2019, tikuyambapo ntchito yokonza zonse waononga Mutharika – atelo a Chakwera
Ati a Mutharika ndi chipani chawo cha Democratic Progressive (DPP) agwilira dziko lino. Aliveka manyazi. Kuliyamwa kalikonse ndi kulisiya mbu. Lokhuta ndi umphawi. Koma a Malawi musadandaule, chifukwa ati a Chakwera ndi chipani chawo cha… ...