Mtsogoleri wa dziko la America Joe Biden wapezeka ndi Covid-19
Mtsogoleri wa dziko la United States of America, Joe Biden amupeza ndi Covid-19 Lachitatu. Izi zikudza patangodutsa nthawi yochepa chabe mtsogoleriyu chinenereni kuti sazayimira nawo pa zisankho zili mkuza ngati madotolo adzamupeze ndi vuto lalikulu. … ...