
Nyumba za Adam zikunyasitsa mzinda wa Zomba – zatero mzika zokhudzidwa
Mzika zina zokhuzidwa zaloza chala m'mwenye ochita malonda a H Adam kuti nyumba zake zikunyatsitsa mzinda wa Zomba popeza ndizosawoneka bwino. Patrick Gama yemwe amachita bizinesi yokonza foni zowonongeka wati pali nyumba zina zomwe zili… ...