MCTU, ECAM athandiza achinyamata kupeza maphunziro a ntchito za magetsi a mphamvu ya dzuwa
Ngati mbali imodzi yotukula achinyamata pa chuma m'dziko muno, mabungwe a Malawi Congress of Trade unions (MCTU) komanso Employers’ Consultative Association of Malawi (ECAM) ati akonza ndondomeko yophunzitsa achinyamata 800 kupeza luso la ntchito za… ...