Owina Lotto agula nyumba ndi galimoto
By Gracious Zinazi Mdala Mkwinda wa zaka 57 yemwe anapata 45 million kwacha chifukwa analosera molondola ma nambala folo mu Premier Lotto wagwiritsa ntchito zina mwa ndalamazi pogula nyumba ndi galimoto. Iwo agula nyumba yapamwamba… ...