Following the depreciation of kwacha in the country Carlsberg Malawi Limited has raised the price of beverages.
The increase is in both alcoholic and non alcoholic.
According to Carlsberg Malawi Marketing officials the rise is between 12 percent to 18 percent.
The two litres Sobo Squash has jumped from Mk1, 200 to Mk1,500 while the 300ml Carlsberg Green has been raised from Mk 400 to Mk450.
Minerals like fanta, Sprite and Cocacola are going at Mk200 from Mk 140.
Carlsberg official added that the rise is aimed to suit with the current situation the country is experiencing.
They cited the kwacha depreciation has hit hard on the companies cost which includes production and price for raw materials.
The rise has also came at a time soft mineral are scarce on the market despite being on high demand due to the season.
PEPSI CO & AZAM SODA BWERENI MULI OLANDILIDWA MBAVA ZA SOBO CO ZIKUTIBERA.
koma dis goverment eish plzz….ubwino wke ife timamwa masacheti
ife tizimwa juwesi ndi chibuku!
Ndamwa kale dzulo otsika
Jumped?
why katundu opangidwa kwanthu komkuno kumadura conco nanga wakuja apenga bwanji? wake up malawi
Fantayotu mtengo wake ife timagula omwewo kale :p
Wh@?……
olo mukweze mowa achina Phwiyo ndi anzake aja azitigulilabe.
Fanta from 160-180….u lie too much….mukumatenga mitengo ya Ku ma bar
Malawi shaaaaaa????
Tixikumwabe olo ukwele,wamva iwe green.
Thanks Malawi of today
No wonder Malawi walero
this z too much
Malawi walero ndi ameneyu.
Chalachanga ndinakulakwira
Mwachita bwino kukweza mtengo wa Sobo ife wathu nd Win (mkalabongo)
Malawi for sale
osadanda ula tizingomwa kacháso
Point ov collection on two litres sobo the prise is higher than it has bn indicated here its almost 2000mk
Beer prize raised? Wow! Mathematically solved ,money for relish will be deducted with 10% .kkk I COUCH BEER!
fanta ndi 180 osati 200 analiso pa 160 osati 140
2lts coke 16 rand and black label 750 ml 13 rand no need of coming bak home
2lts coke 16 rand and black label 750 ml 13 rand no need of coming bak home
Munazisankha nokha pa 20 may ndiye musalire simunati ichi ndi chiyambi, nanga mafuta agalimoto akakwera ndiye zinthu zikwera bwa, kaya ndi bwanpini wanuo.
For soft drinks its MK180 from MK160. A MK20 rise.
achina #Biliati kuchuluka problem solve #Matokonso pa malo iwe green go away wth m
Thobwa from K25 to K75
Posachedwapa muona Blue Band akusowa.
Sobo kukweza ndi 300 mowa 50 basi? Ah simuli serious
Thobwa ndi dhilu!
Kumwa kwakwera mtengo
we are complaining those prices because of poverty if we are rich we can’t complain so the thing is lets work hard and pray to God to helps us !!!
its part of reform kkkkkkk
Ndzomwe makape ena anasankha pa 20 may paja
Malawi wanga
Castle lagger amutsitsa from k600 to k400. Nde zikwezani ma green anuwo
Kukweza mowa nthawi yotentha nkulakwa
hmmnmm kumalawi sindibweraso zawonjeza
Koma eeeee!! Paka 1,500 two litter only ha haha
Wrong comparison really. Don’t you know Malawi is the poorest country on the planet?
Or zitapanga expare ngati ndizanga .ife tizisungunula juice ndikumwa
We have no money to buy soft drinks yet they raise the price
Thobwa k100 ,joly jace k50 Ndi Banks K30=K180 oky.tzmwa pa xrismas ndipa new bas
Cmon Cnto Kamanga Gift Kamanga
tifa kumene
Zili Bo Tizgula Joly,banks.Pamtenga K50
ubwino wake masiku ano sindikumadwaladwala.
ganja ya k100 imandikwana
hiki wth k300 on squash? wo! mwaonjeza heavy.
dziko Lili mmanja mwa agalu
dziko Lili mmanja mwa agalu
dziko Lili weak
(singing) divorce ine fanta wandilephera aaah aaah! Eti akungokwera mwachibwana kwinaku ma rider kutchipa aaah aaay eeeeh ndisifere dzina fanta safuna innee! Divorce ine fanta wandilephera
Fanta was not in k140 u are lie
Guyz koma,,mowawo osaukweza kwambiri cholinga an2 azichimwabe koma ma soft drink’wo ndiye kutipheratu cholinga tisiye tizimwa mowa,,,,eeish tricks of a devil
Vinu ivo ise tikupalula wa chingoni (masese) pala ukumala mbwe tikukama visika
Eee Koma Ziliko
thts better.ndie cheaptu
Ok aaa osaopaaa!!!
Koma timwaso pamenepa ooo ndebola kachaso ndi super dip apa ndi2
Kungoti dziko lathu lili rabwino mukuthandaudza chani monga ife tizingi tchona kuno bola moyo
Wachake ndi wachake we wont and cant stop kumwa coz of mitengo.even zitafika pa 200pin botolo tizamwabe mpaka kulezela olo kukhuta nakubokola chitali….
Dziko likutha ili amalawi.kkkkk
Malawi walero ayi
mai nangozo sanakweze tondondo.carlsberg,chibuku or jada kuledzer nd kumodzi.jada ayende malonda tsopano.
akuona ngati zokumwa pamalawi ndi fanta ndi carsbeg basi…..mai Ulemu alipo atichengeta ndi ma tondondo
Masachet abwelere
Malawi WA lero sopano
Ma weekend ndiye adzibhowatu. Basi tidzikangodzadzana ku Church poti kumeneku chopereka sanakwezwe!
Basi ife palibe kumwa idzi. Poti sidzisasa ndiye muli bwino koma apa ndiye game yagona.
Ife timagula kale 200 ndiye sitikuonapo vuto
Was fanta @ 140 or 160
kaya zanu izo
Kwinaku timagula 250 Coca-Cola ndiyekuti tiyamba kumugula 300 mk
Kumalawi ndekwawilila athu samwa fanta chakachake ndendi chino 2015 ameneyo athu azichitakusilila zakumwa zozizilitsa kukhotsi kamba kantengo fanta ntengo ngati wa ticheti kuphana kumeneko bwezanikomitengo
Price yoodera madzi yakwera due to forex kkkkkkk koka paMalawi… Mwina azatsitsa nthawi yamvula
Koma nde boma silikuyenda bwino mpaka size imeneyo basi anthu fanta azimwera pamatenda.dziko lathu latendere koma umphawi sikutha zinthu zikungokwera.God bless our malawi
I dont care
Kumalawi sikuzatheka basi
Bola masachet aja abwererenso nanga zinazi nkuzikwanisa mawa timvanso a landlord nawo awonera kukwera kwa fanta nyumba akwezanso kuchoka pa K20,000 kufika pa paaaaaa……………. Chaaaaaa kukhala mmalawi ndikulimba mtima
musadandaule mamember ndapeza nsika,Zuma akufuna agule Malawiyo..zisika zimenezo
Concerning Calrsberg wil quit temporaliry til the price goes down & cane or dry spirit wil b my alternative beer…minerals stay away pliz,hv been drinking jolly jus 4 so long tym..am out!
Malawi the HOT HEART OF AFRICA
zusiyana pati kundende ndi kunja kuno??
Koma yaaa,,,,What ever,,,,,Koma boma iliiii,,,,,,kaya
My malawi my land….
kufa kulipo!
bas apapa mwandipangitsa ndizingomwe veti kapena marider zokwezazo ziziwakomera ndi namakhumutcha
shaaa kachasi nde atipweteka asah
Alo mutakweza kufika pa 1000 kwacha mowawo tidzamwabe coz mowa sudula…umadula ndalama zikatha
Akanakweza mowawo kwambiri zinazo asise
machende ako ngati sumwa mowa nde likhare vuto?? wat u deserve it’s bad other pple deserve its gud
Zibag more fireeee
Kod palibe munthu wina agule malawiyo
Muxavutke nkukweza manyi anuwo, tidzimwa Jolyjus.
kaya amene mumamwa ma soft drink nu ine ndiye ndimamwa ndika dwalatu aaaaaa
Carlsberg bèers k400
Kuno fanta tikugula k180.ndiye palibe zachilendo apa.
Nde tithera kuno tu!
Kukhosi kukauma tidzingomwa madz dzimenedzo mudzimwa nokha muyisova
you mean minerals were 140?
man mwava ndemukufusaso
Kaya ine ndimamwa thobwa k50 yokha basi.
Kachaso komaso Masacheti apa ndiye amwedwa zenizeni k450.00 imeneyo ku beer hall uthakugula Veta, kukoka hule, komaso Mogo muwili ndi kanyenya zikukwana m’midzimu…,Zobelana ayi apa mulemelele payine…!!
kkkkkkkkk
Ine Ndiye Ndidazolowera Kumwa Thobwa
late update, three months has gone with these prices
Eee! Koma timwa.
Koma mowao akanasisa kufika 250 kuti tiziufinya kwambiri!!!
Boma la anthu ophunzira kkk JB ndamulira.
Kaya zanu. I do take water only
pa zed ndi k3. tose tisiya kumwa zimenezi
pa zed ndi k3. tose tisiya kumwa zimenezi
Minerals inali 140 mk?? Kuberana
Eya man ife timagula mk133
Eya man ife timagula mk133
Nthawi yandiphuzitsa zinthu
dats 2bad nde mkuwona ngati tingakwanise zimakomera inu konko ku town zaziiiiii basi
Madziso akweraa ndiye kaya tidzimwa chan kaya.?
Tidzimwa Madzi
In South Africa, 2 litre Fanta is at R15, 0.5 litre is at R8 while a 300ml bottle is being sold at R4. 750ml of Castle Lager beer is at R14 while 340ml is at R9
Utiuze za ku malawi wekha wachta kuona kti malawi24
Mwasanduka aku south africa musazabwele kuno
Wrong comparison Mr. Taymon Banda? 0/10
your prises x40 osangoti R9 apa ayi
nanga kuni ndi ku john usamaletu
kkkkkk #Taymon sanalakwise.koma wangoiwala kusungunula(fo-exchange)
Zithu zakwera oro kujohn ko usamanamize athu
#Taymon, as u ored knw RSA has many beverages & beer companies thats y the commodities u hv mentioned r cheaper..Take a gud comparison btwin MW & RSA pliz i beg ooo!
In CT, 2litres fanta =, 1.5litres R10, 300ml R6.50, all prices x 40,
,
zikusonyeza kuti kumeneko zodula zedi…. fanta @ 4rand=180mk ife pamene tikugula 160mk
Iwe R15 ndi bwanji kumalawi
Guys zithu zikudula jowen kuposa malawi koma ubwino wa kuno dola timaipeza mosavuta koma pa malawi eeeeeeeee ndi survival of da fitest tu!!!!
Kumatiuza marandiwo kuno nizingati?osati chabe kuno zikudula yet zauko we dnt knw ukamati 8rand nizingati kuno tizisiyanisa bobo
You can’t compare RSA and Malawi. The former is a developed where as the latter is below the poverty line.
Zikufanana man
Vuto ndi chiyani poti ndangokupatsirani mitengo yomwe ine ndimagulira nginiyo kunoko?
malawi 24, check your facts rights (on the non alcoholic beverages).
Mulibe shirt umu..
Kubwere ma company ena …d demand z high 4 ds underproducts yet d suply z low
they can’t,kamuzu sign 100yrs with carlsberg to work with malawi on monopoly agreement
So when wana d agreement end
hahahah sober man 4 lyf
Jst cz uli mmaluzi iwe…
Eeh bus tixingfulula paden
so the price for minerals was 140 kwacha?
Me wonder coz here in Mwanza tinayamba kugula k200 paka nthawi
tingosiya kumwaa
dyera lachuluka,economy izingogwb
zavuta pa malawi ambuye mulowelelepo