Ka chakudya tili nakoko tigawane, atero a Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera apempha a Malawi kuti akondane pogawana ka chakudya kochepa kamene anthu ali nako mu nyengo ya njala ino yomwe imakhala miyezi yovuta kawirikawiri. Poyankhula lero Ku Dowa pa… ...