
Akufuna ndithu wina aphedwenso – watelo Chihana
Mtsogoleri wachipani cha Alliance for Democracy (AFORD), Enock Chihana wati satekeseka ngakhale kuti anthu ena akukonza chiwembu chofuna kuchotsa moyo wawo komanso ena ochita nawo ndale. Chihana wayankhula izi pomwe anthu ena omwe sakudziwika agenda… ...