
Oganizilidwa pa milandu yakupha adzitengeledwa ku khothi mwansanga – Kaiyatsa
Mkulu wa bungwe loona za ufulu wa anthu la Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR), Michael Kaiyatsa wapempha anthu m'dziko muno kuti apewe m'chitidwe ophana ponena kuti aliyense ali ndi ufulu okhala ndi moyo.… ...