
Kulibe chipatala cha Namiyasi ku Mangochi – Kingstone
Phungu wa dera la pakati m'boma la Mangochi, Victoria Kingstone, watsutsa kwa ntu wa galu zomwe wanena mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera, kuti boma lamanga chipatala cha Namiyasi. A Chakwera anafotokozera Nyumba ya Malamulo… ...