Bungwe lowona za zisankho la Malaŵi Electoral Commission (MEC) lanenetsa kuti kuyenda bwino kwa  zisankho zapatatu mu 2025 kudalira kuti anthu amvetse bwino ndondomeko ya kayendetsedwe kazisankhozi. M'modzi mwa makomishonala a bungweli, Dr Anthony Mukumbwa,… ...