A Malawi ayembekezere nkhani zakathithi zakunyumba ya malamulo
A Malawi ayembekezere nkhani zakathithi komanso zothyakuka bwino zokhudza zokambirana komanso zomwe zimachita m'nyumba ya malamulo pofuna kuonetsetsa kuti anthu m'dziko muno akutsatira bwino lomwe za momwe zinthu zimayendera m'nyumbayi. Izi zikudza pomwe bungwe la… ...