Norman Chisale apezeka osalakwa pa milandu yoposera isanu
Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lagamula kuti Norman Chisale ndi mfulu pa milandu isanu ndi umodzi (6) kuphatikiza omwe anamangidwa kamba konena mau onyazitsa nduna ya za chilungamo a Titus Mvalo. A Chisale omwe… ...