
A Bon Kalindo omwe amachititsa zionetsero lero mu mzinda wa Blantyre apempha boma kuti likweze malipiro a anthu ogwira ntchito m’boma ndi K50 pa K100 iliyonse. A Kalindo, ati ndichitonzo kukweza malipiro a ogwira ntchito… ...