Tichita Zionetsero m’mabwalo a ndege – HRDC
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu m'dziko muno lomweso akuluakulu ake ndi omwe akutsogolera zionetsero la HRDC lalengeza kuti zionetsero ziyambilaso pa 27 mwezi uno zomwe ati zichitikira mu zipata komaso mabwalo andege a dziko lino.… ...