
Chitetezo sichilibwino ku Nyumba ya Malamulo
Dzulo anthu ena omwe akuganizilidwa kuti ndi a Malawi Congress Party (MCP) anabowola mateyala a galimoto za a Phungu achipani cha Democratic Progressive (DPP). Lero mu nyumbayi aphungu a chipani cha DPP adandaula kuti chitetezo… ...