M'mbelwa speaking at an event in mZIMBA
Mfumu yaikulu ya angoni  ku chigawo chakumpoto Inkosi Ya Makosi M’mbelwa Ya Chisanu yayamba yaimitsa kaye mafumu asanu kamba kothandizira kuwononga chilengwe. Mfumu Mbelwa yayankhura izi pa mwambo wobzala mitengo womwe unachitikira pa sukulu ya… ...