Joshua Malango ndi aphungu aboma sakufuna Suleman
Phungu wa boma la Dedza cha ku m'mawa a Joshua Malango limodzi ndi aphungu a mbali ya boma m'nyumba ya malamulo agwira pakhosi phungu wa DPP a Sameer Suleman kuti awachotse pa udindo wa wapampando… ...