Malawi Police in the commercial city of Blantyre have arrested a man and a woman for having sex in a vehicle at a public place.
The two, Timothy Bonzo 29 and Liz Banda 23, were caught at it in a Toyota sprinter registration number BP 4009.
Confirming the development to Malawi24, Blantyre Police spokesperson Elizabeth Divala said the incident happened in the early hours of Sunday.
“The two were having sexual intercourse in a vehicle at Zodetsa bottle store around 03:30 hours,” said Divala.
The two are yet to appear before Blantyre magistrate court to answer charges of idle and disorderly contrary to section 180 of the penal code.
Bonzo hails from Mfera village, Tradition Authority (TA) Katunga, Chikwawa district while Banda comes from Chafilama village, TA Juma in Mulanje district.
Minority rights
Freedom
i cnt c any problem.lol
Zakudazo zimachitika ku Zodetsa Bottle store?
Kkkk asova
Vacab yongopangira mu mabar m’ma location mayazi. A police angofuna kuipitsa mbiri ya Timo coz anakana kuapatsa ndalama.
Paja mumakonda kuauza anthu kuti azipulumutse okha mix maluzi kumachita kusowa yogulila chibuku fountain kapena kugula uniform yamwana ku school. Ntchito zinazi abale! Kkkkkkkk!
owky…now let them go plz
haha iiiiiii koma kumalawi mwasowa chochita ndithu malo momateteza athu mziko muli bizy kugwila athu axigololo haha apolice akumalawi mukudya dollar zama halakkk
They deserve punishment
Is This Picture Taken From Inside A Car?It Was Not Yet Morning And Obviously The Police Wanted To Steal Inside That Car And Fortunately They Found Job Inside!!!Wow
It z unlawful to have sex in a public place, even if u r a married couple, BIG UP OUR MEN IN UNIFORM
Za zii mesa sexual feelings was stronger nde mmati atani anthu
Tsono munthu atakhala kuti Ali ndi akazake, pa galimoto, nde atopa akufuna kugona koma alibe Ndalama yolipilira Ku nyumba ya alendo. Nde angoganiza zogona mgalimotomo, nde asapange mwambo wa ubatizo mugalimotomo?
Utsiru wake ukakamakhala umenewu, wankhani zabodzawu, ndiye mungonena. Mutha kundionetsa khomo lotulukira.
apolisi mwatotani
Palibe vuto apa nkhani yomangila munthu iyi
Hahahahahaha! Analibe kwacha madolowo
Osawasiya bwanji galimotoyo anatenga yanu?
Zamkutu
No body z above de law….ngat walakwisa amangidwe basi..
nyele ilibe kudikila pa air nd zotheka
Auze ndiiweyo monga samachita
koma zimenezi
Hahahahahahaha. That is very good Malawi24. Let us have a break away from politics!
anakanika kupeza ofesala mpaka anakasuzumila kkk
Koma inuyo kumakwerana kuseri kwa building kkkkkkkkk
Sex Rights ooooo yaaaaaaa
Never knew that’s an offense, go around pubs that’s what we are doing all night long
did he enjaculate?
at night.
Nosese!!!!!!!!!!!!!!!
Mongokumbusana. MALAWI (1) TANZANIA (3)
Usilu basi
Abale wen nature calls u have to asnwer…. Jst dnt answer in car lol
inuo apolice galimotoyo inali yanu?Anthu amapanga mu church,tamasuleni,inuo mukuona sitimakuonani ,vindele imwe .
mmmmm dziko lathu kuyaluka
mmm dziko lathu kuyaluka
Mulilongwemuno inu apolice mwakhala mukupanga ma roadbrk adzidzidzi usiku koma palibe chimene munauzapo ntundu wamalawi kuti mwagwila,koma pafupifupi dairy usiku mukunka mutseka miseu nkumati mukupanga chipikisheni……shupt zanu…kuba basi,inu mugalimotomo munawaona bwanji?
Anthu opusa ndio amavera ndkukhulupilila amalawi 24.anthu angamakwerane chotani kunsi kwakafamily car ngat kmeneka,sndlo bodzalo limenelo?musawade apolice coz of ur false stories.apolice akwathu kuno amagwila ntchito yao mwachilungamo. Zachamba zanuzo osadzaikaso mwanva?
Early hrs bt inu kuwanjata aaaah sibho
good development
kukanika kugwri akuba kumagwra funz ngt imeneyo mesa nchimo ndlao apolice apamalawi kuvets chison
Malawi 24 ngat mukumasowa zolemba muzkaphka kachasu!
Hahahahaga koma pa mpanje adha pali chifukwa chowamangira anthu wa apa Mmmmmxxxxieeeewwwww
hahahahahahaha kd m’vehicle ndi public?zodelera baxi,no vuto here
A police jealous too much
Azikagwira mbava
Alangidwe basi
did they enjuculate?
Malawi 24 full of false stories
Analephera kugwira a cash gate akulimbana ndi zibwenzi za anthu.
Amenewo akayankhe mulandu ndithu sanazisungile ulemu pachikhalidwe chathu guzs olo cash yavu
Maresthouse samawawona mxieeeeeeeew
Nanga bwanji sitimamva kuti apolisi agwira anthu patchire kapena mu office? Nchifukwa chiani police yathu imalimbana kwambiri ndi magalimoto? Kodi tinene kuti milandu yeniyeni ikusowa?
Apa ndipa ntchire inu
Apolice u are disgrace umbanda onseu ukukanikani mukalimbane ndi akuluakulu ogwirizana mugalimoto yawo usiku eeeshi u dissapoint me
mwanyanya mpaka kugwira munthu nkhani yake imeneyi kusowa tchito eti.
Disclose of their names pliz
simuchita manyazi mukamanena zaboza nanga umu ndi m,galimoto? ngati mwatha maplan muzikalima kumudzi minda ya azgogo anu aja ikukudikilani
W a trying to stop pornographic movies for our childrens sake n u a hea bringing pornography to de streets.shame n u. .achita bwino aku kwizingani
Mmawa ndi iwe siukut nd mulandu ? kkkk
Ana apachire samaona cholakwika kapena samaziwa tanthauzo LA public place a police agwira nchito yotamandika akhoti ndi amene akagamule.
The place is privacy!
Mbuli Inu A Police Amamanga Aliyense Amene Waphwanya Malamulo Mukuti Chani Ankhandwe Inu Bravo Our Police
Gayz tizikhala ngati tinapita ku xool pa brick prence ndimalo osaenela kupanga zopusazo ngakhale anali munjale ife timamangabe basi coz sana zisungile ulemu
Thats being stupid,,,were thy disturbing anyone’s peace?… idnt blame you…
thats why apolice ku malawi simupatsidwa ulemu cox ua always busy with stupid thngs… you #guys_sucks
love in tokyo
enanu muziyendako muziona zomwe zikuchitika mmaiko anzathu.osamangothamangira kutukwana ndi ma fundoles apa. maiko enawa olo kuyenda ndi botolo la mowa mmanja osaika mu bag kapena mjumbo kukumanga.public drinking.what more sex in the calb.mukamatukwana zinazi nkumaxiona inu ozindikira. akuyenera ayankhe milandu basi.sanalemekeze umunthu. better akanaimika pa ka tchire galimoyo.ikanakhala njira ina.
Hehehe mumati asaufire shuga mtape
Mgalmoto Nd Public?
Mexa Aku Anal Mkat Mwa Galmoto?
Ndchmozmoz Mnyumba Guys Zopoira Bax
Nde kuti pamenepo ali m’galimoto?
Dziko la malawi silotsalila pauzimu ngati maiko enawo akupanga zigololo public ndiyekut akutsalila muuzimu,malawi police gwilani ntchito yanu ok ok
Guys mnali nditatota.
Sign of the times
Akukana zochedwa galimoto iliyake.
Kuleka kumanga acashget kumalimbana ndikususuzumira m’magalimoto anuwake fodya eti? Ndikuveso udziona
Bad
chopusa ndichomwe chaika khaniiapa
Kodi Galimoto Yake Ndiyamaudzu? Inutu Simunakawone Mukunama.
Malawi 24 Mbwerera.Tsono Apolice Mulipachintchito Chosaka Milandu Akuba Anatha Ku Mw
koma akanakhala iwowo!!
Padangokhala
In a vehicle ….i thought in the street…nothing wrong…it is the same as having a fuck in ones house.
bwanj anthuwa anasowa malodge kapena kulibe kumeneko, amangdwe kumene, very stupid
bwanj anthuwa malodge kulibe kumeneko, amangdwe kumene,
a
Court liyime!!
Is that in a vehicle ? Mabodza basi
wow, ma ideot.
Kuti uwelenge ma comment udziwadi kuti ndiife amalawi, apolice sanalakwitse apa
MW24 Mwasowa nkhani kodi??
M,maiko anzathu apolice sakhala busy ndizimenezi,iwo amalimbana ndi akuba komanso zigawenga koma kuno kwathu ku NYASALANDE apolice akatero amati agwira ntchito,mwinanso anthuwo anakana kupereka zam’manja paja apolice ali ndimkhalidwe omuuza munthu kuti “dzipulumutse wekha”
maiko a nzathu amalandila money syz ya bho koma kuno mayazi, tizitani unganene ndiwe
Some think that public place means ‘presence of people’ no,the issue is about the place they were @ and,not the car they were in.
Ndiye mapazi bwanji ndi anthu awa inu a police?
eee public sex amapanga ndi mkazi wamwini awo
Rubbish ! Rubbish!
Mbuli inu simukudziwa kodi kuti it’s unlawful to have sex in a public place?I say “public place!”
Mboli yamako iweyo nzelu mancheeeeeende
Mboli yamako iweyo nzelu mancheeeeeende
Ntchito za apolisi akuMalawi,zinazi zikukondwesa kwambiri.Osakagwira akuba bwanji
Apolice mukanangopanga nao.
kkkkk e koma ya!
Ngati alibe mulandu akagamula kucourt
What’s Wrong After All It Was At Night… Ma Galimoto Akumatha Mashokowa Mmesa Enawa Akuthera Zomwezo! Leave Them Alone Coz By Going Into Th Car At Night, They Were Excluded From The Public. Bwerani Ku Chez Muzamanga Anthu Mpaka Kutopa
Bodza nanga umu ndi galimoto malawi24 b serious
Kkkkkk…nkhani ya Busiri ikupezekanso bwanji apa?
Malawi @ 51
M’bale Malawi waipa uyu
A car is a private property. I also did it on Saturday but nobody can arrest me. Maybe it was a bakkie so the encounter was in the body but sedan is free for bonking
kodi inu apolice vakabu mpaka mugalimoto?
WTF is wrong there? u cops want promotion? lol
Kod inu nkhani zoputsazi mumazitenga kut,kusowa zolemba eti.
Lock them or put them in Zoo,tourism them
Akuba m’makanika aaaa fokofu
Kodi paja Ku mw ndizachilendo et kusalira
Mmmm
Prophet Shepherd Bushiri I was praying few minutes ago and I saw the soil shaking and it seemed like an earthquake. I saw many houses falling down and many lives lost. My prayer partners all over the world let’s pray for Africa. you and me can stop anything that is bad from happening. As days approaches I will tell you more in details so that we can resist it in prayer in Jesus name. Shalom
Zopusa Mwai.Bushiri anthu ovulala mu church mwake anawatumiza kuchipatala bwanji,mmalo moti awachize iyeyo awapemphelere.Kupepera
Asa! Apolisiwo anasowa chochita? Nanga umenewo ndimulandu! Mexa amapangila pawo… Nsanje ndimene inawavuta2 apa
Mwana Iwe Wachenjeretsa Masiku Ano
Luks lyk th Police aint got shits to do osamagwira ma Criminals ndi okoza mbali mwa nseu buanj, z avin Sex acrime nw
COME TO CHAPIMA HIEGHT YOU WILL ARREST AS MANY AS YOU CAN.
Malawi lol
So what?
COME TO CHAPIMA HIGHT YOU WILL ARREST AS MANY AS YOU CAN.
Mgalimotomo ndi public? Kodi a police mukumayendera yosuzumira galimoto zaweni eti?
Apolisiwo amafunamo chani munjalemo? Dyera kuba kmaso anatotedwa amenewo
anthuwa kma kkkk
hahaha thats gud newz bt isee nthng wrong fo them to get arrestd…apolisi mwabonga eti
Zaonjeza
Zaonjeza Apolice Kapena Ogwidwa?
The charge is”idle and disorderly”.Free these people because they were not “idle”when having sexual intercourse neither “disorderly”because they doing it in the privacy of their own car.Find another charge
which will hold water. There’re sharp defence Layers these days.
Anabisala Wosat Pagulu Anaxowadi Chochita Apolice Et
Kutan?
Thoz r human chickens ,no wonder mpaka mgalimoto.Nanunso ogwiran mmafuna chan mnjale yawen?
bluff
Zikumathekanso kodi eti
Uu zikuchuluka
Nde alakwa chan?
kusowa zochita apolisiwo
Shame last dys like dogs
kunyasaland aise nde akumati ndiku mpanjev
I recommend transparent cars now