
Polojekiti yalimbikitsa uchembere ndi ubereki wabwino pakati pa achinyamata
Achinyamata okhala m’madera a mafumu akuluakulu Amidu komanso Kalembo m’boma la Balaka ati tsopano ali ndi mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana okhudza uchembere komanso ubereki wabwino, zomwe akuti zapititsa kwambiri patsogolo miyoyo yawo komanso maphunziro awo.… ...