
A Malawi valani zilimbe magetsi akwela ndi 16 pelesenti
Pomwe a Malawi ambiri akukhala movutika malinga ndi kukwera kwa katundu nayo bungwe logulitsa magetsi la ESCOM laganiza zokweza mtengo wa magetsi ndi 16 percent kuyambira lero. Malinga ndi kalata yomwe bungweli latulutsa, kukweraku cholinga… ...