![The Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) says about 7,000 have been displaced by flash floods following heavy downpour in Nkhotakota and Karonga Districts.](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/02/Floods-Nkhotakota-276x176.webp)
Namondwe Filipo wabwelera safika kuno, mvula ya mphavu ipitilira- atelo a za nyengo
Pomwe panali chiopsezo choti namondwe otchedwa Filipo atha kufika kuno ku Malawi, nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo m'dziko muno yati namondweyu tsopano wabwelera ku nyanja ya nchere ya India komwe anachokera, komabe yati… ...