Nyerere zija azisasantha, azisambwadza ndi kuzisiya kukamwa kakasi
Mankhwala a nyerere adziwika tsopano, ndi fodya wa Nyasa. Nyerere za manoma zachoka pa Bingu National Stadium zikulila chokweza, a neba awo a Bullets atawatibula masana dzuwa likuswa mtengo. Pa masewero amene anakodola khamu, nyerere… ...