Lolemba lokha palibe alepheletse ziwonetsero, wanenetsa Namiwa
Silvester Namiwa yemwe ndi mkulu wa bungwe la Center for Democracy and Development Initiative (CDEDI), wabetchera kuti kubwele mvula ngakhale kuwombe dzuwa, ziwonetselo za Lolemba sizilepheletsedwaso ndi akuluakulu a boma monga zachitikila za lero. Akulu… ...