DPP sikanawina popanda ine – atero a Chilima
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ati iwo ndi omwe anapangitsa kuti chipani cha Democratic Progressive chipambane zisankho za m'chaka cha 2014 ndiye chipanichi chisiye kuwasokosa. A Chilima ananena izi dzulo pomwe… ...