Kenani ayamikira boma kamba kachitukuko cha nseu
Kwa nthawi yaitali nzinda wa Lilongwe wakhala ukutchedwa ‘nzinda wa fumbi’ kamba koti uli ndi misewu ya fumbi koma pano, fumbi litha kukhala mbiri yakale kamba koti boma likumanga misewu mu nzindawu. Kudzera patsamba lawo… ...