Kuno zautchisi zanuzo ayi: bwalo likana mathanyula ku Malawi
Pomwe ena anali ndi chiyembekezo kuti adziyenda shosholo mtaunimu komanso kupanga mathanyura momasuka, pemphero lawo lawomba mgolo pomwe bwalo la milandu lalamula kuti mtchitidwewu ndiosaloledwa kuno ku Malawi. Lachisanu silinali tsiku wamba, koma lomwe linabweletsa… ...