Mbava inatsakamuka kudenga komwe inabisala apolisi atathira utsi wokhetsa misonzi
Apolisi kwa Jenda akusunga mchitokosi njonda ina yazaka 33 zakubadwa yomwe inapezeka itabisala kudenga la sitolo ndipo anachita kuthira utsi wokhetsa misonzi kuti itsakamukeko. Malingana ndi mneneri wa apolisi m'bomali a Macfarlen Mseteka, njondayi yomwe… ...