
Kwelepeta wadandaulira boma kuti litsekule chipatala cha Domasi Community
Nyimbo yoti chipatala cha Domasi Community m'boma la Zomba chitsekulidwa yakhala nyimbo yomwe yalira motopetsa. Phungu wa dera la Zomba Malosa a Grace Kwelepeta omwe lero mnyumba ya malamulo apemphanso unduna wa za umoyo kuti… ...