![Bullets](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/06/FCB-Nyasa-Big-Bullets-Silver-Strikers-235x176.webp)
SULOM ilanga omwe anagenda pa bwalo la Kamuzu
Bungwe la Super League of Malawi (SULOM) ladzudzula zipolowe zomwe zinachitika Lamulungu pa masewero a pakati pa FCB Nyasa Big Bullets komaso Silver Strikers munzinda wa Blantyre ndipo yati ilanga onse omwe apezeka olakwa. Anthu… ...