![Pemphero Mphande and a Malawian musician received fake honorary doctorates](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/11/Namadingo-Pemphero-Mphande-235x176.webp)
Azibambo atatu onyenga! UNISA yawakana a Pemphero Mphande, a Karim ndi a Namadingo
Kaya mwina pano tiziti Mr anavaya, kapena chabe kuti atate anavaya? Chifukwa ati za doc anavaya zija ndi za ukapilikoni basi. Utambwali wa masanasana. Komanso pali nkhawa pang'ono kuti kodi nkhani amalemba Mr P, hiii… ...