Malawi Police in Ntchisi district have arrested an Agriculture Marketing and Development Corporation (Admarc) official for stealing maize valued at K787,930 from an Admarc depot in the district.
The arrested Admarc official, George Kambwiri, 56, works as unit marketing officer for Msumba Admarc in the district.
Malawi24 understands that people around Msumba Admarc had complained to Admarc officials at Mponela that the Admarc unit marketing officer for Msumba was just receiving money from people without giving them their bags of fertilizer.
After receiving the report, an Admarc internal auditor followed up the matter and stock was carried out for both maize and fertilizer where it was discovered that bags of maize worth K787,930 were missing.
The matter was reported to Ntchisi Police Station and on Thursday police arrested the suspect but the maize has not been recovered.
Kambwiri hails from Nankhako Village in the area of Traditional Authority Ntema in Lilongwe.
Masiku otsiriza
I think atamangidwa ndi 2months basi nanga okuda 2 billion mmesa paja ndi 3 years kkkkkkk
0.8 million ndizingati
Sorry for him kuti wagwidwa. Vuto la mmalawi amagwidwa nkumazunzidwa ma juniors ma seniors akungokula mimba nkumapeza mphanvu zokabera. Tereko wina akupita kundende bwana ake akuchitidwa promoted chikhalirecho anamutuma ndi iwo.
Anaonera jb kuti ndalama za boma sumangidwa nsiyeni kkkkkkk
Cashgate imandiwawa zedi bwenzi pano nditalembedwa ntchito ndiye mpaka pano palibe chanzeru boma lachita koposa kudzipatsa mbavazi ufulu womanama mu khoti;God wu judge fairly on cashgate!
AGalu amenewo amangidwe basi
Well done police in ur job
Admarc ndi anthu ake ogwira ntchito anali okhulupilika mbuyomu nanga pano bwanji? Muzifunse
Thom, kodi ngati akuti munthuyo wagwidwa atinso katunduo wapezeka ngati?
Godfrey, u know ngati Boma sili lokhudzidwa ndi ulamulo wake oligwilira ntchito ngakhale anthu wamba saliopa sure!
Mwa masiku apasidwa chilango koma cashgate up to 2 years no judgement
Ameneyo akanandiwandikila ndikanammenya kwambiri. Ino sinthawi yokuba ma thousands Ayi ino Ndi nthawi yokuba ma million kapena ma billion .
Zili kuMalawi..
Amangeni agalu amenewa amene akuononga ndikufuna kupha mizimu ya a Malawi
Amangidwe musanyengelere akuzolowera kuba mwina ena atengeleko phunziro
Amangidwe musanyengelere akuzolowera kuba mwina ena atengeleko phunziro
Ameyo kundende zaka 100 akusaukisa boma la malawi
Boma lilibe chitetezo!
Ngati boma lilibe chitetezo ameneyo wagwidwa bwanji? Kkkk
Mwati ikupelewera K70.00 ?kkkkkkkkk
Osangolemba kuti k800,000.00 bwanji?
Why?
akanangolemba kuti K800,000 osati kulemba ngati inakwana Million.
F**ck him anthu akuvutika ndinjala ameneyo khumabanso akuganiza kt athu apangezotani aphedwe bas ameneyo galu u mather f**ck
kunonso ku mzimba bwerani muzamange
Wakubayo asabeso koma kuti anyongedwe monga mwa kulakwa kwake
Leave them coz stealing kumayamba ndi bomali
Aaaaaa basi????? Zachepa sakupanga qualify kupita kundende ameneyo
wausiru,amangidwe basi
Siinakwaneso K 0.8 million ikupelewela 70 kwacha
Kkkkkkkk mesa to the nearest whole number!
Steals k 0.8 million worth. bwanj akanat at least k 0.8 million udaona bwaaa
better sale admarc!
Ibani chomeni ise tifwenge nanjala nthennanthena.
Ikamatha 48hrs akhala atatuluka musatipusitse apolice mwava!.
Malawi @ 52
Aliyese amaba mu department yomwe amagwira ntchito just that ogwidwa ndiwochepa
Musiyeni inu, mbuzi imadya pomwe yamangilidwa.kkkkkk.
aresting coz of k0.8 million but ur falling to arest bwampin, folish malawi police
Arresting whome? for what? Wtf wasted sperm,
Akawolele ku ndende komko. Njala, nthenda ndi msanje sizidzatha ayi chifukwa cha anthu amenewa.
shupiti zake!!!!
Amengeni ndipo musawapatseso bail
don’t let him out
Jail that dog!
Ife ophumzira ife! inu mukuvaya ku Joni ndinu makape, while this has been the life for most officials in Malawi.
Dpp yr so thiefs
Atate, palibe kugwilizana kulikonse pakati pa official wa admarc ndi Dpp
Bt admark belong 2goverment
Akumatuluka Pabelo
Any Number aftr decimal point is regarded as 0,so they stolen about K0.000 Million kah??
Like serious?well I can’t put blame on you but yo fucken teacher if am not wrong,
Haven’t you held of tht?? Conel Q Hammissih well I can see You r underfive guy,there’s no wei to insult
Haven’t you held of tht?? Conel Q Hammissih well I can see You r underfive guy,there’s no wei to insult
Mmangeni and tisamveso za bail, komaso apolisi afufuzibwe, kamba koti chimanga chosecho sichingabedwe ndi munthu mmodzi.
Adayamba siiye koma kulikulu. Mtayeni Ameneyo
amangeni inde