Kodi oyimba akwathu kuno adzasiya liti kuyimbira a Malawi okha okha akapita mayiko akunja?
"Pena vuto ndilakuti oyimba aku Malawi amakakamira kuyimba ngati akunja komweko ndiye anthu akunjawo zimangowamvekera ngati za kwawo komweko, ndi chifukwa zili zovuta kubooleza," anatero Ben "Michael" Mankhamba. Anaonjezeranso kuti vuto lalikulu lirinso ndi anthu… ...