
Anthu ena akungofuna potchukira – Mponda
Mphunzitsi wa FCB Nyasa Big Bullets wayankhulapo pa zomwe zakhala zikumveka m'masamba a m'chezo kuti katswiri watimuyi wapakati, Lameck Gamphani akufuna kuchoka. Poyankhulapo pa msonkhano wa olemba nkhani mu mzinda wa Blantyre Lachinayi, Mponda wati… ...