Musamange mahule – Khoti liuza apolisi
Apolisi a vakabuali pa chi ntchito choopsa pamene alamulidwa ndi a khoti kuti asiyiletu mchitidwe omanjata azimayi oyendayenda usiku ati chifukwa kutelo ndikuwaphela amayiwo ufulu komanso ndikulakwila malamulo a dziko lino. Malingana ndichigamulo chimene khoti… ...