Chiwerewere ndi tulo ndizo zidzetsa chimwemwe – atelo akadaulo
A kadaulo a zofufuzafufuza a ku sukulu ya Oxford mu dziko la Mangalande ati tsopano apeza zinthu zodzetsa chimwemwe pa moyo wa munthu. Ndipo ati si makobili ayi. Malinga ndi tsamba la nyuzipepala ya Telegraph… ...