
GVH Makungula akuyimba lokoma chifukwa cha ng’ombe za mkaka komanso nkhuku za mazira
Mfumu Makungula a mdera la T/A Nkagula Boma la Zomba akuyimba lokoma pakhomo pawo chifukwa akupha makwacha ndi ng'ombe za mkaka komanso nkhuku za mazira zomwe amaweta. Poyankhula ndi Malawi24, GVH Makungula adati alindi ng'ombe… ...