisokoneze GO… CIVO GO… Noma nkachaniso tidapha kale akulu awo.
iwe ngati umausata mpira udziwe kuti bullets ndi mwana amene talera tokha anabadwa kubanja la nyerere aneneuja wamva
Go konko
best??..in what way??…chinthu chot chigwa nthawi iliyonse
Kublantyreko mumanyanya kulowa ulere,nanji akatisegulira stadium yathuyi kaya mutani kaya
Civo Ndyowinawina Kale
Nyamilandu paja ndiwa noma nde pakamuzu aneba zimawavuta anazolowera kumenyera pa udzu no wonder akaxova
ngati umautsata mpira ufufuze soon carpet imeneyija akuchotsa adzala udzu wamva ndipo zama carpet zikutha even the new stadium kuno kulilongwe adzala udzu, ndikuwona wakwapuludwa kuchitowe eti kusatha kumenyera pa udzu usova neba
Kikkkkk sangachose carpet imene ija man yaku Elaz tkuziwa kale ndiya udzu mot tzakukwapuliranxo konko ungolimbikira paja uli ndi shi vep choxayamba kikkkkk neba sungamake
zili boh
Thats Not Fair To Us Blantyre Fans
Capital city woyeeeeeeeeeeeeeeeeee
Woyeeeeeeeeeeeeeeee!!
bola ku LL komweko kulibe mbava za mmageti.iwo koma ku capital hill.
Zilibwino