
Julius Mithi apata shuwa
"Khaaa kuti khaaa.."Julius Mithi apata shuwa pomwe ma loya odziwika bwino mdziko muno a Silvester Ayuba James ndi a Khwima Mchizi ati akayimilira mwa ulele a Mithi omwe awamanga dzulo mu mzinda wa Mzuzu. A… ...